Chifukwa cha chipongwe chomwe a MCP anapangitsa kuti ambiri ife tiyambe ndale chonde kwa m'mene zinthu ziliri apa tiyeni tipange Ndale muno M'malawi.UTM never forgotten.
@wisdom20mkango49
14 күн бұрын
Do it kwanuko ndi abale ako.... leave Chilima to rest in peace guys
@FrankAdonis-zl6qc
14 күн бұрын
Chakwera chiwanda cha munthu
@FrankAdonis-zl6qc
14 күн бұрын
We don't do the politics in such way to dismiss the importance people in order to get power this What chakwera did is stupidity and useless mission
@alexandermeke6994
13 күн бұрын
Chamba 😅😅😅
@alexandermeke6994
13 күн бұрын
@FrankAdoniswatanichakwera-zl6qc
@actuarialscience2283
14 күн бұрын
Kaliati ndimakukonda kwambiri ndi mtima wanga onse.
Matthews Mtumbuka is very intelligent. You have my tevo
@VincentMagriva
14 күн бұрын
I like him too
@ChimwemweKaonga-k5i
11 күн бұрын
✅
@DorisNkwanda
14 күн бұрын
More fire utm
@ciprianopedro3590
6 күн бұрын
Kakkkkkk A LUTA CONTINUA ,imatanthauza Kuti Nkhondo ikupitilira
@S-rr1eu
14 күн бұрын
Sitiopa. , mpaka chakwela afe.
@ShamilKumwembe
14 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂 Koma ndaseka, mpaka afe😂😂😂
@user-ww4ei5fb7d
13 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@adsonphiri6497
12 күн бұрын
😂😂😂 uyu afa ndithu
@user-wl7xn3or6d
14 күн бұрын
Mai kaliyati mupitilize kupephelela mukanafela limodzi ndi Achilima moti Chikangawa zamavetsa kuti ina kuphonyani pati moti ntima umamuwawa b kuti simuna kwelenao ndege ija Mulungu apilize kukutetezana kungona
@VeronicaChirwa-ct4os
14 күн бұрын
Ndipo ndi Mulungu ekha akanakhala ali limodzi. Ndipamene anthu akanalira kwambiri ndipo tsogolo la UTM likanakhala lokayikitsa kwambiri. Because Madam Kaliati she is very strong woman.
@chifundobuledi
14 күн бұрын
Mathews Mtumbuka takulandirani
@EuniseMasuku
14 күн бұрын
Chitukuko NDI chomwecho deile nkhan yake imeneyo ai zikomo siyani nzimu wa chilima uwuse muntendele 😭😭😭😭😭😭
Timapanga ziganizo tili ndi mkwiyo zosakhala bwino
@doreenkaliati3166
13 күн бұрын
Ndipo Chakwera mwatilanga Mulungu akuoneni ndithu mukutililira ife tsiku ndi tsiku yoooooh Chakwera kuiwala zoona kuti pa mpando mulipo anakuikani ndi Chilima 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@aliceLunji
11 күн бұрын
RIP SKC YOUR LEGACY WILL LEAVE LONG BIYENI ANALAKWANJI Analakwachani mwanawamunthu anaanjoka inu!
@MandalaChaona
14 күн бұрын
Chakwera ndi Oyipa ndipo ndizokayikisa Kuti angapange zoyenerera pa kafukufuku wa ngozi ya Ndege chifukwa chomwe chinachitika Ku Chikangawa akuchidziwa
@IshmaelImulan
10 күн бұрын
Ang'alule akuphawa
@JosephBotoman
6 күн бұрын
Ndife Malawi so osagwilitsa ntchito chilankhulo Cha kumozambique
@wisdom20mkango49
14 күн бұрын
Malawians busy crying for someone that didn't even know them😂😂😂😂😂 he was enjoying his life didn't even care for you fam ....you have never even cry like this all this month's kwa abale Anu....stop putting politicians on top of the elephant selfish people 😢
@NelsonGumanyiwa
14 күн бұрын
Charcoal is still smoldering
@CathrineBizza
14 күн бұрын
Dr mathews mtumbuka takulandilani tikuvotelani muyimile
@JeanBanda-zy6wu
14 күн бұрын
Munamuphela njiru Chilima munalakwa koma Ambuye ali nanu ntchito 💔
@witmosgongolo4982
14 күн бұрын
Ndipo mwa nkhaza😢😢😢
@emilynthite6545
14 күн бұрын
Apanga bwanji komisho of inkwayare poti amupha ndiyemweyo chakwerayo mukutuma munthu amene akubelani kuti akakusakireni yemwe akubelani
@user-ww4ei5fb7d
13 күн бұрын
Akupanga dala bcoz president ali ndi mphamvu zambiri. Ndi zija Chilima amkati mphamvu za president mzofunika kuzichepetsa bcoz amazipanga abuse mkumaswa nazo malamulo. Afa ndi chikumbumtima makamaka akazaluza azalira zenizeni kuti adapha anthu ulele
@JeremiahPhiri-y7h
5 күн бұрын
Azingokamba fundo zogwira mtima osati zamaliro achilima mpaka lero aaa
Kandiverere adanena za mumaluwa koma aliyense akudziwa ndi kuwona zomwe MCP members omwe ndi akulu akulu kuyambira president amachita kuyenda tsiku lilironse kuwonongetsa chuma chanthu. Tiyeni tizichotse mu Mbavazi.
Nde mukatelo mupeza mavoti kkkkk mavoti sichipepeso ai
@DONNEXKhama-bk1gy
13 күн бұрын
I feel like ndimuhage Mai kaliyat Iweo ndi 1 chikangawa amva madzi Chaka Chino.
@alexandermeke6994
13 күн бұрын
Ngati ndi choncho iwenso tulutsa lako ndipo uyikemo zakukhosi zako koma udzaweluzidwa nazo
@JasperKaleni-dx6nn
13 күн бұрын
❤❤❤❤my vote
@dysonfysonchifundo2284
14 күн бұрын
Be serious guys, Akhadzikitsa bwanji committee ina yofufudza while apanga zina za chinyengo, mumupatsa bwanji ulamuliro ofufudza za ngozi aaah no man Ngati ndikufufudza mukanapanga dongosolo boma litsasogolele
@BrotherPaul-ln2ld
14 күн бұрын
Constitution ya MW ikutelo
@DavidKanyemba-n2s
11 күн бұрын
Biyeni anafa mopweteka😢
@DJcliffBandakhudzanga
13 күн бұрын
Ipondeni fada mpaka wina apenge misala
@IreenMwachande
14 күн бұрын
Mai kaliati ndimunthu olimba mtima mumawandiwaza kobasi
Yinu funani ano woti achite kafukofuko wosamangolankhula
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
14 күн бұрын
Ili silipoti ayi koma Ili ndi nthano chabe ife tikufuna ripoti osati zabodza anena zija tikufuna ripoti chakwera masa ambuzi
@LucyKulemeka
10 күн бұрын
Mcp paulendo basi
@IyahMohyoh
14 күн бұрын
eya , nanga A Bakili Muluzi bwanji anaitanitsa marasi hundred chakuti kuti ayankhe za Manafaleyo kuti zinakhala bwanji. nkydzakambanso mumadya kanundu imakupatsa mwano koma zimene mumaenderamo mongati chikhalidwe anaiona amawerenga elder salimo one ku msonkhano wa oau ku addis-ababa. etu ndi aitanitse anthu ayankhule , ndiye ndi phanvu wa anthu, ko.anso zipezeke zoti zoyankha zimasonyeza kuti ndi olakwa mulimonse all the rights to tek dem out by anyway or means are just. thats it. traora ananena no more coward, incompetent and ignorant are acceptable. got do deal with the future , no matter what and even the fact that we cant deal with other more physical matters right know.
@witmosgongolo4982
14 күн бұрын
😢😢😢😢 ishii zithu zokhudza kwambir
@BrotherPaul-ln2ld
14 күн бұрын
Why my eyes are shading tears?😢
@rashidadan2533
14 күн бұрын
Commission of enquiry yopanga chakwela ? But are you serious Mr ? You're still trust mr chikangawa ?
@user-ll3qi5im7x
12 күн бұрын
Chakwela uzafa ifa yowawa anthu tikudandaula mulungu akulange chakwela
Пікірлер: 222