Usachita sanje musiyen agwire ntchito ya dziko jealous down please
@AchinaKellz
Ай бұрын
Changu changu kaya akalowera pati
@TopoTopo-bm4vw
Ай бұрын
Chofunika kulandila ndalamazo koma osavotela
@kevinchipembere1137
Ай бұрын
😂😂😂ndalamazo atipatse
@AchinaKellz
Ай бұрын
100percent
@user-zv3cy2xj5p
Ай бұрын
Upresident ukukuyenera bwana usi
@user-xb6em7nj3r
Ай бұрын
Yudas Iscaritots cannot be taken seriously. I am waiting for the convention. If this guy will be endorsed that will be my last day as a UTM member and am going back to DPP.
@kevinchipembere1137
Ай бұрын
Then ndiwe wa DPP aise 😂
@jacquelineboya9529
Ай бұрын
Osangopita ku DPP ko lero lomwe bwa
@MustaphaCassim
Ай бұрын
Manganya ndi kapolo wachakwera
@ayaanchaudhry9370
Ай бұрын
This mn will bring change in this world , reason he knows how to deal with poor people , belive me , lets just give him chance
@omarshaffi447
Ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂 Are you sure 😂😂😂😂😂?
@BornwellChipango-s9m
Ай бұрын
U don't think in your mind
@CharlesPhiri-ds1rk
Ай бұрын
Ine munthu uyu ndinkonda kwambiri... osamalankhula ngat kulibe mawa...usi ndi munthu amene amalankhula akudziwa kt kuli mawa....❤❤❤❤❤❤ Powerful vp....more ❤❤❤❤❤❤
@KingfrahMachado
Ай бұрын
Choka apa ndiwe galu 🐕🐕🐕kwabasi tamuoneleni ndevu zake bodza ukunenali Zachison Kupemtaso ndevu ngt malemu Chilima mmm zachison 😂😂😂😂😂
Dr Usi must be aware of what he is doing, ili ndi Dziko. Akapanga masewela awa ndi mathero ake. Ayenela kudzukuta Mmene. Chililima ankamusankhila U VP. Uyu thembelero limupeza Akapanga masewela.
@Chikumbuso-l5m
Ай бұрын
Ndipu ameneyo ngati Akutuluka muchipani cha UTM mlungu amulange
Akut abwana ngt wina anapereka abwana ake inu sazakuperekan???wina akuziona ngt dolo km dkila tsku lako likubwera 😂😂❤
@SifatiMoses
Ай бұрын
Koma Fada katundu wakwiratu kongolero mukunama kwambiri musuzitsa anthu.
@Chikumbuso-l5m
Ай бұрын
Mndiyakhe ndani president wa UTM now
@SaidiMbawa-st6bj
Ай бұрын
Zikutathauzanji zimenezo abale
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
Ай бұрын
Koma amalawi sitizaphunzila munthu uyu mkamwa mwake palibe fundo
@WillyZuze
Ай бұрын
You have too late,usi unali kuti nthawi yonseyi and I have no time to give u my vote Mr chikangawa
@BenadettaThom-n8n
Ай бұрын
Galu iwe tizingokhalira kumva za matako akowo, pereka ndalamayo koma vote yako kulibe
@BestMtawali
Ай бұрын
Et chilima pot wandiuza zonse mowe tingapangile campain then ndimuphe ine ndzapanga zimene wandiuzazo😆😆😆galu kwabas 😂ndevu szinali choncho🤣🤣
@CharlesPhiri-ds1rk
Ай бұрын
Zooona usi. Auzeeee kt mau alionse ankamwa mwawo amene Ali olipa Mulungu adzawerengera mulandu....tsiku Lina adzaweluzidwa.
@TroubleMuthala
Ай бұрын
Zigawenga inu MCP ndichipaninso?
@CatherineDesire
Ай бұрын
Mbuzi yaimuna phongo usi
@CHIMWEMWECHILUNGA
Ай бұрын
Kkkkkkkkk koma ati ali ndi ukadaulo opempha maiko akuja (masikini wamkulu)😂😂😂😂
@WallyMsiska
Ай бұрын
MCP yabisala mwamanganya kt atonthoze anthu akhale bata pa zokwiya za SKC
@user-pn1yo3ll9e
Ай бұрын
Fundo imodzi imodzi kulionse angapite mmmmmmm😢😢😢😢
@user-dl1dg4yz1j
Ай бұрын
Usi ndichitsiru cha MCP. Wapanga chani iweyo gwape? Tikaonana ku convention
@TonyMhone
Ай бұрын
Chadza ndi yani a Usi. SKC wamwalira lero busy. Mmmmmmmmh. Njawala sakunama" mkango ukafa fisi sangalere ana"
@user-le9su3mt7r
Ай бұрын
Yunda sikalioti chikangawa party
@doreenkaliati3166
Ай бұрын
Akubw inu mukugura mavote panyopanu
@EstherNamasala
Ай бұрын
Eya tipaseni ngongoleyo kkk
@kangungufoundation2020
Ай бұрын
Anthu amene akumunena Michael usi alibe nzeru ndichifukwa chake tizivutika nthawi zonse, tili busy kuyankhula za imfa ya chilima kumutenga chilima innocent pamene chilima anali gulu la chakwera remember the birds of same feathers flock together, chilima was not innocent, the president that was innocent and was killed by the citizens of Malawi was bingu wamutharika, alipo mwa inu amene akumukumbuka bingu pa zabwino zonse zimene anachita??? After that inu amalawi munapanga chani bingu wa mtharika?? Lero muli busy kutukwana chakwera amene munamulowesa nokha kumuchosa Peter mwa chipongwe do you think malawians will go unpublished, mzimu omwe wakwiya ndi wa bingu not chilima and if you are not careful chakwera akhala mpaka 2030 just for your punishment chifukwa sindikuwona wanzeru mwa onse omwe akuzitcha omenyera ufulu. Truth is bitter koma ndakuuzani chilungamo sinthani khalidwe amalawi, dziko lathu tikuliwononga tokha chifuwa cha dyera ndi kusaganiza
@AchinaKellz
Ай бұрын
Tachokani apa kodi iwe uyimira pati dikira tione convention ukagwa ngati atakulabade tiona uzasowa mtendere my friend Chima chopanda Zimu woyera sichikoma olo aturo oil kutota njeeee
@PreciousBanda-mq3kf
Ай бұрын
Tambwali weni weni manganya
@Nefitalamoises
Ай бұрын
Pitizani masewero osati vp simukukwana
@Jessica-pg6ep
Ай бұрын
Uku mwangogwelako koma siphatso yanu, inu koma ma drama mumatha. Munalemela kale koma kusakhutisidwa. Zinazi umangoona wadziputa😮
@evancenasoro922
Ай бұрын
Malawian are malawian indeed😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@YusufChipojola
Ай бұрын
Manganya mwanama zaka 4 ambuyanuwo apangachani
@fatsosmart4295
Ай бұрын
A president akowo ngongole yo nthawi yonseyi saamapeleka bwanj? Nde mwakambilana lelo fukwa iweyo wabwela pampandopo? Is tht what u want to tell us? Hmmmmmm ayi ndthu may SKC’s soul keep resting in peace😢
@CatherineDesire
Ай бұрын
Mugendeni ndi miyala
@innocentpalapasa5059
Ай бұрын
Anamizana ndi chakwera wakeyo,Need siyochiitira Campaign
@RodgersMhango-ff2nu
Ай бұрын
Zikakhala ndalamazo tilandila nawoo koma Micheal usi ndi Chakwela mukagwere tsitikumvotelani malawi wake sii waleroyi ayi, wagwa nayo iwe galu wamuthu iwe
@user-pv2xx3lu8b
Ай бұрын
Aaah koma umphawi sizithu mmmm 😢
@JaneMoyo-ws2di
Ай бұрын
Mu misonkhanoyi ndikuona kuti anthu angopemyesesa chetee okuwa ndi ochepa zeedi. Cheteyu kaya anthuwa akuganiza chani?
@AchinaKellz
Ай бұрын
Watha ameneyo mphamvu zake zatha pamene skc adalowa manda,chilegwalegwa kapeta ngongole last minute,njara chani? Mfiti chedza ndizitsiru zizako koma for ma y nod z not bc,udampeleka dzako iwe woyipa kobasi ine nditenga nawo koma vote yanga nyooo
KOMA USI PAMATAKO PAKO WAVA ,KODI ANTHU ALI APA NDI A UTM UKUFUNA UTANI NAO KOD ,PALIBEPO WA MCP APA AI KODI USI ULI KU UTM MWINA KU MCP UFATU IWEYO NDI NDALE ZAKO ZOPUSAZO
@RemitterFlik1130
Ай бұрын
anakakhala wa UTM original bwezi pamenepo Pali kaliyati achina njawala koma apo Ali ndi chakwela awiri
Ngongole mpakana liti chitsiru iwe usatinyatsepo eti tibwezera nchani ngongolezo ngat tili ndi business yolongosoka galu iwe
@EthelKubalasa
Ай бұрын
uyu ndimpera kuwiri. Tisamale naye amalawi satigulitsa ku MCP.
@CatherineDesire
Ай бұрын
Usi nda chakwera ndapao midzu yakachere akumana pasi Asaaah mbuzi eti umphawi ndi njala ya mmalawi mwauona lero?👹👿😈👽💀
@LawrenceBelson
Ай бұрын
Hmmmm usamachule dzina la mulungu pachabe ndiwe yudasidi a2 sakukunamizira
@ClementMinyanga
Ай бұрын
Uphawi kachitsiludi et🤣🤣🤣
@SamuelMthengo
Ай бұрын
Kodi mwayamba kugwila ntchito ku neef?
@vincentsitolo1224
Ай бұрын
Aaaaaa koma ndale eeee dziko ili ngongole ndikupempha kwa azungu basi.
@osmanwanja3733
Ай бұрын
Malawian don't trust this man he is not capable of changing Malawi their is no readership in him
@chrisboyce2
Ай бұрын
Ine kuno ku Ntcheu ndinalandira kale 1M yangongole koma sindibweza chifukwa ndadya Misonkho yanga iyaaa!! ndipo ndapangitsa kale passport Next month ulendo wa ku Capetown Ukandipezera kuti Manganya
@wisdom20mkango49
Ай бұрын
Kavutikeni adhara ....kukhale kunyadira kumeneko south to.....pitani UK or tipezeni Ku USA kuno 😂😂😂😂😂😂 anthu koma ...you are pathetic my guy better ukanayamba business ndikubweza you could get opportunity yoti uzatenge ndalama yambili
@BptomanPhiri
Ай бұрын
A usi si wandale koma akutsiluza nthawi ya chilima mudzamuona akupita ku tikufelanji uyu
@LinesiKanzota-fw7sj
Ай бұрын
Ndipo anthu Ife tichejere ndithu asatinamize thawi yotha yithayi NDI ngongole Kuti tazavoter ayi ndarama Zo tilandire Koma osayiwala m,fiti NDI m,fiti sangasithe kukhala wabwino
Пікірлер: 242