Kkkk mzimu.wa a chilima wayamba kuwaopsyeza a chakwerawo ..ndipo chilima awabwezera ..aphedwa chakwera ndi mzimu wa a chilima..kuyenda yendako.akusowa mtendere.
@MaggieBanda-ft5tu
2 ай бұрын
Ndipo the way I feel pain pano,mmene akuwanamidzila anthu pano,kumawombela manja ndithu hhhiii Malawi amayiwala,vuto ndife okomedwa
@NifuDagas
2 ай бұрын
Mumatiyimilila Mulungu azikudalisani❤
@AsiyatuAkila
2 ай бұрын
I love you DC tikuyenela kt tisambe abale
@HalimaShafie-o7g
2 ай бұрын
❤❤❤❤ mr bon kalindo
@0wenNkhambule
2 ай бұрын
The Dc bon kalindo good Messnge ❤
@AdiniKhama
2 ай бұрын
We're together born kalindo don't give up
@xinalungu9616
2 ай бұрын
Opengawa sitingachite kuwasate ayi. Munthu okhala ndi nsapato ina yoyela ina yakuda ndi wa madrama basi
Koma mwini page iwe kuyika mau it that form bwa j?
@DjshukulanGift
2 ай бұрын
Osagulisa mwadzi wachilima
@KondwanipascalMalembo
2 ай бұрын
Be straight to the point nginiyi bwana imafunika data
@KondwaniNguleti-x1q
2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 Ine kudabwa ndinali kumsika ku Blantyre ndimagulitsa boiled eggs ndinangomva Manganya ati iwe! Ulembane ndi a Mazira anzako ndikupatseni ndalama ine kudabwatu ndati eee izi zayambanso liti kkkkkk
@OnenessLestas
2 ай бұрын
Sanje yakuvutani
@ChizymanJason
2 ай бұрын
Tiye nazo Kalindo 😂
@Jerry-vm6mo
2 ай бұрын
Malawi nde mwapenga Kodi president amayenda daily watch out
@TrizaGeorge-q8w
2 ай бұрын
Ndipo mulungu atichitile chifundo dziko la Malawi ndipo MCP yatikhazika ngati dzikoli su lathu ngati tachita kubwela. Ambuye atithandize
@yohanenene
2 ай бұрын
DC ati ndine wa nyape😂😂😂😂
@MebleNgulinga-hi6rg
2 ай бұрын
Kkkkkkkkkk Kkkkkkkkkk Kuchikangawa kwavuta
@PatrickLikole
2 ай бұрын
The DC 🔥🔥🔥🔥🔥✈️✈️✈️
@DymondMasala-fo4vm
2 ай бұрын
Umakwana
@CarolineSululu
2 ай бұрын
Kkkkk the DC 😂😂😂
@clivemhango6183
2 ай бұрын
Ziyenda ndiweyo kalindo?
@masterkachingwe7448
2 ай бұрын
Kuswa kuswa sankiyu DC
@LysonMkomadzinja
2 ай бұрын
DC mbambande
@VictoriaKumwenda-k6o
2 ай бұрын
Boza ndiye likupwetekani
@SafariBvumbwe
2 ай бұрын
Mmmmmm inuso kod tiziti iweyo sukuwona
@NerieMkandawire-y3x
2 ай бұрын
Tarira kwanthawi yayitari zooona
@MauriceTayali
2 ай бұрын
The DC number one
@KenChitete-pg3ws
2 ай бұрын
Koma Peter Mutharika akakwela pa mpando,,asiye sakho akonde Malawian,, chifukwa akadzapanga ngati za chakwela tidzakutchotsa
@WalesAkazianyenga
2 ай бұрын
Kkkkk asiya bwanji ngati dziko amalamula ndiye Mmesa tinkalamulidwa ndi Chisale the bodyguard
@HalimaShafie-o7g
2 ай бұрын
Chakwera machende anu
@VictoriaKumwenda-k6o
2 ай бұрын
Kalindo upenga ndiwe ndi chamba chako komaso nsanje
@AgnessMatchado
2 ай бұрын
Upenga ndiwe ndi chakwera wakoyo
@AngozoMalunga
2 ай бұрын
Mbambande the dc
@actuarialscience2283
2 ай бұрын
Malawi Chikangawa Party=MCP=Ufiti
@MassahSym
2 ай бұрын
The D C !!!!!!!!!😂
@GiftrichardRichard-re1co
2 ай бұрын
😂😂😂
@ChomboNgosi
2 ай бұрын
❤❤❤❤😂😂
@VictorKachulu-y3n
2 ай бұрын
Ufune usafune ndi president wako ndi wangaso or APM president wake ndi chakwera basi nsanje ikupwetekani mufa ndi mtima ndipo sadzawina APM mudzaphulika abwerera ku America 😅😅😅😅
@@HannahNtenda if you don't know how to comment be silent mbuli iwe ndi opposition yanuyo
@FanizoKawindula
2 ай бұрын
Choka mbuzi ya munthu iwe
@chilingachilinga6059
2 ай бұрын
Km awa iyayi zikomo
@preciousNtonya
2 ай бұрын
Mizimu yakwiya mutu sukugwira
@SifatiMoses
2 ай бұрын
Siziru za anthu boma lonse langozaza ndi mbava, palibe olo ndi modzi yemwe angavotere MCP, ndalamazo adyereni koma osakavotera 🐔 🐔🐔
@LinosLangishon
2 ай бұрын
Kkkk the DC
@GiboTakondwa
2 ай бұрын
iiiiii olo ine ndinali odabwa anthu mpaka kukanganilana ndalama chonchija pa ground ine ndinkaona Ngati payambikanso masewelo ampila Koma eti anthu kunali kukanganilana ndalama
Пікірлер: 78