Keep it up brother mtanyiwa tiuzeni zinsisizo boma lamukanika munthu oipa ameneyi
@lyiemax
11 ай бұрын
More 🔥🔥🔥🔥 comrade, kuswakuswa, kuika MCP poyera, proud of you always 🔥🔥🔥🔥🔥
@Chrissyluwe
Ай бұрын
More 🔥🔥🔥🔥🔥
@JohnChibalo-wf8gr
11 ай бұрын
Mamina chakwera kufuna kupereka dziko ku ruwanda koma chakwera ukunama
@JamesMusheka
28 күн бұрын
Sure
@DishonieChisambi
27 күн бұрын
Zooon
@user-gs7wc3nx3q
2 ай бұрын
😂😂😂😂😂 koma nkhanga izi zimaonadi khosi kuti poto
@AugustineTheu-of6nv
2 ай бұрын
Bon Kalindo si size yawo akungozivuta agaluwo
@user-lz2wy7fr4b
11 ай бұрын
Awona kuti asilikali akumalawi ndi opepela akanakhal kuti ndi asilikali azelu akanapanga zoti chakwela adziwe
@MaxwellMustafa-ec8fc
11 ай бұрын
Asiyikali anthu wamkulu wawo anapasidwa bazi ndi MCP chakwera chifukwa chake ali ziii
@AminaPhiri-pp9tw
5 ай бұрын
Kodi asilikali alikuti mungomupanga step down chakwera yo basi
@AminaPhiri-pp9tw
5 ай бұрын
Nkhanga zawonadi koma step down chonde chonda asilikali anthu
@AlexManuelMisomali-sv1vn
2 ай бұрын
Awaponya miyala chifukwa akutetedza Chakwera ndi nduna zake mbavazi m'malo motetedza anthu
@user-cy3js1sf2u
10 ай бұрын
Tikufuna kt adzipita zigawenga za gagame auzeni adzipita sitikukhala mwa ufulu tikoopa agalu amenewa
@Edigar-nt8jj
11 ай бұрын
Osapanga bwanji? grup pa wasapu la nkhanga zaona timaku nyadilani ma boss
@JohnChibalo-wf8gr
11 ай бұрын
Ntanyuwa kulankhula mosapsyatira mosabisa chilichonse ndi kutchula mayina awanthu kuchosa ena ntchito ndiyikapo anthu oti azizunza anthu koma mukunama mulungu simunthu nkhati simukuchoka koma mufa nonse 😂😂😂😂😂😂
@joebrown1158
11 ай бұрын
Once again, where is Malawi 🇲🇼 defence force? Is really Malawi got Malawi defence force?
@JohnChibalo-wf8gr
11 ай бұрын
Chisiru chakwera panopa 2 years yathatu ndiye wasintha chani ? Pomwe unkalowa m'boma fertilizer ali pa k 17 .000 pano ndi k 90.000 kumeneko ndikusintha kokomera owalamulira kapena kuwapha 😂😂😂😂😂?
@DanielJuwawo
2 ай бұрын
Kuendetsa dziko simasewera ayi
@marryphili5419
5 ай бұрын
Koma chakwera mulungu akuwone
@AleksaWilliams-qc6cn
11 ай бұрын
Zomvesa chison
@AbuOsman-ts6ef
11 ай бұрын
Chakwera usamare Mulungu akuwotcha ndimoto
@yusufbakali-zm2hq
11 ай бұрын
Bolani atula pasi udindo chakwela
@mbaliehaward947
11 ай бұрын
Malawi watha
@mbaliehaward947
11 ай бұрын
Asilikali timakunyadilani tithandizeni
@AnishaMoosa-ej7yr
8 ай бұрын
😂 Kwayakatu
@user-gv9vl7uq2e
8 ай бұрын
Musasiye mutiziwitsa zambiri
@FrancisDay-br7xb
11 ай бұрын
Chakwera alufinika mademo anyoo
@Goliath461
11 ай бұрын
So sad to malawi defense force ,
@JohnConar-kq4hi
11 ай бұрын
Basi timenyana so amalawi okaoka self war🤔✊✊✊✊🔪🔪🔪🔪
@JohnChibalo-wf8gr
11 ай бұрын
Kodi nkulu waasikali tidziti suukuona ndikumva dzikuchitikadzi kapena uchisiru ndi mantha ndi zomwe zamanga m'mitu mwanu minyero yanu asilikali nonse
Пікірлер: 33