Mutalika akuwoneka bwino kwambiri timangomunyoza akadali ndi nzeru
@paulmakaula4937
10 ай бұрын
One of the best assuring speeches from the true servant leadership...mabodza a boma onse ali pa mbalambanda...boma lanji lodana ndi REFORMS...Apa a Malawi 🇲🇼 mwazimvera nokha utsogoleri wabwino after Bingu ndiye ndi APM basi...anatiphula mu cash gate apaso atha kutiombola mu 3 months only! Apapa ndayamba DPP 2024 camping 🏕 basi...
@maxwellntungama2003
10 ай бұрын
Politics is a profession where people venture in to sustain their families.
@rashidsaid2232
9 ай бұрын
Kukhala Chete sikupusa DPP is greatest democracy in Malawi God bless DR president Mthalika Mthalika
@GiftFrancesco
10 ай бұрын
Respected to you thanks for coming and to talk Tu your people thanks
@mabletungande349
10 ай бұрын
Only chilima wud change our country.Chilima has my vote
@jafaranusa503
10 ай бұрын
I'm gonna fasting for you to win in 2025 May almighty God continue to grant you knowledge ❤mr. President
@MarryMummy
10 ай бұрын
Too far. This year we want change.Amen
@rechealbracia-vk7np
10 ай бұрын
Chakwela ndiwe bb ndipo kungonva kuti wafa tsiku la Christmas lisitha kuzakumbukira dzana la chilombo iwe! Ndizako Chilima munve kut anthu akupephera kut bola miyoyo yanu isakhalepo kt anthu 17 million apulumuke. God munve kulira kwathu😢😢
@IbrahimWezely-qd4vj
10 ай бұрын
Kabambeyu ndiyemwe ine ndimamuona kuti ndi solution ya malawi
@MarryMummy
10 ай бұрын
We are doomed, are these the choices we have. Who is less evil to the citizens. Come on dpp, you have a great Economist ,make him president for you party and let's get rid of the Nonsense not tonse , government
@chippiephiri4505
10 ай бұрын
I love this speech may the good Lord keep blessing Mr munthalika
@BusiBusisiswe
10 ай бұрын
Tabwezani matayi mwazimanga kwambiri mukulempela kuyankhula maka amsaka 😂😂😂😂😂😂
@user-xe7zi8pr2l
10 ай бұрын
Pls Mr APM may God bless you all the time we're waiting for you to rescue us in aur loved Malawi country agaruwa atikwana ife tanchona mumaiko ano ayeni because of those people who call them self tonse alliance the don't know anything about running the country wht the know ndikuba basi in fact ndika group kamamafiya akuba komaso kwawo ndikupha
@DamianoKapachika-ft1ye
10 ай бұрын
Ilove dpp
@henrymkwapatira
10 ай бұрын
Madala team, zinthu zimayenda ndi nthawi, kukwera mtengo wa zinthu ndi nthawi basi, osamnamiza anthu
@patrickmacheso5062
10 ай бұрын
That's my vote ❤❤❤❤Yes indeed APM can change this Government only for 90 days very true, but Chakwera even titampatsa 20 years nothing can change only ana ake ndi mkazi wake plus azipongozi ake.
@user-vq9if2ep5q
10 ай бұрын
Adad....Boma iro❤❤Ife tili pa Mbuyo panu.....osaopa ...more fr🔥🔥🔥
@alinanegulumba8277
10 ай бұрын
I Like how blind we are as Malawians 😅😅😅😅 timayiwala mmmmmmmm
@aaronkachipeso3586
10 ай бұрын
kkkkkkkkkkkkk ameneyo nde mMalawi
@leviticusbonfancio
10 ай бұрын
Kunena chilungamo we were blinded pomuchotsa Peter pa mpando zilibwino chifukwa zafikapa ndipa usandiuze naneso ndunvutika 😢, eeetu 2025 Dpp ikalowa m'boma ikonza ma mistake ake akale aja poti adali wochepa osati izizi.
@noelmunthali3516
10 ай бұрын
Bright Msaka you are very bright
@Maggiemarket-wx5wu
10 ай бұрын
May almighty God continue to protecting you and gives you more yrs tinkaona ngat mukutisocheresa koma pano taziwa kut munalidi munthu wolungama mwa chimwenecho mutikhululikire pa zomwe amalawi tinkalankhula pa ulamuliro Lero alimi ife akumudzi tikusowa chichita tilibe ndalama zogulira fertilizer sitingakwanise kugula thumba limodzi 110 0000 mpamene mu nthawi yanu inali 17 to 18 Kulima ndiy tinalima koma mbewu tilibe ma ID athu Anatipasa koma mulibemo kalikonse anatinamiza kut muli mbeu komaso fertilizer komati bwana kukapangisa scan kupezeka kut ma ID aja ndiya Empty kotèro bwana ndi kugwada pamapazi anu bwana kutula nkhawa zathu monga ife akumudzi tikuvutika msima tikumadya ka wili pa week chifukwa chakapezedwe ka zakudya kakugisowa tikusowa mtengo wogwira pano bwana
@madalitsosingle744
10 ай бұрын
This is wat we call a leadership ❤
@webstermbewe8395
10 ай бұрын
Yes there is need for muthalika to come in and dialogue the chakwera
@preciousmaononga
10 ай бұрын
We need you back, sorry kusamva kwa2 pano tkulra nako
@LameckMagona
9 ай бұрын
Go on dpp we need to change
@user-yn9ky7gj7v
10 ай бұрын
Peter yemweyo 2025 bas mbanva zichoke chakwela ndi chilima chokani mwaulemu
@user-kr1kg5hy9l
10 ай бұрын
Bravo my president.you deserve another chance
@austinkadzuwa7273
8 ай бұрын
IS THERE ANY CHANCE TO SPEAK WITH PRESIDENT PETER ? I HAVE SOTHIN G TO TELL HIM BUT IN PERSON .
@user-bq3xk1dg5y
10 ай бұрын
Sitikufunaso mzukwa uwu wa ku Thyolo udzatilamuleso.
@idrisssaladie5078
10 ай бұрын
zeru mumakhla nazo when you are out of government. mukalowa ubongo ose umathawiria kuchinena.
@austinkadzuwa7273
8 ай бұрын
i wonder who typed the name of president wrongly without fixing it . that is very bad . anyway i wish president Peter can be a minister of finance not a country leader neither LAZALO .
@user-ko9ht2pj8d
10 ай бұрын
Amai awa 120000 feteleza shop itiyo a navicha kupanga rent minda musaiwale kwanu kulibe minda ili mmanja mwa ma estate tisanyozeke kuti mukupanga rent minda kwathu kuno uzani a Malawi chilungamo
@user-bq3xk1dg5y
10 ай бұрын
Sorry Mr APM,you are in the shadows of incompetence. Your government did nothing to the development of Malawi. Today is not tomorrow.
@Littlefair7
10 ай бұрын
Pemphero la mtundu wanji ili? Ku malawi kulibe opposition. Boma lolephera nayonso Opposition mbola. Atolankhani athu mbola, amafunsa mafunso opusa ndi opanda phindu. Tinali ndi Eunice Chipangula pa dzana, ankadziwa kufunsa mafunso osati izizi, Kaya ma school ake anapita kuti. Mbola
@user-ko9ht2pj8d
10 ай бұрын
Munali muboma munalephera inu kozani kaye mavuto akuchipani then mutiuze solutio ya dziko
kodi mulibe office? Basi anthu akulu akulu peya peya kunyumba ya munthu?
@macdonaldmunthali9895
10 ай бұрын
Yes Malawi is in bad shape but dpp is not a solution,too much tribalism
@kalimawandale7161
10 ай бұрын
Did you accept defeat Mr APM? Kuvomeleza nkofunika kenaka mupepese kuti mutapasidwa mpata nanunso dziko munaliononga
@HarodNyando
10 ай бұрын
Aaa Aaa Aaa ndie chani
@HumblenessTafari-sc8xs
9 ай бұрын
He just said that the. Depreciation is man made
@BlessingsNyoze
10 ай бұрын
That's great
@user-yn9ky7gj7v
10 ай бұрын
Eyetu nde udolowo nyumba izinkhala ndi office
@CharlesNambela
10 ай бұрын
Zomvensa chisoni kwambili zipani 9 zoona kulephela kumanga chimodzi tikati dziko la Malawi mwina zithu tiona za chilendo koma mbuzi zeni zeni moni Steven maseya i hop uremember me I ❤ DPP A busa awa ngakuba Kwambili Pls tikupepha ma vote 2024 pls pls
Everyone must vote for peter of course who else can Malawian vote for someone else except p.m , chakwela asazawone ndi vote imozi yomwe, pake wamubo lake iyaaa .😢 shameful on chakwela mufiti yomwe sakuva kulila kwa anthu
@LuckyEmmie-ht1nk
10 ай бұрын
Wa nyau party ukumva bwanji ku dambweko 😊😊
@VincentSinos
9 ай бұрын
I love u fadah God may bless u ❤❤❤❤
@clintonhodda9830
10 ай бұрын
Dpp chipani chosamalira anthu osauka
@SymonMwingitsa
10 ай бұрын
Inu zimenezi musatiwuze ife zimenezi mukamuwuze chakwela kuseliko ife palibe chomwe tingapange anthu okula mtima inu musangatithandize nonse ndi mbamva
Mmmm Ona macoment inuyo zuyekuyenderani vuto kondwani ndi azake angofuna udindo not masomphenya
@ziyamporoma377
10 ай бұрын
Koma aMalawi muzitengapo phunziro. You're now excited with the same APM you kicked out just 36 months ago just like you were excited with Tonse alliance 😅😅😅....learn to be rational not emotional
@francistsutsu4811
10 ай бұрын
koma zoona zimene akunena a Bright Msaka? bwanji osauza a Malawi chilungamo. kodi mmatengera a Malawi kuntoso bwanji? you are just taking Malawians for granted. kodi chifukwa choti a Malawi ambiri ndiosazindikira? basi kufuna kuwazunza a Malawi ndi mitima yanu yongofuna kuzikundikira chuma basi? enafe tatopa nazo zamabodza zanuzo.
@MwenyeCheNsoma-gb2yz
10 ай бұрын
Worthy watching osati zina zija
@user-yn9ky7gj7v
10 ай бұрын
Nthawi ya peter timadya kanayi osat uyu wa nyawuyu angoyendayenda munthu nkulukulu
Inu tinakuonani kale nanu munalephera kale musatipusisepo boma lanu mumaliso ndi mavuto aakulu kwambiri. Bola tiyeseko ena amu dpp momwemo Koma usati inu madala ayi
Koma Amayi mwarankhula bwino... Ambuye Akudalitseni
@DennisMakanjira
10 ай бұрын
Adad omwewo 2025
@yusufsadic2930
10 ай бұрын
Vuto lomwe ine ndimskhumudwa ndi dpp ndilakut kosuts amazimvetsa chison kwambir kom akamalamulir amakhal anth amwano limandinyasa zina kt An adhat lelo mul kosotsa zakuvutan
@clintonhodda9830
10 ай бұрын
Ndiye mungayelekeze ndi manyaka apanowa
@goodvisionmedia2023
10 ай бұрын
❤❤❤❤❤❤ APM
@BusiBusisiswe
10 ай бұрын
Chipani chot chalamulapo never my vote
@ChisomoNthumbo
10 ай бұрын
Zopanda ntchito izi inuso musakhale ngati abwino zinakuvutani kale izi ndi zizindikiloza masiku otsiliza mukawelenge bible muzinamiza anthu osazindikila omweo
@memorygondwe1635
10 ай бұрын
Adad 2025 boma❤
@usseintomasbacar8612
10 ай бұрын
Koma Maseya pa prayer NDE mwaiphatu
@madalitsoyobex1642
10 ай бұрын
True why devaluation comes when people are expected to buy agriculture inputs why why chakwera knows nothing
@user-ko9ht2pj8d
10 ай бұрын
Look at statistics from 90s kwacha imapanga gain only time ya tobacco tikamafika these months get affected and mind you tobacco selling seasons imafika November koma pano by August msika watha where do you expect it to gain?
@user-ko9ht2pj8d
10 ай бұрын
That's why Kabambe you had the audacity to grant your colleague loan ya 187 years eti ? Mumaononga chuma ndinudi you have come out in open kuti muli mu boma you were the ones enjoying
Akuluakulu ndi dambo mozimila moto a bro....even judges put on white hats meaning to say there's is wisdom in grey hairs
@gilamwelekedwa4889
10 ай бұрын
Why boma should pay school fees for everyone’s kids school fees for mai osauka why can’t they work for their families instead of waiting for government is it not the same thing that AMP is blaming Chakwera that is bagging IMF loans of free money to run the government instead of finding ways of getting our forex economy in order. Ife school tinaphunzira yolipira nthawi ya Kanuzu Banda.
@AugstineManda-pl1dz
10 ай бұрын
You malawian why saying 2025 it's 5 years that's 2024 voting constitution ya dziko la malawi imatelo osati 6 years malawi wake uti?
@MaxwellMustafa-ec8fc
10 ай бұрын
I thought is my phone me too no sound, dpp is my trust.
@DwinDwin-d3w
10 ай бұрын
Zidakukanikani kale chipani cha family ichi munadya kunakwana palibe chachilendo pa zomwe odalawa ayankhura ukamakalamba umakhala ndi makani...siyilani ena achiteko mbali Yao za inu zinatikwana..
@stankaphinde7259
10 ай бұрын
Adadi 🔥🔥🔥
@user-vx4vu9pz2t
10 ай бұрын
Koma ndiedi a chakwera chizungu amathadi koma pa ground jee
@user-lw4hw9ce4w
10 ай бұрын
Apm ndi machine including their executive 💪
@user-ko9ht2pj8d
10 ай бұрын
Machine ogona mpaka tpin izigwilitsidwa ntchito ndi bodyguard memories still fresh
@user-ko9ht2pj8d
10 ай бұрын
Olembedwa ntchito mosaoneka bwino apose aku mombera University?
@GiftKatunga
10 ай бұрын
Boma ili latipha koma adad adatiuza koma kusamba anthufe
@lloydmazengela
10 ай бұрын
Zikuoneka ngati a DPP sakuziwa chomwe akulankhula akalankhula za kusowa kwa mankhwala zipatala ulamuliro wawo Ku chipatala sikumapezeka mankhwala,,, komaso ndi anthu ozikonda kwambiri,, ongoona zao zokha osati za antnu,,, lero muli busy kunamizatso amalawi ndizambiri zomwe munakanika
Пікірлер: 170