APM my vote izi mzochititsa manyazi kukakamiza zinthu
@MjombaMoosa
2 сағат бұрын
Lozani nzanu nyimbo ya bhooo Peter oyeeeee 2025 bomaaaaaa
@MarthaBango
2 сағат бұрын
Akuchita kuoneka kut akuchita manyazi😂😂😂
@aggogokina8992
2 сағат бұрын
Zamanyazi kwambiri
@mariamwandwanga3035
2 сағат бұрын
Manyazi adan .kusowa zochita .za ziiii .adad my vote
@austenbushiri-cx1kh
Сағат бұрын
Apm ❤🎉❤🎉 my vote
@JonesChingaya-yf4gg
2 сағат бұрын
Once upon a time, there was Chilima and Mia, komabe zabwino zonse Dan Luu ife tidakali pambuyo pa APM.
@giftmakuluni
43 минут бұрын
Dpp my votes❤❤🥰😍
@cynthiakamwana6809
2 сағат бұрын
Zuchita kuoneka kuti,nyimboyo yodyera pasi pamtima ukudziwa kuti zonse nzabodza munyimboyi. Lozani zunu wooyeeeee. APM my vote❤
@DeenesNurudMeke
31 минут бұрын
Dpp my vote muona 2025 inuyo
@MlaziJames
Сағат бұрын
No vote zisiluinu a mcp
@MuhammadSamson-yz1kl
Сағат бұрын
Aaaa Danlu manyi okhaokha ine Munthu uyu kt wa chiyao ndimakaikira kuchiyao kulibe chitsiru ngati ichi
@hagayichiluwe
2 сағат бұрын
Chakwela my vote
@CheManganda
Сағат бұрын
Mbuzi yamunthu
@BarnetMwanyula
36 минут бұрын
My vote dpp 💯/
@ShalomMtonda
33 минут бұрын
Apm my vote 2025❤❤❤❤❤
@PeterMsukwa-i1n
22 минут бұрын
APM my vote❤️
@kingsleydaud9094
Сағат бұрын
Mzimu wa Chilima ukukwapulani ,,mukuwonekaso mwamanyazi zisiru za anthu
@GeshoMwakitwile
Сағат бұрын
Ambiri akhamukila ku congeresi chifukwa nkhalamba ija ikukakamila pa mpando
@heavisonjames1203
42 минут бұрын
Komabe lozani zanu ija ndi number 1. 😂😂😂😂😂 Sine WA Dpp koma Utm
@WisikiBlack-gj4gu
2 сағат бұрын
Dan Lu idyani ndalama yamisokho ya malawi 🇲🇼 yo ife dpp woyeee
@FebbieNjewa-g3k
2 сағат бұрын
APM my vote
@ElizabethMajiga
2 сағат бұрын
Mesa mumati mwasita kiyimba, munali kwa atelala kosokeke kasuli ka chikangawa ka etiiii !!!! Boni kalondo sananame Ku ti tiwona zithuuuu 😂😂😂😂😂😂😂
@johnjoachim3820
27 минут бұрын
Dan Lu nyimbo zako ndikuchitsa mu 🖥 yanga ndimaona ngat ndi iwe solo koma mmmm paja pamuthu
@YasinSabili-dj9xe
2 сағат бұрын
Apm my vote
@EsnartGirivin
41 минут бұрын
Ndimakumbukila chaka China ndinalandila msalu zachipani chilichomse Ndidzovalatu idzo sikuti akulandilawo kuti ndimavoti anu.mukunama atidye nawo amenewo Voti ili muntima mwawo
@ElizaSoko
2 сағат бұрын
Akuloza iwe Dan lu 😤😤😤😤😤😤😤😤😤😤😤
@WisdomMwale-j9h
Сағат бұрын
Eeeh, Anthu awa ndi Amodzi Asiyeni!
@jamiajafali6619
Сағат бұрын
Chimwendo Allah akakulange iweyo
@MpanjeHardware
2 сағат бұрын
Apm may vote
@MaliGomani-z4k
2 сағат бұрын
Anthu akuoneka kuti sakukondwa 😂😂😂😂😂
@DeenesNurudMeke
27 минут бұрын
Ndipo kwambiri
@WiliWili-y2d
55 минут бұрын
anthu akuopa chikangawa 😂😂😂😂
@mariamwandwanga3035
2 сағат бұрын
Akupha ndi inuyo a mcp😅
@JOSEPHTAPSON
2 сағат бұрын
Kkkkkkkkk ife ndi mcp basi chete chete
@NosiphoMazibuko-e9z
35 минут бұрын
Inu Dan lufani pangani kapeni nick chakwera mwana president chakwera akudya ndalama uko minister ndimwana wake nick chakwera chipani cha family ichi kd nick chakwera bwanji zamabwela kuzapanga kapeni iyeyu basi asigwira ntchito mu office inu muzivutika udindo ndimwana wake wachakwera ine chipani cha mcp ndidatuluka kuyambira pomwe adakhala mwana wake nduna yoyang'anila ku immigration ndidanziwa kuti chipa cha family komatu mwanawake zabwera kukapanga kapeni ya mcp km udindo amapatsa ife mamembera amcp ndikupanga kape yopangila nick chakwera kuti zapatse udindo kachikena amamayi kuvutika kwamalawi ozasindikira kodi tikufuna atuluke mwana wa president achakwera nick chakwera yemwe Ali nduna yoyang'anila ku immigration atandize abambo ake kapeni chifukwa chipani cha mcp ndicha family mawudindo akupanzana pachi family chipani choyipa icho mpaka mwana wa president kukhala nduna km amalawi kumangoyang'anila zotero
@SqueyaHosmane
53 минут бұрын
History is best teacher
@FungulanReuben
Сағат бұрын
APM my vote 😊
@bissankal774
28 минут бұрын
Wachiyao mukutamikatu ku mcp mpaka munthu wankulu 😂😂😂😅
@BlazioKamagwira
59 минут бұрын
kuseliku akuti safuna ndalama koma kufuna kudzasintha zinthu koma ndaseka kkkkkkkkk
@GeorgeChirwa-i8v
36 минут бұрын
Adyeleni ndalamazo koma nyimbo zanu zizingabebe ngat zomwe mumaimba mmbuyomo
@thomasbotha9790
2 сағат бұрын
Mbuzi zekhazeka zili apo chakwera ni kawawa MCP nchipani cha ng'ona
@FunnyKatchenga
28 минут бұрын
Zosakoma anta, angotengana okhaokha kumalandilitsa nsalu,ati cholinga anthu aziti anthu akulowa Ku ng'ona party 😅😅😅😅 shame on you.
@LawrenceDickens-jk3zx
15 минут бұрын
Kamanjekete yomweyo😂😂😂 DPP my vote
@doreenkaliati3166
45 минут бұрын
Nkhondo ya pansi pansi ine Chilima kulibe mwayaluka inu Adani sory 🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@Samson-ve5rs
58 минут бұрын
Apm my vote awa alephera nduna zopanda nzeru
@DeliaKaduya
32 минут бұрын
Mwaiwala muja tinagwetsa ndede ku chikangawa chitsekoso atseka 😢
@NosiphoMazibuko-e9z
45 минут бұрын
Km amwene mcp yata basi inu zowoona okupangilani kapeni akhale Dan lufani km mcp nde basi yata vuto mcp palibe yemwe angakope anthu chifukwa chake akugula woyimba kusowa kwachipani inu amcp okupangilani kapeni yokopha anthu kuchipani Dan lufani
@EstherchavulankhomaNkhoma
11 минут бұрын
Inuyo Pagani zaddwanuzo dzuwa salozelana aliyese amalionakaye musiyeni dan lu
@SherifaG.Mlelemba
Сағат бұрын
Koma ngati nkusaka chakwaza,anthu azungulira mitu...Shaa! Akuti n'chiyani!??? Popeza ndi ndale...Zikazavutanso,tizabweleranso.....🤔🤔🤔
Chakwera ndiye satana, kwake nkupha, kuba ndi kuwononga, sangawine or pang'ono
@ChimwemweMguntha
42 минут бұрын
BOMA ndilomweli kulibe kusintha
@JamesChiphwanya-m4v
2 сағат бұрын
Koma ineyo olo oyimba onse atatha kufa kumalawi koma dan lu sindingamunene kt ndioyimba komaso iweyo Dan lu kuti uziwe zoti ndi ofoila umati achiyawo saluza iwe apa siunaluze bolaso Sena
Chikangawa km kugwesa ndalama azuse kwacha cnanga akugwesa ndie chitukuko chake sakumukonda kumene ndipo okupha ndi chakwera ndi iweyo galu kaye kunyasa khope iwe mapwala iwe okupha chilima mesa munapha chilima munapha sadiki Mia munapha anthu 9 pa ndege ija chamba eti
Пікірлер: 183