Koma Bima umatha komatu bwino angakumenye akaziwa ukawapusitsa kwambiri
@lastonchikopa9524
11 ай бұрын
Koma DUmbula mmmmm hiaaa mpaka pa nsana pake kkkkkkkkkk thumbs up
@georgedesiremkamanga2210
11 ай бұрын
Character ya Selina in the play ndi yoopsa and such women amawameneyera nkhondo ndi Mulungu. Amakhala pheeee sikuti amakhala kuti apusa koma kumakhala ija Amati khala chete nkondo ndimenya ndine. The repercussions which follows are always dangerous. Azibambo let's not take advantage of such innocent women one day is one day God will fights for them.
@agnessjuttah7491
11 ай бұрын
Ndipo nde ndi zoona wamva amakumenyela nkhondo ndi Yahwe iwe uli chete
@AlinafePhiripindani-fu5ng
9 ай бұрын
Koma Sellina ndiwe odekha bp ulibe
@TrizahPaul-bh8tu
10 ай бұрын
So nice guys u always make me happy
@groliamazengo5891
11 ай бұрын
Bima you are coming nice bro. Zapamwamba
@aubreyzulu4007
11 ай бұрын
nice guys koma chepesani kugwilisa ntchito mawu ena osakhara bwinowo
@chifunirokachingwe3700
11 ай бұрын
Zoonadi ofunika mau Ena azisefedwa ndithu
@chifunirokachingwe2627
11 ай бұрын
Sellina ndidolo
@LovenessChinyama-xs4ke
10 ай бұрын
Koma Bhima ndiwa bodza iiiih, ndeamanyengerera iiiih 🤣🤣🤣
@sarahmtekama725
11 ай бұрын
This is nice
@HopesonMandanda
Ай бұрын
Mbambande
@Halima-nj2cb
11 ай бұрын
How much
@Twamynice
11 ай бұрын
Za ma blesser zokhazo atsikana simungathane nawo, Chilembwe wabvuta😂😂😂
Пікірлер: 117