Ayi a Manganya mukuoneka okondwa, chasala nchiweruzo basi pa imfa ya nzanu, continue rest in peace SKC, tizakulira mpaka kale kale Biyeni
@bristonmwenga5286
2 ай бұрын
Mmmmmmm,,,koma Malawi,,,,z
@petroszgambo9949
2 ай бұрын
Manganya is a happy man nowadays, he is exactly where he wanted to be all along. RIP CHILIMA.
@ElizabethKazambwe
2 ай бұрын
Ndiposoo
@stephancommercial580
2 ай бұрын
He is more than happy
@LingaSaidi
2 ай бұрын
He is just a puppet wa apule uyu😅😅 kd anthu simukuona what's going on... 😅😅 8:35
@RahimYusufu-u2b
2 ай бұрын
He got opportunity he was looking for 😢😢
@vukanifracksonchinkonde7324
2 ай бұрын
You guys are unrealistic,you expect him to always morn....remember you can not keep crying for a workmate as if it's your mam and Dad. Why shouldn't he be VP ?
@Andrewmwamadi
2 ай бұрын
Balaka ppo mwachìta bwino osapitako keep it up
@DeenesNurudMeke
2 ай бұрын
MBAMBANDE
@EdwardZuze-r7w
2 ай бұрын
Watching from Johannesburg
@BeatriceProfessor
2 ай бұрын
Koma guys sindikufuna kuseka ati monica imeneyi wig yanji 😂😂😂😂😂😂😂😂😂ndakomoka ❤Dr chikangawa woyeee and mr short chakwera ndi manganya mukuvala mochititse manyazi bwanji Kwachema ndi ku Balaka no people 🙌🙌🙌
❤ Maiko usi a chakwela pano a kuyendela nzeru za Maiko usi
@yusufbakali
2 ай бұрын
Akugofuna kumugwilitsa ntchito then asamuphe mcp plan
@ManuelMalunga-mb4hr
2 ай бұрын
Watching from Capetown
@ThokoGomeza
2 ай бұрын
Kuononga ndala kukayendera nyemba basi ndi matumba angat achimanga mukanagura kupasa anthu akusowa chakudya 😢😢😢😢😢
@StevenMjMbama
2 ай бұрын
Good job Mr president and vis wanu limbikitsa ndinthu ulimi umenewuu
@marryphili5419
2 ай бұрын
Keep it up balaka people mupitilize wosapitako achikangawa akamabwera kumeneko
@EdwardZuze-r7w
2 ай бұрын
My district ,keep it up
@CleverJosafat
2 ай бұрын
Ai zikomo anthu aku Baraka ❤❤❤❤❤
@iangondwe6857
2 ай бұрын
leave chakwera and usi God bless them
@SaloDavie
2 ай бұрын
Mamie ndiye mumangolondora kuli konse mulibe zochita zanu ndiyekut eti achakwerawo ndiye ayamba kuondatu chonsecho akudya misokho ya malawi or mutero chaka cha mawa muchoka mudyeretu misokho ya malawiyo paja dzina lina ndi chikangawa 😂😂😂😂😂😂
@chrisschikozera7271
2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂 koma akuliziwa dzinali LA chikagawali
@LingaSaidi
2 ай бұрын
Ndipo pansana pawo ndithu😅😅😅
@prettytambala5687
2 ай бұрын
Kumaka, dad asayende okha angayambe kukodwa ndi ana anjoka😅
@chitanibenito1109
2 ай бұрын
Ka msanje bwa???? Mix ti atsikana tosezenzedwa ma unduna tili ku mcp kkkk kuopa kulandidwa
@cynthiakananji1608
2 ай бұрын
Ulibe manyazi manganya kuchenjera konsekuja kumupha nzanu ngat galu ndi chikangawa nzakoyo,anthu akakuona akumakumvera chison chifukwa mawa ndiwe.utm yake itiyo yomwe uli iweyo,popeza chilima ali Moyo sunasapotepo utm.anthu amagazi mmanja
@anthonynkhoma4265
2 ай бұрын
With or without anthu program yachitika basi. Zomwe amakapanga president ndizothandiza anthu omwewo. Kupanda nzeru eti. Ndale zanji zimenezi. Nsanje paMalawi
@RachelNkhoma-vn2jo
2 ай бұрын
Kkkkkkkkkk koma kuli anthu kapena kuli achina yudasi okhaokha?😂😂😂😂😂😂😂mbali yakuno chikangawa yomweyo msonkhano wa Mr chikangawa.Balaka number one pitilizani mtima umenewu❤❤❤❤❤❤ ndakukondani ndife abanja limodzi zigawengazo mutalikile Nazi zingakupheni zili ndi poison
@MonyaNtchona
2 ай бұрын
A Malawi chenjerani chakwerayo ali ndi asilikali akulwan
@MonyaNtchona
2 ай бұрын
A Malawi chenjerani chakwerayo ali ndi asilikali akulwan
African countries need different type of Democracy designed by Africans them self. The one we follow now has a lot of European influence, control, and interest. It contains ideas whose goals are to control and pin down developing. countries. China has its own type, and Russia has its own. Many European countries have what fit them better. While in Africa, we are controlled by the West. People who shared our continent among themselves in 1884 without involving any African representative. So, let's not blame our leaders so much. But let's fix come up with our own type of Democracy.
@ElizabethMulinde
2 ай бұрын
Manganya or utavala zofafana ndi chilima sungamake 😂😂😂kod apule mwachedwa nazotu nthawi yonseyi munalikut
@joyahmedjoma4615
2 ай бұрын
Ndipo live ife tikufuna chilima basi
@JeanKambala-gm1zr
2 ай бұрын
Ndipo inu galu manganya Kwa basi ufiti basi kulakwa Koma chomumohela munthu ndichani mmmmmmmmm takaoneni kufupika
@prettytambala5687
2 ай бұрын
Koma mpaka kukayendera nyemba like seriously apule?
@YoungMwacho
2 ай бұрын
Kusowa chochita
@chitanibenito1109
2 ай бұрын
Bolanso kukanapita anduna okha mwinako kukanakhala anthu not as it is manyazi bwanji koma!!
@AleksaWilliams-qc6cn
2 ай бұрын
Ku Balakatu anthu anafika kukenani mkona mwapeza kulibeko😂😂😂
@HannahBandah-ks1uh
2 ай бұрын
😂😂😂
@SteveriaNyalugwe
2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@HevenChiwaya
2 ай бұрын
Kodi ku Balaka anthu anapita kuti kukumangowoneka asilikali okha ndi Chakwela zikukhala bwanji
@AleksaWilliams-qc6cn
2 ай бұрын
Anafika kukenani mesa
@ColetteMalunga
2 ай бұрын
Anthu ali busy kupanga zaphindu osati kukaona Chikangawa ngati ndi anawafera 😂
@YamzyNedson
2 ай бұрын
Mr chikangawa ndi VP nde akuyendatu ngat campaign yayambika kale😮
@FWhite-w3l
2 ай бұрын
Aaa uchisilu basi 4 years munali kuti afiti inu Dr chikangawa ndi mr chikangawa
@thomasbotha9790
2 ай бұрын
Mfiti za zikuru zikuru zikufuna kunamiza anthu zakupha anthu opanda chifukwa, akatura pasi udondo sadzawonaso ma vote ameneyu chikangawa
Balaka ndikumene inayambila referendum thawi ya kamuzu balaka siyogonatu ayi
@GanieAlidih-gu7no
2 ай бұрын
Athu kod alikuti zukhala bwanji kumeneko😂😂😂😂
@GospelSoldiers-sr7np
2 ай бұрын
Kaya alikutiko kkkkkk
@CleverJosafat
2 ай бұрын
Inu simukuwona noka akuwopa kuti akawagesa
@jeremiahmalikebu2393
2 ай бұрын
Kodi ndiye mwati ku farm ya Demeter ku amakataniko. This farm has been there b4 iyeyu kulowa m'boma.
@GospelSoldiers-sr7np
2 ай бұрын
Koma guyz kkkkk anthu alikutiko kwangoti ziiii😊😊😊
@RachelNkhoma-vn2jo
2 ай бұрын
Mwamuona pharaoh ndi Yudasi anthu oipa kwambiri bola winayo asasanduke Chulu Cha mchere
@ZaithwaMatchado
2 ай бұрын
Bala wooooye mwachita bwino Mr chikangawa ndi Mr chifunga osapitako
@MaryBanda-n3h
2 ай бұрын
Kkkkkkkk
@ajasikalonga3210
2 ай бұрын
Nosence where were you all these days
@AREFRIEDNELSON
2 ай бұрын
Sazidziwa zawulimi mukungo tha mawu palibe chomwe chikulowa mmakutumo. Koma zomwe akuganiza akachoka kumeneko ndi kukaba mitsonkho ya thu avutika ba mutamuwuza zamitsokho nde nde eeeeeee sngajowejowetu Tsinzina mntole mr Raza 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@muhammadisaid3968
2 ай бұрын
Zachita bwino osapita anthu, chipani chokupha chimenecho, chondee ma boma ena mutengelepo phudzilo osawasekelera akanganya amenewa , I'm White Willison from machinga T/A chamba , Lulindi villege
@MaryBanda-n3h
2 ай бұрын
Anthu aku balaka Mulungu akudalitseni kwambiri ndinu okonda dziko lanu anthu tikuvutika palibe chifukwa chokhalira busy ndi anthu amagazi mmanja
@RhodrickBanda
2 ай бұрын
🤣🤣🤣🤣🤣 koma Malawi penapake zimaoneka ngat ena tidakali muzaka zamma 1980 nanga tikamunene munthu chifukwa choti wavala mofanana ndiwina wake kkkkkkk 🛌🛌🛌🛌🛌🛌🛌
@Lee-lee-w1r
2 ай бұрын
😂😂😂😂😂😂😂
@DaeyangSonon
2 ай бұрын
Balaka! Balaka! Balaka! How many times have I called you?😂
@AlexMlenga-kc5cz
2 ай бұрын
😂😂😂😂 km monica yekha ulusi amayika sangachite kufuna phunzitsi 😂😂😂😂😂😂
@bristonmwenga5286
2 ай бұрын
Ngati sanapite so what?good show a PULE
@magex887
2 ай бұрын
Chikangawa crue
@EviChio
2 ай бұрын
Ndipo ameneyu olo mavoti osadzamupatsa galu ameneyu. Tikuvutika
@zimmekapachika6784
2 ай бұрын
😅😅😅😅😂😂😂😂😂😅😅😅Balaka woyee 😅😅😅😅😅😂😂😂
@Henry-vw2cz
2 ай бұрын
Kkkkk Koma ndiye kwadza zatu anthu 😂😂😂😂😂😂 chikangawa yomweyo
@inessmsiyambiri8517
2 ай бұрын
Munthu paliponse
@AREFRIEDNELSON
2 ай бұрын
Mukufuna kumangoba zitukuko chamuthu chabe osati ndi boma linalima zimenezo mabodza basi 😅😅😅😅😅😅😅😅 koma azitsogoleri Enawa eeeti
@thomasbotha9790
2 ай бұрын
Sikulina anthu azapanga transfer ena Azapita ku Zambia ena ku Tanzania 🇹🇿 chifukwa cha mavuto boma silibwino ndalama zimabedwa kwambiri chithandizo palibe
@IyshaBakali
2 ай бұрын
Kodi Michael usi wavala kut afanane ndi big akunamatu uyu komanso iye kuzavula chipewa. Manganya iwe ndiwa map to see tikuziwa
@JesseKanjanga
2 ай бұрын
Koma SKC udindo wauVP umkamukhala osati zinazi
@YohaneColumbus
2 ай бұрын
Dr. Chikangawa Chifunga mwapeza nyekhwe, balaka siimasekelera zopusa. Rest in peace Dr. Saulos klaus chilima
@PatriciaMbewe-xn7ke
2 ай бұрын
Kubalaka kuno tinali busy kusaka ya thumba lachimanga mpata opita Kwa apulesidenti sitinaupese😂
@MarvellousTech-kz6no
2 ай бұрын
Abale azanga musiyen manganya ,usamunyoze zakutsogolo sizidziwika , adzatero Ali ana anu Ali pa mpando wa up resident
@MeriaMasinga
2 ай бұрын
Mayi chakwera ndakaika ngati akuvanawo
@HaliJana
2 ай бұрын
😂😂😂😂 ZIKUTANTHAUZA KUTI CHAKWERA AKAMUVOTELE NDI ASILIKALI NDI APOLIC AKEO KKKK CHIKANGAWA YOMWEYO
@anthonynkhoma4265
2 ай бұрын
Ku mangochi aja avotera councilor wa mcp ndi asirikali?
@henryphiri6100
2 ай бұрын
Kodi Monica ntchito yake ndiyolondola Chakwera. Iye alibe organization yake yoti akhoza kumagwira ntchito zake ndi azimai komanso atsikana
Пікірлер: 261