We need people like you in our country. The people guided by love, care, humanity, ❤❤❤❤❤. May Allah bless you sir, and the people who are with you.
@MosesNdebele-kc2cp
20 күн бұрын
Zikomo Inu abungwe la CDED mulungu akuyendereni abwezedi. Anthu akufa ndi njala.awa utsogoleriu angogwelamo let's do it more fire
@wilfredkazembe676
20 күн бұрын
Wow!! I like you guys first kumva amalawi akuyakhula chonchi public tatopadi amalawi tikusekedwa kwambiri tikamakhala mayiko eni wakewa good job guys
@user-pv9uk6sc3w
20 күн бұрын
Yeah! Apa ndiye anyera mapiko a Chakwera, saulukanso. Abweze ndalama za boma basi, asah!
@user-uc1pd1tc2x
20 күн бұрын
😂😂😂😂
@thomluciouss7360
20 күн бұрын
Kkk I like the topic Malawians nowadays they are clever than before keep it up guys job well done
@user-ig5uf9pb3n
19 күн бұрын
Much respect @ cded! Dese people works in iniquity, it's why dem nuh care about citizens Rastafari bless, Selassie I de first🤝
@DONNEXKhama-bk1gy
19 күн бұрын
This is type of people we need in our country
@ahmedmsume1489
20 күн бұрын
The DC must be a member of CDEDI also once is there,is going to be a fire🔥🔥🔥🔥🔥
@homeremedys3748
20 күн бұрын
Chakwera ndiwamisala ngati Habakuku sinyangwe😂 , analonjeza kuti atakanika utsogoleri mu zaka ziwili he will resign pano chikukakamila
@JamesChiphole
20 күн бұрын
Chilungamo abweze sizikutikhudza
@DavidCainoiss
20 күн бұрын
Zilikotu kkkkkk
@PrinceThom-pe6ie
20 күн бұрын
Tili ndi a malawi womwe akuvutika chifukwa cha umphawi ku Malawi ena akugona ndi njala ena akufa ndi njala wina ndikumatenga 90 million akuti kukumbikira galu wachabechabe kamuzu chigawenga chomwe chidapha ndi kuzunza makolo athu.
@AhmadumkomaTambala-lr9gp
20 күн бұрын
Amabungwe tithandizen chisankho chichitike ....may ..Abale osati september
@marryphili5419
20 күн бұрын
More 🔥🔥🔥 we need people like you anthu akuvutika ndi njara ku mwalira kumene pomwe ndarama zikungowonongeka
@MustapherLino
20 күн бұрын
That's great message
@user-is5dl7np9g
20 күн бұрын
Abweze chakwera ndalama zoonad big
@rashidadan2533
20 күн бұрын
Inshort , Tonse alliance has come to finish MALAWl, Corruption is now on every where , Corruption now is like culture & behavior of MCP. If MCP will continue to rules am sorry my fellow malawians , my brother's and sisters
Пікірлер: 252