Thanks comrade, our true freedom fighter, keep the eye open and proud of you always 🔥🔥🔥🔥
@georgesmart3791
11 ай бұрын
Powerful nkhanga zaona❤❤❤❤
@FrancisDominic-w1s
2 сағат бұрын
Mumakwana itoseni itoseni acomsy
@amadichembe4068
11 ай бұрын
Mutanyuwa monimoni
@mbaliehaward947
11 ай бұрын
Zoona atiuze
@alexsumani6823
11 ай бұрын
Taona a Mtanyiwa alipo,koma ma comrade enawa have gone into a cacoon 🕺🕺🕺
@BILLYMACHOMBE-fw5nn
11 ай бұрын
OI amIf
@amadichembe4068
11 ай бұрын
achimwene nkhanga zizikumveka masana ano zauluka ? kkkkkkkkk
@FrancisDominic-w1s
2 сағат бұрын
Kodi lero timva zotani za aerio chair man anali kuchinawa
@mbaliehaward947
11 ай бұрын
Embassy wathu samatithandiza kuno
@JohnChibalo-wf8gr
11 ай бұрын
Mwanayo waphedwa ndi m c p zikanakhala kuti waphedwa ndi andalewo osakhala m c p bwedzi zitafufudzidwa ulamuliro wakupha kumphamvu ya mulungu ukuyenereka kutheratu. 😂😂😂😂😂
@moseskavalo3304
11 ай бұрын
Anthu amaganiza kuti azakhala muyaya padziko pano,, Kamuzu used to call himself life president koma pano alikuti, Blessings Chimangeni anaimba kale zaizi. Pangatalike pangatani aliyese adzafa and this is the fact
@user-nx7yz4qo8f
11 ай бұрын
Kod ziiiiyu bwanji Malawi first yonse sikumvekatu,KZitem siyikukomaso PANO antaaa,mulikut pls
Пікірлер: 27