Listening you from Zambia 🇿🇲, May God protect you more Man of God Kambili
@patrickndojime1632
Ай бұрын
Abusa akambwiri Mulungu adzikudalisani ma unthenga anu onse munthawi zonse ❤❤❤❤❤❤❤❤❤ Amen
@user-iq5xk6ju7y
Ай бұрын
A very good reference to Malawi. Let SKC be Moses but our Joshua is not here yet neither what we are remaining with. MAY THE SOUL OF Dr SKC KEEP RESTING IN ENDLESS PEACE 😭😭😭
@LinesiKanzota-fw7sj
Ай бұрын
Amen pastor kambiri mwatilimbikitsa ulemu NDI matamando zipite Kwa iye wamwambayo
@StevenMbewe-d8x
8 күн бұрын
Mulungu apitilize kusunga pastor kambiri ndimoyo wautali
@user-ks2fq6ep4t
Ай бұрын
Pastor kambiri you are a blessing to us, we mourn with u here in Zambia.
@CharityKachigamba
8 күн бұрын
Amen powerful msg
@victormaluwa6710
Ай бұрын
Amen Pastor 🙏🙏🙏
@LuskaMoses
20 күн бұрын
😢😢😢poti simulakwitsa ambuye munaxhitira dala kuti tione akapuku kudxiko kuno kuti ndani ndipo tikwaonadi eish ambuye chitani monga mufunira😢😢😢
Abusa zikomo kwambiri chifukwa cha uthenga wotilimbikitsa , Zoona ndi Mulungu yekha amene Ali ndi mayankho a zonse. Mizimi ya abale athu kuphatikiza a Vice President iuse mumtendere
@user-zs7yq3tj7n
Ай бұрын
Mulungu atithandize kunvesa uthenga wabwinowu mu thawi yowawisayi
@kondwanivyalema9449
Ай бұрын
Blood shed mcp
@HusseinMoffatt-mi1fl
Ай бұрын
Komaambuye achitapokanthu Kwa achakwela ndi MCP yose ndiinu ayipisitsa kobas 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
Пікірлер: 77