I support your opinion Koma zoti pali Bola mwawiliwa ndiye kwaine ai Peter kulekerera zinthu two much ngati chakwera yemweyunso ndiye sindikusiyanitsa ndianthu okhutitsa mimba zao kuiwara udindo .
@JohnPetro-vv3er
24 күн бұрын
Malawi need people like Dr chilumpha very brilliant
he seem to be a good and experienced leader. alibe mbiri yakuba
@EricKaikhediKhozalimoChirambo
20 күн бұрын
I have always been worried about the bill for the entire electoral process.
@LilianKachala-yz2xf
Ай бұрын
Waoooooooo mr Chilumpha.Now. U are Speaking God bless you
@Harlod5566
Ай бұрын
Uyu nzeru zirimo ndithu. Ndipo alibe nkhwidzi ndi munthu koma Chilungamo chokhachokha. Sungalamulire bwino opanda experience (UKADAULO) Walongosolanso bwino za chisankho ndi zina zambiri. Wa nzeru akuvomereza.Bingu anamumanga komaonani akuyamikira ng'ono wake Peter Muthalika. 🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🙄🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔❤️👍
@wisemanbanda8465
27 күн бұрын
The man is genius ...he's saying the truth
@HopeKhembo-qe7qs
21 күн бұрын
💯% even a tac shop they need experience people what more a country
@georgemponda
19 күн бұрын
This is true.
@Jermah51kennias
Ай бұрын
Apayu Legend nde mwayankhula momveka bwino okumva wamva
Osangopita kwa apule ndikukaunikila Pomwe akulephelapo bwanji
@user-ee6be5kl5o
Ай бұрын
Munthu you akuyankhula za nzeru ndithu ulemu wanu kuyankhula kuposa pulezidenti chakwera
@HopeKhembo-qe7qs
21 күн бұрын
Vuto laku Malawi oimba Ati akhale MP.azisudzo MP
@user-pv9uk6sc3w
Ай бұрын
Tiyamike Thokozani Chiwaya chifukwa ukuyesetsa kulondola aliyense, ndipo ukukwana Thoko. A Mr. Chilumpha ali ndi mtima okonza Malawi mosakaika, koma akhwima, koma akunena zoona.
@user-xb4fo7tk6b
Ай бұрын
Thank you so much bwana, it really means a lot to me
@ElizabethMajiga
Ай бұрын
Chilungamo chabwanji ichii❤❤❤❤❤❤❤
@FatimaUmali-pc8sy
27 күн бұрын
Uyu ndi munthu wa bwino Allah akudalitse mene mwayakhulilamu ndi zosowa kuyakhula chulungamo mwa uamikilaso Peter bingu pazomwe anachita pa Malawi
😂😂😂😂😂 sanamangeko ndi toilet yomwe ku assembles 😂😂
@ChikumbutsoPortpher
29 күн бұрын
Unakalamba
@FrankBaison
Ай бұрын
Zoonadi chakwera sakukwanila kukhala president
@TrinityManeya
Ай бұрын
Zamzeru kwambili
@odarm4334
Ай бұрын
Akuti "sindimagwira ku Chipiku iyai" 😂😂😂😂
@user-pv9uk6sc3w
Ай бұрын
Mr. Chilumpha mukusongosola chilungamo, Chakwera ndi chilima sadakonzeke komanso ni mbuli pa kuyendetsa Boma. Chakwera amapusha Wilber lomaso crerik ku Chipiku basi. Sadziwa chilichonse za boma.
@Dorah-zl9uf
Ай бұрын
😂😂😂
@peterchikwakwa8476
Ай бұрын
It's true what chilumpha is saying, malawi we made a mistake
@user-wn2hm2dc8e
Ай бұрын
Yes Mr chilumpha We made a big mistake
@wisktepani-bo3fw
23 күн бұрын
Zoona ndithu taziona ndi maso bola mutharika
@user-xx4jb9se3z
7 күн бұрын
Zoonadi ndipo muthalika
@user-wd9yd1bg9n
Ай бұрын
Madala oona patali kwambiri
@blessingsmangulama8442
24 күн бұрын
zala zathu zinatilakwisa. tingozidula basi
@sharifujoe7633
29 күн бұрын
No fundo iwe that's why anakuphatula Amuluzi then anaona bingo wamutalika
@audreymoffat1356
29 күн бұрын
Mau omwe anatichenjeza ndi kulozera pa debate aja ndi Atupere Muluzi ndi awa akupelesera ndi kaka
@user-gj4li2gc8o
Ай бұрын
Nkhalamba iwe unakhala 10 years unakwanisapo chani pa u vice president
@charleskafodya7019
Ай бұрын
🤐😛😛😛
@user-bn3fg7sm2o
29 күн бұрын
Kulankhula mosaphyatila,zoona,zokhazokha
@EuniceSomanje
Ай бұрын
😂😂😂
@OrtonKabbichi
29 күн бұрын
Chilima analakwira a malawi chifukwa cha jelasi
@danielmsowoya9107
Ай бұрын
Mwa inu muli magazi a UDF simunganene chilungamo baba
@danielmsowoya9107
Ай бұрын
Vuto mpira umayamba kuuona ukatuluka mu ground. Mwakhala m'boma zaka zambiri lero mwayamba kuona mavuto a anzanu
@lonjezomainjeni5803
Ай бұрын
Chilumpha ndi dolo amalawi timakhala ndi phuma koma next year achoka osadandaula
@GilbertKaliwa
Ай бұрын
Kodi iwowa angaloze, chiani chimene anapanga Ali mp ku chia munthawi ya udf I was there nothing Ata kukoza hot springs madzi mawir a
@ziyamporoma377
Ай бұрын
Uyu ukalamba wamufikadi mmafupa ndithu. Zoti Chakwera was leader of opposition sakudzika? Ku america akukutchulako did Trump hold a public office before the presidency?
@user-se8ze3fn3o
Ай бұрын
Chipiku boy 😅
@ineyomphunzitsi5554
Ай бұрын
But the other muthalika anakuthila dzigwe osalakwa
Пікірлер: 139