Ana Amma 2000 za mcp amkangomva lero aziona okha .
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
Күн бұрын
A UDF mumakhumudwisa anthu mumanena zina kupanga zina
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
Күн бұрын
UDF ITS MY PARTY AND I WIL NEVER ABANDONED THIS PARTY
@HenryTrevor-nb4ik
Күн бұрын
Atupele mwai alinaooo Kma santha kuyendera wanthu akumidzi komwe anthu ama vota OK Pali maderawena atupele sanamuonepo.akuyenerakudziwonetsera yenkha ndi kumasuka machezedwee bambo bakili muluzi amadziwa kucheza ndi wina aliyense ndichifukwa pano mulalo alinaooo please hon AA muluzi dzimasukirani anthu anu mwai ulipooo 90%
@BakaliPhili-es3xj
7 сағат бұрын
Ndipo ndakunvanananu brother
@user-oc9vl9xz8e
2 сағат бұрын
Dr Bakili Muluzi adanenatu izi kuti musazavotele MCP koma amalawi ukhutu kumve kufuna kuona za nuwani ndiye tikuziwonaditu
@watchingu-bf2hb
4 сағат бұрын
To defeat this arrogant leadership so called MCP make alliance between Dpp,Udf and Afford
@user-ft5gp2bo3d
Күн бұрын
Inatha ngati makatani
@DavidJames-uv1jr
Күн бұрын
Chaka cha mawa kwatalika
@user-pw4dv1el3d
Күн бұрын
They know what they are doing.
@user-cp4qt9hs8w
19 сағат бұрын
Mcp isadzayimeso pachisankho coz 5yrs yakwana bs aononga kale
@Tabithamulundila1
Күн бұрын
Fire 🔥
@TawongaGSMwale-cc2vm
22 сағат бұрын
Chipani ichi ndichabwino kwambiri Koma mwina wa chipani ichi ali ngat Ras David Chikomen safuna kuzungulira / kupangisa msokhano Muma boma ose aku Malawi Maka chaku Mpoto
Пікірлер: 31