Uyuyu ndi wabodza weniweni ine ndili kuno ku Mzuzu abale kunali mvula inayamba Sunday koma inagwa kwambiri tsiku la Monday komanso onse akuti ndege ku LL inanyamuka 9:17 am Ife tikulira nanu limodzi sogolo lowala lathu lapita koma mmm ma boza satithandiza kuno kunali chifunga
@ChikondiGlibert
3 ай бұрын
Iwe ndiye chitsilu chothelatu udziwe. Komwe uliko
@JimmyIsaac-xd4ef
3 ай бұрын
Zikomo m'bale chilungamo chidziwike, komaso a Mbuye akhale mbaliyanu
@harrispheleni2205
3 ай бұрын
Iwe ndi kape video ya momwe inanyakukira mpaka kugwa? Anakanika president Raisi kapusitse ana a utm azako
@sammyjonnes
4 күн бұрын
ETI NDI ZOONA NSILIKALIYU ANAPEDWA ???
@YobuSatinphiri
3 ай бұрын
WHY ANACHOSA BLACK BOX?
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
3 ай бұрын
Apa sipakuyenera kuwopa chifukwa zikatero mawa zizachitikira kwayena ndiye tizivomeleza zimenez mpaka liti apha anthu asogoro lawo angat pangani zomwezo bwana anthu ali pambuyo panu, tima dikira anthu ngat inu ndipo izi zowawa kwabasi, titeteze dziko osat kuphana tokha tokha ngat ndife anthu ndife obwera zoona
@GarkiThom
Ай бұрын
..nkhan za ndale..IZI
@PriscaChapsa
2 ай бұрын
Iwe ndi opusa iwe ngat umaziwa chilunga umakeka kuulula chilima asanafe bwanji
@JoeMwandira-tq9rs
3 ай бұрын
Mno mu Malawi ngatimli anthu ngati awawa bwedzi dzikolathu likanakhala lachilungamo tsangakuphe mdzanga amalawi ose akuimililani bwana opepela okha ndi amene adzvotera mbuziyi
Anthu for aja ndiAmene anapanga kokupha avice prsdnt
@ShelingtonMtemula
3 ай бұрын
Ulemu wanu munthu wankulu apa ofunika audio muilengeze mu English kuti imveke ziko lonse lapansi
@ernesthkaunda7902
3 ай бұрын
This sounds fake to me. How could the crew members not notice that before starting off from Lilongwe. Tulutsani bodza lanulo .......kodi ngozi yayambira ku Malawi?
Mulungu Ali painu ndi kwa onse omenyera ufulu wa chilungamo
@murraykaliwo6638
3 ай бұрын
Nanga bwanji samauulula zisanachitike
@bostonbanda4774
3 ай бұрын
Zabodza izi unatani kunena zisanachitike
@BenPhillip-fw8hi
3 ай бұрын
Eti eti
@Hellenistic109
3 ай бұрын
Its Bwana Mumandinyasa ndisakubiseni 😂😂 for me
@mariajonasse9792
2 ай бұрын
😂😂😂
@ClementKamtedza
Ай бұрын
God bless you bwana
@JudithAbinaele
2 ай бұрын
U guys u are really taking us for granted..busy making up stories..bring the videos u iditots. Ma phone ama camera amapezeka even kwathu ku Tukombo ..osajambulako bwa? Akwa minyu biiii
@barnettbmphanda108
Ай бұрын
Ndiye kunkhalangoko anachita kuyinyamula kukaponyako ndipo video imeneyo umajambula ndiwe? In your statement mwati ndege sinagwe tafotokozani bwino timve? Iweyo unali kuti?
@TWINKIDDMARSECOAL
3 ай бұрын
Nde mwati mundege kuchotsamo mafuta??? APA mwanamatu and zambri seems bodza coz even galimoto imaonetsa level yamafuta so u mean ma pilot sankaona zamafuta??? Nde analolela kuyendetsa kuti afe???? And video mukuti yochoka ku airport mpaka kumene inagwa munkajambula munadziwa kuti zitere??? Bodza ili
@milanzichikondi7330
3 ай бұрын
Black board??, Benzene (this is just a small component in gasoline) how did they suck it? , Every pilot before flight makes a check list. We need real facts gents. We are with you but we need facts.
@koncyk7138
3 ай бұрын
Olo ngati driver amapanga check ma tyres, engine coolant, engine oil. Galimoto likalila amaonso all warning ⚠️ lights pa dash board and levels of fuel. Should we say gage ya fuel mu ndege inali yokufa. If at all they use a dip stick, sanapange zimenezo? Facts are really supposed to be laid osati trying to trigger unnecessary riots.
Пікірлер: 335