Ngouzo uli PA mavuto akulu 😅😅😅 mpaka masamu ukuletsedwa kuthandiza 😅😅
@feranjifeza6802
2 ай бұрын
I love every bit of all the series Best show ever
@mishhillinvestment1672
2 жыл бұрын
Uli bwinotu ngozo muja Akuthamagitsira muja ndimaona ngati. Uvuta pa ndalamayo.koma we are loving it
@Liam-ky5cu
2 жыл бұрын
Zopita ku Lilongwe zanthera faw basi😄😄😄😄😄😄😄😄😄😄😄😄
@markmsisya7155
2 жыл бұрын
Hahaha angozo mumaona ngati ikhala nkhani Ya nsapato kushop mupaka kumubweresela heater..... afana kushop ali bho amatha. Enjoying every clip. You have my back.
@ahmednkwanda4246
2 жыл бұрын
Ati mwachenjera Darling 😂😂😂 Black Nina akuitha koma.
@chifundochilambe2266
2 жыл бұрын
4 pin lunch plus 15 pin🤣🤣🤣🤣🤣
@neptunieleo2
2 жыл бұрын
Anthu inuyo eeeee 😂 Nina wadya dolla ndi zinsisi zake😂😂
Koma blackNina nd sister wake😂😂😂🙌🙌🙌 Amachita bwino osamulipila issssiiii
@constancehusband7364
Жыл бұрын
Azimai ndife oseketsa.hahahaha
@tazmeenmdals9904
2 жыл бұрын
Hahahaha ....Angozo ati anthu amabadwa awiri awiri di😂😂😂😂😂 also black Nina wow wabhebhetsa...Asis amangoti ndikupatsa chilichonse...has the game in control....nice content....also don't understand why angozo is being too nice, so extra nkhani yake ndi ya nsapato yomweyi kapena Pali inanso🌚🌚.....Koma big up guys today's episode was perfect and so much fun to watch
@Titan-wb7em
2 жыл бұрын
Nkhan yake ndi yansapatoyomweyo😂😂😂😂
@MindsetChange144
2 жыл бұрын
Was busy watching American couples. Big up guys
@paulsinosi1967
2 жыл бұрын
Akut azimayi amwene andifuna kale Nthawi yomweyi koma ngozo kkkkkk
@tholo86
2 жыл бұрын
when is the next episode guys... kudikila kukumavuta tungobweleza ma episode kkkkk
@madalitsophiri7457
2 жыл бұрын
This Is Classic🔥🔥.... Mmakwanaa I Like Your Videos
@malawivideos4025
2 жыл бұрын
Ine mayi Ngozo amandiwaza heavy 🥳🥳🥳
@tabithachombe1435
2 жыл бұрын
Kkk angozo akufunatu kupepesa Koma poyambila pa kusowa
@Mariam-v8w5g
10 ай бұрын
My favourites
@alinafemakandanje4687
2 жыл бұрын
forever my favorite people hahahaha keep it up you make us happy
@phirimathews234
2 жыл бұрын
Mumanipanga last, from Zambia 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
@dylessmwanguku5958
2 жыл бұрын
Tikuziwa chomwe mukunyengerera😂😂😂😂nkhani ya nsapato tu siitha lero
@susannekamwendomachira17
2 жыл бұрын
Mposo 🤣🤣🤣🤣
@montychisao1262
2 жыл бұрын
Koma amwene😂😂😂 black nina mbali inayi ngozo kwinaku
@christaldjmtegha2503
2 жыл бұрын
Big up Mr ngozo and Mrs. Phiri sangie kkkkkkkkkkk 😄😄😄😄😄😄🤙 we waiting next episode..........
@chifuniroboyce4714
2 жыл бұрын
sangie and pisky 😍
@royaltyfam536
2 жыл бұрын
Z
@giftgrasham4020
2 жыл бұрын
Nice one guys keep it up We're enjoying!
@chiikas1607
2 жыл бұрын
Didn't know you've such a project. I like the shopkeeper.... the bouy is hilarious. How he's negotiating with the shadow guy and his sister makes it even more 💥💥💥 Piksy is familiar to me, Who are the rest?...Watching from Canada🇨🇦
@lovewellmhone2176
2 жыл бұрын
The shopkeeper is black nina, a musician aswell
@grayjames904
2 жыл бұрын
Kkkk koma ndie kuwakhumatisa masten kungowauza kut ulula zomwe amapanga kwa amunawo afewelatu 😄😄😄 umatha khezen
@corneliusphiri5519
2 жыл бұрын
Tiyeni Ku Ntunda konko basi big up🍾🍾🍾
@squatmansaidi561
2 жыл бұрын
Banja kma ili, osati mkazi kungoyankhula pang'ono ndi mbama
@phunzirozilinde8530
2 жыл бұрын
🤣🤣🤣🤣BlackNina wadekhetsa
@thressakampondadothi9887
2 жыл бұрын
Black ninja ayayaya wayitha
@geofreyzuze7479
2 жыл бұрын
Kkkkk azimayi amakunyoza akudziwa kuti akufuna
@joycebanda2029
Жыл бұрын
Angozo being Nice😂😂😂😂
@madanyanda1987
2 жыл бұрын
Akut muzit shop yathu🤣🤣 Koma black nina ase... big up guyz
@geofreyzuze7479
2 жыл бұрын
Koma zabwino zonse... Mumandisangalatsa kwambiri pitilizani kutero ndithu
@justicedzinkambani7112
2 жыл бұрын
Bola isakhale mwatumiza kwa MG2 ndalamayo ngozo, Sangie masiku ano bale wakoyo ndamene amakupanga chipongweyo. Mukapusa mugwira chiphwisi kkkk
@JohnThomas-ji1uy
2 жыл бұрын
Ndi chinsinsi chanji chomwe #Black_Nina akubisa choti mpaka sister wake kudekha chonchii mmene adayakilamo? Kma mumatha guys 🔥🔥
@samuelkalingozi7543
2 жыл бұрын
Makwana ma guy,,🔥 ife tikufuna chi usauver cha 1hour
@BillySaukani
Жыл бұрын
Akumana ndi nyambalo angozo
@zionekupatsa12
2 жыл бұрын
Tufuna chinzukulu Ife angozo muchedwa kkkkkk
@thressakampondadothi9887
2 жыл бұрын
Black nina pena pake, nzanu mpaka pa mute🤣🤣
@da-teachermanda6877
2 жыл бұрын
I love these videos guys
@khumbophiri9006
2 жыл бұрын
You guys makes me hahahaheheheheheheddeeeee but please notify me.
@kingsleymbemba
Жыл бұрын
Kodi osangokwatirana bwanji?
@hussienjcmakawira6738
2 жыл бұрын
I hope project Ya bar sikhalaso bar lolephelekatu ndi Achina Ganizani ake amenewa
@imranahmad1565
2 жыл бұрын
Ganizani sangajambule zinthunzi nthaw alibe😂😂😂😂
@lasnavaya5310
Жыл бұрын
Ndisaimbe nyimbo😂😂😂😂
@idrissaeliassa
2 жыл бұрын
mmakwana koma mudziikako english subtitle nkhani zanu nizokoma
Пікірлер: 230