Ndikuupempha Mzimu wa S K chilima ukuvutitse manganya. Asagone tulo mtenderenso asaupeze mpaka imfa yake
@ThomasMlowoka
19 күн бұрын
Chakwera ndiye akufuna ma demo
@user-fy7qk6kk5s
14 күн бұрын
Comrade palibe cha mzeru chilichonse wachitapo chikangawa ndi amene akufunika mademo a dziko lonse lapansi,peter ndi mtunda 2025 akubwerera osati manyakawa, dzisilu dza MCP ana a satanic
@WilsonChisoti-dz6vs
19 күн бұрын
Chakwera ndiye afunika ma demo
@VeronicaChirwa-ct4os
16 күн бұрын
Ka michel usi ko nkachitsiru kwambiri
@MusaPatireck
18 күн бұрын
Tinazimbidwa ndikukhuta nthawi ya Peter ija lero ndizimenezi kkk
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
19 күн бұрын
amalawi tinazitemberera tokha kumuchotsa Peter Mutharika ndikumuyika satana pampando lero akutipha taonani amalawi anzanga koma ndikuona ngat kukhuta komwe timkakhuta ndi apeter Mutharika muja
@priscillamangata4023
19 күн бұрын
Paja amkati akufuna asitha ndiye asithaditu
@ChikumbaLenzo
13 күн бұрын
umakwana comred auzeni anthuwo
@ZainabZainab-sh2qv
11 күн бұрын
Comrade mmmmmmm ulind bodza 😂😂😂😂😂😂 mpaka nkhan ya degree yafika kumeneko
@EagerChicken-qj6xu
18 күн бұрын
Manganya usatilakwitse chonde yendelani zanu.
@ShalifuMatola
19 күн бұрын
Ausi akufuna kufa naye
@veronicagullo9373
18 күн бұрын
Amtanyiwa mudzapatsidwa u minister mu m,boma LA dpp
@JoyceBanda-k8t
15 күн бұрын
Amalawi mulungu atikhululukire chifukwa sitimadziwa comwe tikuchita chakwera anatiseka maso ndi mphavu zake wakumidima kt tisamaone ubwino wa peter mutharika koma kunena zoona chakwera alibe masophenya utsogoleri mwa iye mulibe koma mutharika abwererenso 2025 dpp woyeeeeeere chikangawa alongedze adzipita
@lukathamison1984
18 күн бұрын
Apa ndiye panja peni peni
@S-rr1eu
13 күн бұрын
Akazafa chakwela ndi manganya ndizasangarala
@HassanMillion
18 күн бұрын
Ngati akub madigili anthu ena mosiyeni naye afa ngati chilima tili popano ndithu
@ThoccoChimbali-h6g
18 күн бұрын
Vuto a malawi munaika chitsilu pa mpando, munthu kumtola chipiku mpaka pulezidenti?a malawi sitinali serious ngati dziko
@EvanceRazaki
16 күн бұрын
Peter muthalika ndiyamen tingamenyele khond
@yunuschiutula
14 күн бұрын
Palibe cha nzeru chachitika katundu wakwera mitengo ma business tinaduka
True he knows how Chilima killed manganya Utsi he failed to go n visit n see where Chilima n 8 others killed shame
@YasenYasen-q9g
16 күн бұрын
Chikangawa achoke
@AubreyMkwaila
15 күн бұрын
RIP SKC
@NancyNyelenda
19 күн бұрын
Chikangawa
@FreddieNkhoma
19 күн бұрын
Kodi ndani asakuziwa kuti UTM inachoka mumgwirizano, Ndichifukwa chiyani akugwilisa nsalu za UTM
@LilianKachala-yz2xf
19 күн бұрын
APM Sadayenele kuchitsedwa pa mpando pano tikuvutika Zedi.
@user-ky4ce9gb6j
18 күн бұрын
Ndipo zomvesa chisoni kwambiri
@JamiluSunday
13 күн бұрын
Sizinakhare bwino
@PeterBendeka
19 күн бұрын
Oyenera ndi chikangawa Peter inali nsanje chabe
@user-ky4ce9gb6j
18 күн бұрын
Ndipo zinari za against esh
@geraldjeremiah686
16 күн бұрын
Oyenera nd napanyelo uyu!!! Chakwela
@Blessingskanyinji-x7s
18 күн бұрын
Waiting for report ku fm ntanyiwa🔥🔥🔥
@MandalaChaona
18 күн бұрын
Michael Usi usamalise ndi unthira kuwiri wakowo, omweo ukudya nawo iwe mkumasangalala adzakupha. Devil at work 👹⚒️🔨⛏️⚒️👹
@JusticeKawilira
17 күн бұрын
Usi ndi wa MCP, Chakwera achoke APM pachiongolero APM boma
@Shelifibraheem
18 күн бұрын
Can't wait kumva report Mr mtanyiwa.
@ChikumbaLenzo
13 күн бұрын
umakwana manga
@CharityMhone-uk9ym
16 күн бұрын
Manganya si munthu ndpo zintchito zake zikuoneka kakuchita kusangalala ndikungolubwalubwa ngati gwape, osamva chison ndi ifa ya mnzako, ine ndee kamandinyasa kwabasi😮😮😮
Пікірлер: 196