KODI MUZINDIPATSA CHAKUDYA? AFUNSA MOKWIYA NKASA
Anthu mdziko muno anadabwa mkhala kale pa nyimbo mdziko muno, Phungu Joseph Nkasa akuwonekera ku msonkhano wawukulu wa chipani cha Malawi Congress (MCP) kumene amayimba nyimbo yake yatsopano, yandale ime wapekerea mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ndi chipanichawo chawo cha MCP. Kamba ka ichi, anthu en amdziko muno amamunena kuti samva ndipo walakwitsa poyimba nyimbo yotamanda chipanichi. Komatu atafunsidwa za nkhaniyi, woyimbayu anati sangasiye kuyimbira anthu andale popeza ali ndi banja komanso ana amene ayenera kuwasamalira powapatsa zofuna zawo, ndipo ngati sayimbira anthu andalewo apeza bwanji ndalama zosamalira banja lake. Kodi muzindipatsa chakudya? Anatero Nkasa.
Негізгі бет PHUNGU JOSEPH NKASA WADYA ZA MCP
Пікірлер: 21