amalawi musayembekele kuti azibusa angaitanitse mapemphero apadela malingana ndi ngozi zimene zikuchitika mmdziko lathu chifukwa azibusa omwewonso ndi asatanic ndiye sangayitanitse mapemphero akudziwa zomwe zikuchitika mwaona akabwera chakwela awaitana ku state house akasangalale
@zelliachamboto5744
21 күн бұрын
Ndipo inu daily ngozi😢😢😢 my heart is bleeding, God protect Malawi please
@AleksaWilliams-qc6cn
20 күн бұрын
Nsanje to Chitipa ambuye titeteza ife ana anu patokha sitikwanikwa nkhondoyi ndiyayikulu
@MandalaChaona
21 күн бұрын
Thanks Brother Mtanyiwa On LIMPOPO FM for today's updates . May God bless and protect you brother Mtanyiwa wherever you are. M T S R I E P ✝️✝️✝️. LORD HAVE MERCY ON US
@ABc-fk1uu
21 күн бұрын
Mmmmm km ine olo mulungu atangoti abwele lero sindingadandaule chifukwa zomwe zikuchitikazi sindizo
@ChristopherKabanga
21 күн бұрын
akakupezani mukutukwana anthu
@MariamJaffali
21 күн бұрын
💔💔💔💔 koma ayi ambuye atichitile chifundo zikutidabwitsa kwabasi
@KelvinMangwengwe
21 күн бұрын
Zomvesa chisoni zomwe zikuchitika ku Nyasaland 😢😢😢😢
@eunicesaiti
21 күн бұрын
Kwambiri, Ambuye atichire Chisoni. Lord please have Mercy on the nation of Malawi 🇲🇼. May Their Peace Rest in Eternal Peace 😢😢😢😢😢😢😢😢
@MaggieMuhone-r7m
21 күн бұрын
Ambuye tithandizeni ife ana anu
@DavidJackson-ox4xm
21 күн бұрын
Zomachita meeting ku Italy ndi zirombo za satanic mphoto zake ndi zimenezi
Mulungu yekha atithangatile Malawi wa mkaka ndi u hi lero dziko lokhala lathu tikukhala mwa matha mzimu yosala kwa iuse mutendere
@humphreyiman8512
20 күн бұрын
Amen
@JumaGadaff
21 күн бұрын
Wamakamu baba landilani mizimu ya ana anu osalakwa ponkhala nawo kumpando wachifumu alandileni 😭😭😭😭😭😭
@user-ss9bj5eh6b
20 күн бұрын
Dpp inamukanatu BUSHIRI lero ndiizi mwezi uno ndi birthday ya mkazi wa bushiri mwezi okhauno anthu omwalira 130 chaku pangozi Ambuye atithandize ndithu
mchifukwa chake munthalika samalola satanic kuti akadzikike mdziko la Malawi anakamuzembetsa wasatanic ku south Africa kuti azayambitse kumalawi tipemphe azibusa womwe mumapanga za miracle ndinu asatanic nonse
@SueWahna
21 күн бұрын
Eish zosayenda kwachitikaso ina nseu wa Zomba mmmmmm akusolora anthu minibus oh God 😢😢😢😢
Kwa nonse mwapeza Pass mayeso osabwereza it doesn't matter the grades pass is pass but Mbuli zikuti Mubweleze ngati certificate ya 8 or jc ungapeze ntchito
@zelliachamboto5744
21 күн бұрын
Ndipo inu aaaa
@samanthamuller7643
21 күн бұрын
iiiiii koma kumalawi kuno satana akuyenda wapasi basi ndi mr chikangawa uyu
why God? its not asin to ask Gid2 why??? is it bcz of Chakwera or the whole nation? have mercy on us God send the prophets to warn us as you said simuzakanga munthu musanamuchenjedze? is this awarning to us God?? tiyankheni ambuye
Пікірлер: 65