Inu uyu Chawezi yu ndi defender wa MCP ndithu. Program iyiyi ili useless pa Mibawa cifukwa cha Chawezi akumaonetsera mbali. Apa bola ku TIMES kuja pa HOT CURRENT
@AlexManuelMisomali-sv1vn
4 ай бұрын
Program yanu iliyonse ngati muzikhala ndi Chawezi ndiye kuti mukuinonga chifukwa iyeyu simunthu yemwe anthu amamufuna malinga ndi fundo zopusa iyeyu amapeleka
@HappyBirchForest-zy8nq
4 ай бұрын
Wise bro sukunama chawezi is stupid man
@OwenChiwaya-nk2pc
4 ай бұрын
uyu mmati chaweziyu is a partisan guy! we don't want these kind of guys! ine I like victor chipofya coz of he is a neutral person
@ZaidJafar-kk9be
4 ай бұрын
zoba wa kokoliko iwe mboli yako mtola nkhan ochita kuonetsela mbali tisiyatu kuvela mibawa machende ako wava🖕😔😔😔
Chawezi is a good journalist but the trajectory he's taking is soiling his prowess. Advice to Mibawa is to engage him only if there is a political debate between political party representatives. He is more of a government spokesperson than a commentator.
@georgemponda
4 ай бұрын
chawezi ndi ndiwaboma sakutha program yi nchotseni we are not hear to listen all his allegations, bring someone who who's able to balance the debate mood akuwononga heavy..😢
@stevennthukwa
4 ай бұрын
Chawezi be serious you are on air people are listening to you There is alot of people starving in village even you nephews and aunt please be honest
@MarkBannda
3 ай бұрын
Education is a key, and pa Mzimba bridge ( chakazi) Mzimba South East electricity, no sankho, Mombela University 0, Mzuzu Air Port, 0 so DPP is 0
@rabisonpias5131
3 ай бұрын
Chawezi ndi Mbuzi. Iyeyu sakudziwa zoti ku Parliament zinthu zimayendera ma numbers? Nde ngati MCP ili ndi higher numbers . DPP kubweretsa Bill yochepetsa mphavu za President IF MCP sikufuna zingatheke?
@rabisonpias5131
3 ай бұрын
What is the USE of giving ACB a go ahead Kutengera Milandu ku Khothi, Pomwe Mphamvu Yothetsa Milanduyo ili ndi Anthu a ndale? Nonsense,!!!
@morgansilungwe
4 ай бұрын
chawezi you are so biased.i buy from victor's comments.political will from the executive lacks in the fight of corruption because truly omwe akuba ndalama ndiomwewo.chakwera is a big liar,all what he promised to malawians palibe chomwe wakwanitsa.he has to go
@chippakaribafox2865
3 ай бұрын
...pple knows alot than the president...chizuma did that because she knew that once nkhani yapita kwa amfumu yathela pompo amfumu ampita kukatapisa..allegedly.. She ddnt trust him period
@mkhulukinyata5198
4 ай бұрын
ULEMU WANU BWANA VICTOR CHIKOFYA , MULUNGU ADZIKUDALITSANI NDIKUKUWONJEDZERANI MZERU.. TSONO TIKAKAMBA ZA UYU WA YOUNG PIONEER YU KAYA MUKUTI CHAWEZI ", UYUYU NDIYE KWANGOTSALANO KUTI AKALANDILIDWENO NDI CHAKWERA PAMSOKHANO , AKAMUPACHIKE NSALU YA MCP PAPHEWA PAKEPO
@JamesChingombe
4 ай бұрын
Pa program iyi amuchotsepo chaweziyo akuononga program
@innocentmvundula6010
3 ай бұрын
I used to follow Chawezi with kin interest, I even praised him as a genius alas had I known aaaaa ngati amudyetsa Kenakake akabweze tikufuna Chawezi wathu osati uyuyu. Azinamiza Ana
@KabambeFrancis
3 ай бұрын
Uyu wamisala kwambiri,ofunika makofi. Musamamuyike pa air please. Ndiochititsa ngozi
@BehindThecamera-xo1qg
4 ай бұрын
Kodi chawezi simungamuchotse mu ma program yanuyi , amatinyatsa kwabasi. Sakuyakha funso akuyakha za mcp, chitsilu cha munthu
@D.RJALLI-qo6yd
3 ай бұрын
Achawez, Victor akunena ngani ndi yachulungamo wosati dzandale dzomwe mukujambadzo galu iwe chawez
@StevenMbama
4 ай бұрын
Program ndiyachawezi inee ndisaname koma amene mukutsogolela program musamupatse stupid program nonsense
@mustafahussein1140
4 ай бұрын
Koma chipofya you ndi WA nzeru kuposa nzakeyo olankhula mobwebweta
Victor umatha....awa ichiwezi mphuma yawo ya mayakhedwe awoo akuoneka kuti ndimunthu wa vuto...ndipo mboleyeke
@RaphaelKatimba
4 ай бұрын
Chwawezi ndi galu amabakila galu nzakeyu Chakwela ndipo mukapitiza kumamuika Chawezi pa program imeneyi anthu adzasiya kuinvela. ndipo mukungotaya nthawi yanu ndi galu ameneyu Chawezi..Mr Chipofya ndi munthu wanzelu kwambili koma amayankhula zoona zokha zokha zimene a Malawi 🇲🇼 akukumana nazo. Chawezi amangotaya nthawi ndi bodza mpakana kutuluka thukuta chifukwa cha bodza.
@lamesimatuso
3 ай бұрын
CDF opanga olundula ndi ma MP
@ChimwemweHenry-uw1bq
4 ай бұрын
Iwe chawezi usamale ndipakamwa pako...ineyo last year ndnawalipilira makolo anga ndrama ya fertilizer koma mpaka lelo sanalandre fertilizer-yo ndye uzikanena kt kwabwera cdf 200mita zantchito chani.kod ndlama zimenezija akanakapeleka ku ilovo bwez sugar akugulidwa pa bwanj??? Ndalama zomwe anabesa ku butchery akanakapeleka ku macompany a soap bwez atapindula amalawi angat.ineyo ndwa 28yrs koma singngamaganize mopusa ngt mmene ukumayakhulira iweyo.magesi sakuzima yes that's fine and good koma wachinyamata wa saloon ma customer akawatenga kt pot achinyamata akusowa zochita
@davidmaulana9277
4 ай бұрын
Chawezi ata ndithu
@CharlesMsosa-m9w
4 ай бұрын
Program iyi lilibe phindu chifukwa mwatenga munthu oti Ali ndi mbali ndiye anthu sazikhala ndi ndawi yoyitsata chawezi muchitsenipo kepana program iyi ithe pa radio wanu
@MustaphaChimangeni
4 ай бұрын
Chawezi kamowa amangoikila Boma kumbuyo zilizonse like victor chipofya he's a real man standing for the truth always
@thiyahdyton
4 ай бұрын
Munthu akamapenga sazidziwa yekha, amadziwa ndi anthu ona muthuyo, Achawezi siowowo ayi, koma.
@ShabaniKuswere
4 ай бұрын
Kodi Chawezi akudzataniso pa program iyi akuluakulu takhala tikukamba za mkulu ameneyu Kuti asamabwereso pano
@SildaKatundu
4 ай бұрын
Chawezi ndi wa MCP ,skufuna kuimira ku Ndirande. Asamakhale pa programme iyi
@andrewmazunda3846
3 ай бұрын
Chawezi ndi mbuzi. Take my words, ndale zikuonongera career,, trust me
@cosmasnkanda8193
4 ай бұрын
Chawezi ndiwe kape ndithu, you're there to support tonse alliance basi😓
Пікірлер: 108