Komatu tiyeni tiyakhule chilungamo inde imfa inalakwa chifukwa anachita kuphedwa km chilima anali wamwano and ozikonda mumayakhulidwe ake mphuma linamuphesa uyu koma poti ndi imfa that's why tikumilira kwambiri poti anafa imfa yangozi koma kt anadwala sibwezi tikumulira chocho
@GiftJulius-gx2kb
21 сағат бұрын
Ati kunyada zomwezi
@FelistusTaulo
19 сағат бұрын
Kkk Nanga lero chimanga tikugula zingati?
@BFWCPHIRI1978
13 сағат бұрын
Monica chakwela kumaso kukwinyika ngati chisetero. ,,a chakwela zoona kumupha mnzanu chifukwa cha u president mufika nazo kuti? Msambi.
@FebbieNjewa-g3k
20 сағат бұрын
Zovuta ndithu😭
@MaliGomani-z4k
21 сағат бұрын
Mayi kaliat apangen tag 😂😂
@GumuleKandawala-g7k
8 сағат бұрын
Nthawi mkachitsiru
@FracksonMadani
19 сағат бұрын
Dziko siliramulidwa ndi mfiti kodi? 😂😂adabaya mwana koma mmmmm chosadziwa
@lifayohbenson1994
19 сағат бұрын
Ndikuliratu ine
@EllinaBitto
20 сағат бұрын
Ai zikomo😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@bobykhan3583
16 сағат бұрын
On this fateful day, an individual seemingly embraced their imminent demise by inscribing their name upon the document of mortality. Reflecting upon the poignant passing of the esteemed Sadic Mia, one might discern the wisdom in deriving lessons from such an event. 😢😢😢😢
@MaxonKambazithe
17 сағат бұрын
Iweyo September 2025 watipheraso SADIC MIA ALI KUTI NANGA
@MiddayDeleza
20 сағат бұрын
Nthawi imeneyo mutamuwukira Peter muntharika, achilima mphuno Salota bwezi pano muli president wa DPP
@inessmsiyambiri8517
11 сағат бұрын
Dyera sizinthu mmmmm
@crisspntanie3574
20 сағат бұрын
Chilima Anali katundu eeee
@isaackinod1256
20 сағат бұрын
Anamupusisa
@user-zx3pz2wy1j
21 сағат бұрын
Muziyankhula mokwezako mawu.
@serakillo8668
18 сағат бұрын
Koma iwe ndy unazilodza wenkha ndithu kukupha kuja ndiwenkha unaliika dziko pamoto taona tsopano athu mene akumvutikira tsopano wazilanga wenkha ndthu mulungu kukuseka ndithu chimanga athu akangula ma twety sousandrd ndy lero athu akufa kudya zinkhawo shame on you chilima.
@inessmsiyambiri8517
11 сағат бұрын
Kuzisainila imfa + kuwampha amalawi ndi njala qnthu inuyo mmmmm
@suzanncube7487
21 сағат бұрын
Kkkkk nthawi imeneyo mukuti chimanga chinali 20,000 koma chinali chochuluka aliyense amadya ndi kutaya nsima
@Betty-fe9ql
21 сағат бұрын
Alliance ya Gona mkuphe
@JeanKambala-gm1zr
21 сағат бұрын
Koma kunali zinthu ,,but why achakwela ,,ndi anthu ena mumapanga zakumpha chilima why ,,,,,,,,,,,ndiyetu. History siwola muziona 😂
@MaliGomani-z4k
21 сағат бұрын
Chosaziwa😢😢😢😢😢
@GeoffreyEllias-m9l
20 сағат бұрын
Chilima mphuma anakadekha anakatenga mpando ku DPP mwaize lero sizi kupanga ubale nding'ona zamukadzula2.
Пікірлер: 131