Chomde nyoooo ndi manganya abwelele please komanso uthengawu mundipepheleko kwa vice president wadziko lino kuti chonde athandizeni anzanu atikufelanji kuti nawo atukukeko maka azakhali please!!! Its advantage ya ma members atikufelanji kuti nawo awone kusitha
@lameckmajiga5426
Ай бұрын
Pepho langa ndilokuti bwana micle usi pamene ali vice president wa dziko lathu lino! Asatisiye m'maleleyi chifukwa ndi avice! Kod malamulo aboma samalola kumapanga arcting ali pa udindowo? Komamso chomwe ndawona kwa micle usi ndichakuti wakwanilisa kupanga zithu zomwe amkazinena mu masewelo za ma civle servant ndi ma reforms relo akuzichitadi!!!! Zikanakhala kuti muziko muno kuli athu ngati micle usi zikoli litasitha kwambili
@FloridaOssy19
Ай бұрын
Ineso ndikuwafuna A Vice President athu Akuma bebesa Kwa basii ❤️🔥ndengat zili chocho aziyendesa zonse dzisudzo ndi u president
@ThomezNamaona
Ай бұрын
Manga akuyenera abwerere pa tikuferanji basi , ife tikudikira mr VP by pabric demand
@Senifala
Ай бұрын
This is super movie.....watching from joz.....ndakunyadilani guys
@ChimwemweKamfoloma
Ай бұрын
Much respect to first capital bank for funding the program again 😅😅
@jessienkhoma2492
Ай бұрын
Ine ndufuna winiko please
@GrantNorman-ir6if
Ай бұрын
Welcome back Chisi's family
@chigokhalid9420
Ай бұрын
Please abwelesen Mr Winiko mr Nyooo
@sharrifgwape7169
Ай бұрын
Komaso musamuyiwale mlaka maliro chonde
@amauzak
Ай бұрын
Koma ine winiko ndi ching'aning'ani akhalemo ndi mo faya
@rashik97
Ай бұрын
Inenso ndikufuna kuti programa imeneyo ibwererenso. Ndipaphunzira kwambiri za chikhalidwa cha amalawi. Ndimasangalala ndi dramawa.. ndathokoza kuchokera kudziko la Perú.
@beezboi1050
Ай бұрын
Ndale zinatisokonezela Tikuferanji
@FloridaOssy19
Ай бұрын
Winiko ndi manganya a bwelereso ❤❤
@georchilunga8596
Ай бұрын
Koma Vp adah 😅
@EthelOsman
Ай бұрын
Mlaka ndi mkazi wake abweleleso
@IbrahimkDyman
Ай бұрын
Ngati winiko ndi gitabo sakhalamo nde bola musayambiseso
@BatisonKalonga
Ай бұрын
Winiko abwelele msewelo please
@EthelOsman
Ай бұрын
Ineso ndasangalala imaphunzitsa chikondi ndi chikhalidwe
@YusufJimmy-v1o
Ай бұрын
Achita bwino tizionera
@FisherAction
Ай бұрын
Well come back all
@YusufJimmy-v1o
Ай бұрын
Achisi ndi vp tawasowa
@JoyceLiwonde
Ай бұрын
❤❤❤
@CaphusJailosi
Ай бұрын
Watching from sauth Africa cap town
@geofreydzinyemba6107
Ай бұрын
We want you guys back
@jessienkhoma2492
Ай бұрын
Welcome back tikufelanji
@SparrowBanda
Ай бұрын
Welcome back ma guys ulemu wanu
@sharrifgwape7169
Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂ndiye mwati a vp azipezeka mutikuferanji
@MICKSONMSAMPHA
Ай бұрын
Inde inde inde
@khodotech6481
Ай бұрын
Ine mwandidutsa pati osandifusa abale.... Mawa ndikudikilani pa Depot
Пікірлер: 43