May God give you more wisdom Manganya our Vice president, Dont be shaken lots of people are pharisees
@GoodsonSame
2 ай бұрын
Iyi inali apayi ndi Group la odyazake alibe mulandu,,palibe wa utm apa.
@SolokingChimzy-yt7dj
2 ай бұрын
Ndichifukwa chake Yesu Khristu atabwela sanalimbane ndi ufumu wa Dziko la pansi iye anangobwela kuzapulumutsa chotaikacho bas...He k ew kut ufumu wa Dziko la pansi ngwa oipayo
@InnocentMtafya
2 ай бұрын
Utsogoleri wabwino ulimo umu ,, bwana VP, you got it✊✊✊✊✊✌️✌️✌️✌️
@KondananiNjakwa
2 ай бұрын
The guy is so wise. Now I know why even President Chakwera did not hesitate appointing him
@smallAsima
2 ай бұрын
Muzithako kupanga zanu komaso kuvomeleza zinthu zikachitika aliyese azamwalila nde musapake ena imfa ya munthu azamwalila nthawi inakwana bas iyi ndinthawi ya Usi mufune musafune
@Nya-Jeka
2 ай бұрын
Osadabwa kuti all this time he never wore UTM uniform….. all of a sudden wakayipeza. Shupiti zako Manganya
@JosiahKachali
2 ай бұрын
Manganya the best man. Keep the vibe
@MarvinChilombo.flourish
2 ай бұрын
1.kusayankha ma diss it's fearing kut abwera ambiri 2. Ati nthawi yoyankha alibe koma aziganiza ngongole, kodi akuona ngati wafikapo eti. Apanga mpaka liti? 5. Lero ndie anaganiza zovala party cloth? Ndie wu betrayer umenewo
@CharityMhone-uk9ym
2 ай бұрын
Suka kamunthu kakupha aka...kamwana ka chikangawa aka😮😮
@MemoryMbepula
2 ай бұрын
Don't let enermy scatter us. Viva UTM
@GraceZumazuma
2 ай бұрын
Wagwa nayo Usi dziko lakutulukira kale kuti ndiwe wa mcp osokoneza iwe ukuganiza ukawina ku convention
@StarchJonas
2 ай бұрын
Tikuferanji at the best level, za drama zenizeni, nanunso oyimba ng'oma kumavina apa mumavinirapo zichani?
@PreviousStanley
2 ай бұрын
Chifukwa chani chirima anamunkhulupirila manganya nanga ndichifukwa chani manganya sanachosedwe unduna maulendo onse omwe ankhala akusintha maunduna manganya hi was a trusted person to chirima
Eti eti chilima amangonyozedwa lero zatani manganya bzy bzy chonch chadza ndiyani
@MarvellousTech-kz6no
2 ай бұрын
Thank you Mr vice
@tblon7441
2 ай бұрын
VP ndi more fireeee Image moto Boma ilo
@IshumaerWazakile-u5d
2 ай бұрын
ndikufuna chisot ndi maglass ndipitilize kupanga masewelo ndi nyimbo ya winiko umandisewelesa
@kingsleymsampha2260
2 ай бұрын
Dr. Chilima had no intentions to quit the alliance? Chilima spent more time in courts with powerless position.... Malawians, learn to use your heads properly in reaction to everything which enters into your heads. God shouldn't be mentioned everywhere brethren because a day is coming. Stay blessed.
@JemesMalawa
2 ай бұрын
Palibeso zoti tingakambilane nanu athu okupha inu ngati mukulephela kupeleka ma information yangozi ndiye mukuganiza kuti tingakusekeleleni afiti osekelela 😢😢😢😢😢😢
Awa si a utm,awa ndi a group yake ijayi amati odyazake alimbe milandu lija 😅
@RuthBinali-b8c
2 ай бұрын
Za dyera basi olo inu mukuyankha pasi pasi muganiza ngati gwilizano amauthesa mwini wake malemu koma a malawi muzachangamuka liti ndindale akufuna kukakamila gwilizano cholinga simukudziwa shame
So many plane crushes in the world achimwene sizinayambe kumalawi
@LawrenceBelson
2 ай бұрын
Oro utani naweso uzafa waphesa chilima iwe mwachidule ndiwe yudasi iskariot ndipo pa exclusive unanena kut umapita kwa achakwera komaso kwa chilima zomwe zikuonesa kuti ndiwe waphesa chilima
@stalickkafera3454
2 ай бұрын
Wa chisokoneza chipani cha UTM
@Mtalimanja1
2 ай бұрын
Uyu ali ndi fundo zogwira mtima
@chippakaribafox2865
2 ай бұрын
This shortman cant be trusted....
@StevenMsanyama
2 ай бұрын
Wisdom defeats knowledge
@Emmamalunga-fj4ey
2 ай бұрын
Thawi yonseyi bwanji simunkavala uniform ya utm even mwini wakeyo Ali moyo aaahhh we can't trust you bwanj wakakamila ku mcp relo mwayamba kuvala uniform ya utm chifukwa mu kuziwa kuti joka akufelani alimanja aahhh
@PaulvinMhango
2 ай бұрын
Wayaluka pano angobwebweta
@thulanimpphiri6873
2 ай бұрын
Manganya akufuna kuononga chipani cha utm. Anthu amene alipo si a utm wose koma ena ndima khwangwala. Manganya ndi sweet talk. Ndichifukwa chani manganya akukakamira ku mcp pamene chilima anafa ifa yovesa chisoni. Manganya aononga utm ngati pamene nankhumwa anaonongera dpp. Manganya amalawi asakupusiseni akukuyikani mukamwa mwamukango.Akufunako chani ku mcp? Mcp yo ndiyimene yinachedwesa kufufuza ifa ya chilima. Mtsogoleri basi palipose ngongole ngongole pamene pali bungwe limene likuyendesa zangongole koma pule ndi vp busy kuyakhula ngongole munthu opusa zeru ndi amene akusangala ndingongole koma wazeru amazisakira yekha chuma ndipo akachipeza chimakhala changeiro pamaso a Mulungu.Manganya ngati ukufuna khala ku mcp ko ndi ufulu wako koma asiyire azako apange za utm
@TisopeMkozo
2 ай бұрын
Anthu ali apawa palibe wa utm angovala ngati a utm
@GilbatChimwaza
2 ай бұрын
Manganya amatha
@abdu-razaqxhatiyah
2 ай бұрын
I like manganya but I smell something fishy in him
@MorganMwikhala
2 ай бұрын
Azimayi muzatiphetsa
@inessmsiyambiri8517
2 ай бұрын
Mesa umati suyankha nde ya nthikoyo ukuikambiranji aaaaaa iwe galu wakumpha
@ernestphiri2934
2 ай бұрын
Panga chako chipani , achilima anachoka pa vice president ku dpp alimboma ndikupanga Chao chipani
Iwe manganya usagawinitse anthu autm koma ndalama ndi satana udamupha chilima
@mkhulukinyata5198
2 ай бұрын
Michael Usi usaganidze kuti an'thu ife ndiwopusa ayi , We know the all strategy that you are Playing .. Iweyo muntima mo ukudziwa kuti UTM Unatuluka chilima ali moyo , Makaka a UTM Wayamba kuvala pomwe CHILIMA wamwalirapa , Iweyo olo utapanga timapulani takoto " Koma a Malawi tikudziwa kuti Imfa yachilima iweyo unatenga nawo gawo ,Even Chilima atati Mulungu amudzutse lerolini " , Iweyo ndimunthu woyamba yemwe ungakhale m'dani wa CHILIMA . Anthu womwe alipamenepowo " We know very well kuti ndi anthu a chipani chako cha MCP , Koma apa wangowaveka makaka a UTM kuti anthufe tidziti" Ukutsatilidwa ndi anthu a UTM , Iweyo palibepo chomwe ungamatiwuze a Malawi ife ' Then nkuyiwala zachipongwe chomwe munamuchita CHILIMA ku chikangawa kuja , Chilima munamupha imfa yowawa kwambiri . Ndipo iweyo siwukuyeneranso kumakamba chilichonse chokhudza CHILIMA , MUNTHU WOYIPA , WOPANDA CHISONI , WOPANDA MANYAZI
@AnoldKonde-pd4qt
2 ай бұрын
Ngat alliance ilipo a pule abwere poyera kut ati akaime pa ballot paper nd ndan ulendo uno?
@RaphaelSiyeni
2 ай бұрын
Ng'oma sound yake ndi mcp
@frankpreciousmulwa7006
2 ай бұрын
Palibe chanzeru apa
@FrancisSteven-we1dj
2 ай бұрын
Zikuwoneka kuti mungakhale tsogolo umu
@DONNEXKhama-bk1gy
2 ай бұрын
Uyu ndie satana bas
@EthelKubalasa
2 ай бұрын
kkkkk lero tavala makaka achipani koma zilko, drama sizithu. tisapusepo apa ndi ngongole, tiyeni tilembetseni zimenezo ndi ndalama zathu.
@MariamJohn-dg4em
2 ай бұрын
Rip SKC only God knows😢😢😢😢😢
@TorresBandala
2 ай бұрын
Watenga a mcp okha okha apa manganya
@BryanJSimeon
2 ай бұрын
Politics. Its something one will never understand. 😂
@thulanimpphiri6873
2 ай бұрын
Usi sakuwelenga bible. Munthu wazeru satumikira mabwana awiri nthawi yimozi. Ngati utm ukuyifuna tuluka ku mcp ngati sikuifuna utm khala ku mcp ko ukuganiza kuti marry chilima akusangalala nazo chimene ukuchita. Ifa ya chilima ikutipweteka amalawi munthu inde amakhala ndizifika koma kufa kwa chilima ndi azake cabinet yose yinapanga rigsin ndi president yomwe koma potimanyazi mulibe and amalawi tikuseketera zithu zoduka mutu.
Пікірлер: 246