Ndithudi tinachokera kwa Allah ndipo kwa iye ndikomwe tidzabwerera💔💔
@chimwemwematias6069
10 күн бұрын
Ndikukanika kumvetsa izi am speechless ndithu aaaa I will miss u Mr chibiliti RIP
@blessingsalim3218
8 күн бұрын
Mmmm mzimu wao uutse ndi mtendele 😢😢😢
@sayidimisessa
10 күн бұрын
😭😭😭😭 nzimuwawo uwuse muntendere kuchokera kuno ku South Africa johannesburg ine ndimmodzi mwa anthuso amasatira tonde wadula : magawo ambiri omwe amatenga achibiritu pa sewero, adali. Ophuzisa limodzimwa magawowa, ndi ( kutha banja komaso opandakathu nkubwerera kumakakhala pakhomo paazibale ako, umakhala chisiru) (komaso pabanja masiku ano samalimba ukakhalakuti ndiwe lova/opandachochita? Achibiritu , ngakhale ife kuno kunja kwa malawi tikukulirani R,I,P 🎉🎉🎉
@user-py1qj1nv6y
10 күн бұрын
RIP Mr Chibiliti.YOU WILL NEVER WALK ALONE
@ChisisiSaynett-nm7uq
7 күн бұрын
Zimu wachibiliti uuse muntendele😭😭😭😭😭
@lillahnmahuzahshabah5883
9 күн бұрын
We will miss Mr chibiliti😭😭😭
@user-zi7lt4gg5e
7 күн бұрын
Eish like ndikulota 😭😭😭😭😭
@vincentmatemba1659
10 күн бұрын
Yooh we will going to miss you mr chibiliti 😭😭😭😭 mzimu wanu uuse mumtendere
@user-qs2tx7wt6g
10 күн бұрын
We miss you chibiliti
@elizamaster2168
9 күн бұрын
Mmmmmm 😭😭😭 ndazizidwa nd uthengawu,
@RabsonJosephy-py5hy
9 күн бұрын
Rest in peace Mr chibiliti from Pretoria 😥😥
@owenmagagamsowoya4036
10 күн бұрын
Deep from my heart am really sorry may his soul rest in peace ine ndili kusouth Africa koma ndimasatira ma comedy ose kuphakizapo tonde wadura achibiliti Asiya gapu ku tonde wadura
Just to see the video inenso kuyamba kulira. Ndaphunzira zambiri kudzera mwa a Chibiliti. Kudzichepetsa kwawo komwe akufotokoza anthu osiyanasiyana kumaonekera ngakhale mu sewelo. mmene anadzichepetsera kubwelerana ndi anagumbo, mmene amadzichepetsera achina makwale akamawazumza. MZIMU WAWO UUSE MUMTENDERE
@peternashyo9850
10 күн бұрын
Oooh! too bad. a Chibiliti luso lanu tizalisowa, Mzimu wanu uuse mumtendere.
@watipasomzungu9911
9 күн бұрын
Tood bad! May God rest his soul in eternal peace.
@gressiabel6850
10 күн бұрын
Mzimu wawo uwuse mu mtendere.
@EdythGloryNamponya
10 күн бұрын
Amadwala mmmh abale...we wl mis you achibiriti😭😭😭
@franciscoduartie5762
9 күн бұрын
Ause mu mtendere Mr chibiliti.
@BoccatiKaliyati-ky7cv
9 күн бұрын
Tidzakusowani pasi pano ndithu bambo chibilitu RIP
@AleksaWilliams-qc6cn
9 күн бұрын
RIP MR CHIBILITI,KOMA MWEZI WA JUNE UWU EEE TALUZA ANTHU AMBIRI
Sinto muito ,,, vou sentir saudades ! Que deus abençoe voce!
@zaithwachiwaya8885
10 күн бұрын
Rest in peace Mr. Chibiliti😭 luso lanu tilisowa
@mafukenimasangwi5487
10 күн бұрын
Eish koma imfayi
@khumbophiri9006
8 күн бұрын
Inna lillah wa Inna ilayh rajiun mzimu wawo uwuse mumtendela😭😭😭😭😭💔💔💔
@user-yp9gn2km5q
3 күн бұрын
Rest in peace mr chibiliti.wl never forget you.
@IsaacKachala-ny9km
10 күн бұрын
😢😢😢 Rest in peace
@marryrobert7092
10 күн бұрын
😭😭😭 RlP mr chibiliti.
@AnabelleBanda-gx9ii
9 күн бұрын
Ummm rest well Mr chibiriti tikusowani mu tonde wadula ummm 😭😭😭
@shamiunamuhammad9081
9 күн бұрын
Rest in peace Mr Chibiliti imfa za chonchi zimakhudza heavy
@BenjaminGondwe-po5dq
9 күн бұрын
Mmmmm mzimu wawu uwuse mutendele
@LukaAron-el5qh
10 күн бұрын
Naneso ine kuno ku south Africa ifa ya a chibiliti yanditulusa misoni, maka maka mene amayamba kulira atonde wadula nane zinandililisa zimu wawo ukause muntendele R.I.P 😭😭😭😭😭😭
Пікірлер: 365