Paulo ndi Sila anamangidwatu. Iweyo nd ndani kut umupange declare kut iyeyo ndi olakwa pamene pamaso pa malamulo he is a free man. What if analapa ngat analakwadi? Komanso munthutu amawoneka kudzera muzochita nzake if anakulakwira chitchure chabwino iweyo chomwe anakulakwiracho. Kundale munthuyu samandisangalatsa not coz ndimadana naye koma chisankho basi, koma mmuzochitika zake amawonetsa kuti anali munthu wabwino. Nzanga winawakenso anazandiuza kuti "ngati uli mwamuna ukamati sudzagonako ku police uzinamiza, and ngat sunagoneko uziyamika Mulungu". Ulingarire mawu amenewo. It's better to celebrate someone's life kuwona ubwino wake ndichikhulupiriro zinazo tikawona kumwamba komweko.
@madalitso1000
18 күн бұрын
Who told you kuti amaba?Who proved kuti anabapo?No one is guilty until proven,mind your words.
@SandraIssa-lo8il
18 күн бұрын
My friend you are so stupid, anaba kunyumba kwako? Wopusa iwe eti...zochita kumupangira pa upon zo????
@user-jn9tz3li3v
18 күн бұрын
@@madalitso1000Who should prove? Any reference from the bible kuti Mulungu azadalira someone to prove that one is not a sinner. Zinazi do not be emotional.
@madalitso1000
17 күн бұрын
@@user-jn9tz3li3v Ofcoz God is the owner of judgement,but I remember even Tabitha atamwalira people was mourning kumanena zabwino zomwe ankachita which proved kuti anali wabwino.Similarly we should not judge,all what we should see is the good.😊
Пікірлер: 29