Kodi Achimwene a Charles Sulumba muli bwanji? Ndine kuno chemwali wako Bethsider mkazi was malemu pastor Tavares, Kodi mukudziwa kuti Arch Bishop Zani akudwalatu and akazi awo malemu Agnes Zani anatisiya. Chonde mutenge may details anga ku chokera kwa mwana woopsya the DC you know how he makes jokes with the sense of humour. Where are you now still in Angola, Namibia or South Africa Hilbrow theatre are you still preaching there as a bishop? Please greet mai busa Pink and tell her tamusowa and a a onse. It was nice seeing you here on this plat channel.
@user-ww4ei5fb7d
10 күн бұрын
Amangidwe onse. Ku USA anzathu sasekerera zopusa. Trump ataomberedwa khutu, mkulu wa asirikali ake anakakamizidwa kusiya ntchito polephera kuteteza former president. Kwathu kuno VPkufa pangozi yosamveka koma anthu tiri duuuu kupsetsa mtima kwake.
@isaacchiwaula731
9 күн бұрын
Yamba ndiweyo ma demo-wo
@masartngs
5 күн бұрын
Uzani asilikali anu kuti atulepasi udindo chifukwa apangisa ngozi. Learn to differenciate things. Ngozi ndi chiwembu ndizinthu ziwili zosiyana kumakhala ndi umunthu.
@patrickgalawanda1100
4 сағат бұрын
Bon kalindo, Timothy mtambo,trapence Anthu omwe munasokoneza dziko pochititsa mademo So lero don't fool us
@HaliJana
9 күн бұрын
Big mani katundu amakwana mwana mlomwe nadya nakoka😊
@AleciaFrancis-d7s
9 күн бұрын
I used to underestimate Kalindo's IQ. This interview left my mind blown away.
@karenn2969
9 күн бұрын
I like this guy, he is a principled man
@WisikiBlack-gj4gu
10 күн бұрын
Ndiwe dolo kalindo
@TiyanjaneMkwate-we8gu
9 күн бұрын
Tili mmavuto chifukwa cha inu Akalindo ndi achina Ntambo,ena mwa amalawi osauka ndiokwiya nanu chifukwa munwalozera njiraya ku bagamoyo mmalo mwa ku canane
@user-wl7xn3or6d
10 күн бұрын
Chakwela akukuenela kumangidwa walephela
@user-xe5lb4uf3n
7 күн бұрын
Ulemu wanu Mr Dc
@gkay-striker
9 күн бұрын
And Chakwera akamakuona iweyo amatsegura nawe mmimba 😂😂😂
Пікірлер: 65