Mwayamba bo. mwayilingalira bo kujambulira kumudzi.Koma Selina ndi mlong wakoyo mmmmm Madala a Tadala akuwonesan zinthu this season kkkkkkkk
@OlivettaKadzitche
5 ай бұрын
❤❤
@HalimaMadalitso
6 ай бұрын
😂😂😂 eee km ma bwala bho guys kkkkk
@OwenPiasi
4 ай бұрын
😅😅😅😅 km b man😅😅
@LEICESTERKUMITAWA-zu1iq
5 ай бұрын
Very nice concept,,
@EricCanada-ig9xe
5 ай бұрын
Hanareen zamimba zikutibwanji
@MadaChibwe
5 ай бұрын
Welcome back ❤
@MemoryPhiri-xe7tx
6 ай бұрын
A Tadala ati mugona mutachi momwemo 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂mwabwera mwankonkomo
@GremuMoto-zv7ps
6 ай бұрын
Apa nde mwabwera tsopano ❤❤❤
@SwaleyMaulidi
5 ай бұрын
Okana mimba samwetulira mr Weston
@FelistarTherere
5 ай бұрын
Kod zinthuzi mukuziendetsa bwanj, pomwe inathera paja ndi izi zikufanana,😂😂😂😂😂 mimba ya Hannah ikuenera kukhala ya Bhima
@loycemwanza6638
6 ай бұрын
Welcome back za ma love
@meganabigail-ye7fw
6 ай бұрын
Sinalandile notification yandiphonya life amayo ine😊
@marryrobert7092
6 ай бұрын
Welcome back za ma love ❤ 😍 💖
@etomansailes4932
6 ай бұрын
Mwayamba ndi Moto Moto guys
@owenchitsonga1113
6 ай бұрын
Mwatikumbusa chikaletu , Thivi za nkhongo zikadalipo ?? Kkkkkkkkkk!
@wilisonbornface4282
6 ай бұрын
Makwana zamalove
@jackbello2170
6 ай бұрын
Iyi tayamba mwachipwilikititu zokhala bwa
@FullNdles
6 ай бұрын
Welcome back
@StanielKalumba
6 ай бұрын
Kkkkkkkk zili bwino guys
@simeonkhamwaha8529
5 ай бұрын
Apa ndiye mwabwera eee tinakusowani Weston asakane mimba ndiyake 😂😂 season 2 yabwera ndi moto
@TelezaManase
6 ай бұрын
Ndayikonda ndiphuzita zambiri 😂😂😂😂
@BrendaChimgonda
5 ай бұрын
Iyiyitu nde ndi ina not season 2,, since u changed everything.. ili boh heavy koma
@Chikhulupiliro-b3d
6 ай бұрын
Sound ngat ma Nigerians😂💔
@AishaMkhukumila
6 ай бұрын
Welcome back guys ❤
@sammytokpek8513
6 ай бұрын
Kkkkkkkkkk bhima ati azimay ogulisa mowa amamufuna
@patrickhezronkauye4728
5 ай бұрын
Eti ophunizra uja tipite naye kumunda . Akatiuze za agriculture 😅😅
@ChantyChirwa
6 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂et azigona mu touch yemweyo
@backiewanja7963
5 ай бұрын
Komatu bhima ndi number 1
@fredgabrielnyangulu
6 ай бұрын
Koma kunena zowona zama Love Season 1 ija inali bwino kwambiri kuposa izi kaya mwina chifukwa ndikuyamba
@FaizahKwelepeta
5 ай бұрын
Inuyo nde mwabwela guys mumatha
@GraceCharlie-b6h
6 ай бұрын
Tadala ati waponda tebulo😂😂😂
@MacnightGeorge
5 ай бұрын
Thanks
@CeciliaUmali-vp8cb
6 ай бұрын
Mwatibalalisatu thought season 1 ija ikupitilila
@HamzarHanniff-f7j
6 ай бұрын
bhima wayamba kale kukumana ndi zilango kkkkkk
@chimwemwemartin
5 ай бұрын
Iyi muipatse title ina ikhale season 1 coz mwatigwetsa Mphwayi sakunamizeni
@RahimRichard-fi8ex
5 ай бұрын
Yoyamba ija mukanaipitiliza please ❤
@meganabigail-ye7fw
6 ай бұрын
Machine nafika ameneyo nde kaenga😊
@handsomenkonde2552
5 ай бұрын
Kaye move a westowo kkkkk
@suprianomgalla5512
5 ай бұрын
A bhima akuti kumowa amawaphikira Nyemba azimayi
@andrewBwanaisa
5 ай бұрын
Bima anakoza
@blessingsmajor6296
4 ай бұрын
this is completely new series not season 2 even the characters have changed their roles
@GeoffreyDan-p3d
6 ай бұрын
Zayamba bwino 😂😂
@EstherZintambira-sq3yy
6 ай бұрын
Yajambulidwa kumudzi kodi eti ulendo uno
@CatherineMatope
6 ай бұрын
Well come back guys
@HalimaMadalitso
6 ай бұрын
😂😂😂😂 hannah umatha iweooo 😂😂😂
@chisomongwilinji7219
6 ай бұрын
Koma Jerry 😂😂😂😂😂😂😂😂
@chikondimphamba7102
6 ай бұрын
Komatu mwaitembenuza kwmbr mpka zafika poti Mr bhima afika pomamwela mowa ndalama za khasu??
@BridgetGunde-w9c
5 ай бұрын
Likubwera bho guyz😅
@Junior-zf4ri
6 ай бұрын
Welcome ❤
@ericdonmafuta4676
6 ай бұрын
I wish this was a continuation of the previous season. Iyiyi nde yayamba modalarika kwambiri. The storyline so complicated and yosadziwika komwe zachoka. Hannas boyfriend sali serious. Akumaseka zinthu zosayenera kuseka. Seems like in season one you outmatched yourself and apa mukukanika reaching the level you set.
@VictoriaNyirenda
5 ай бұрын
True ineso zandi balalitsa bolanikoni season 1 ija akanayiyambako pang'ono than kungofikila apopo,,, anyway tiwone momwe dzikhalire kusogoloku😂
@BridgetGunde-w9c
5 ай бұрын
Jerry more🔥😂
@ElifalaBanda
5 ай бұрын
Tadala 😂😂😂
@giftadam2301
6 ай бұрын
Km bhima adha eeeeee khn zina😂
@DebraChimbaka
4 ай бұрын
Movie nde ndi Ina tu si yomwe ija
@NellieMoyo-qr3fl
6 ай бұрын
Tadala mpaka dress eh eh 😅😅😅😅😅
@OswaldSoko
5 ай бұрын
Scene number three, the wife should avoid looking at the camera, akudoja kwambiri and doesn't look good
@godfreymopiwa-yj5zv
6 ай бұрын
akuti atenga shuga abambowo? tadala haha
@gradsonmayira9336
6 ай бұрын
Tadala eeeeeee wayambapo yake ija 😂😂😂
@SamarthaSandra-y7s
6 ай бұрын
More fire
@EstherZintambira-sq3yy
6 ай бұрын
Atadala musawazunze abale anu bwanji kodi mukuyelekedwa kk
Пікірлер: 150