Anthu woopsa ndinu amene mukufalitsa uthenga opanda umboni ndi akupha kumene umbuli basi muchimwa nazo kodi samayenera kufa ameneyo mesa anati tidzafa mukudziwa kuti mudzafa motani inuyo samalani idi amini oposa onse ndinu mukufatsa uthengawu mudzaweruzidwa ndi zolankhula zanu samalani abale kapena mwapeza ganyu akulipilani zingati ndipo ine ndinalakwitsa kuvotera DPP ndawona kuti mtsogoleri wake ndi wodzikonda,osavomereza kuti anachoka pampando ,nanga ameneyi ndi atsogoleri wa msanje mkati 😅😅 anamuchotsa pampando si anthu koma yemwe annamulenga iyoyo munthalika ameneyo ndi yesu basi ndipo economy uvutabe padziko mpaka yesu abwera osati zija zoti ndidzakonza mu zaka ziwili pamene zinatikanika kumbuyoku aaaah aDad khalaani pansi Mulungu akukwezani inu Ngati Mulungu anati term imodzi ndi yomweyo basi ngati malemu a chilima nawonso ndekuti kunalembedwa kuti afzathera pa vice president basi umboni ndi ifa mwayiwonayi so titsogoze yesu osati ndale tiyeni tilile malilo koma lathu likubwera tsiku lina tidzafa ndithu so get ready before we die because Jesus Christ is coming soon get prepared thanks so much 😊😊😊God bless you all ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️🙏
@bisweckchimphamba8497
2 ай бұрын
Palibe cha nzeru mwalembapo apa chi statement chitalikilenji,ana anjoka inu oleledwa ndi ng'ona,
@Okalekale
2 ай бұрын
Koma inu,zochititsanso manyazi,umbuli unachuluka.Democracy inaononga paMalawi.Aliyense akupanga ndale or standard 3 mapeto ndi manyi okha-okha tikuonawa.Zitsiru,zina zikungotukwana chifukwa palibe zimene zimadziwapo eish Malawi wanga
@EmanuelMuotcha
2 ай бұрын
No one can stop kamulepo uyuyu siwamasewela kamulepo ndiakatundu womanga ndimawaya tipita pa seu tithane ndi chakwela tiyeni tonse tiziwe kuti satana wa nkulu ndiye chakwela 😅😅😅😅😅
@DONNEXKhama-bk1gy
2 ай бұрын
😂😂😂😂😂inembo ndina mtambila kkkkkkk I am happy to be Malawian no matter what
Zomwe ukuonesa sizikugwilizana ndi topic yomwe walemba.Zikakhala za malo izo akafunsane ndi yemwe anawagulisayo pano sizikuthandizani angopalapo moto wina
Amayi tapitani kwasing'anga akazapondaso apo azafele popo tatopa naye uyo
@YohanePatrick-lc2lq
2 ай бұрын
Chitukuko chimene amanena ndi chimenechi chomanga anthu chifukwa cholakhula dzona chakwela ndi galu kwambili mbolo yamako
@HaliJana
2 ай бұрын
INU MUSAVUTIKE TAIKANIPO MANKHWALA AFELE POPO BASI NKHANI YATHA NDI GALU WACHABECHABE AMENEYO
@tiwongehojaney5873
2 ай бұрын
Zikhale ndiwakuba😢😢😢😢😢
@WisdomMaseko-fi5sv
2 ай бұрын
Nkhani zopanda mutu mukutithera bundle
@jacksonmaliro
2 ай бұрын
Mukutisokoneza ndi nkhani zanuzi, mwasowa zochita
@marryphili5419
2 ай бұрын
MCP abale anthu enawa amangonamizira Kuti ndi abusa shame on you wubusa wawusatana kumanga anthu wosarakwa
@LukaThawe
2 ай бұрын
Amalawi chimakhala chani kodi uchisilu or bwanji nkhani mungophatimiza basi mapwala nginu mosi panyopino ukongwa. Mosi mutuma nkhani zenizi
@NgomaRaheem
2 ай бұрын
Nthawi ikuza sure azabwezedwa
@danielsaidi7230
2 ай бұрын
Olo mutaika zonyazitsa chakwera maulendo okwana millions koma ife president wathu mpaka kalekale from 2019 to 2060 ndiameneyi. Ife sitidalila zolandila kuno ku Dowa,kasungu, ntchisi, mchinji,Salima, Lilongwe timadalikugwira ntchito ndimanja athu. That's y njala imachepa panopakati. Ife chakwera tilibenaye vuto. Inu amene moyowanu umakhalila zolandila kazilubwani. Nthawi imene mukutaya polemba zinthu zonyoza ena ife timakhala tilibize kugwila ntchito mkumadya pamakomo pathu ,masiku mkumapita. Ifetose amene tikudzuwa kuti ndife achigawo chapakati sitikambanawo zopusazo wathundimtendere.
@EvanceEdson-fz1vn
2 ай бұрын
Ovota si a ku Dowa,mchinji, lIlongwe, ndi kasungu okha-- madera akusala nfi ambri😊
@user-gs7wc3nx3q
2 ай бұрын
Choka iwe chima chine chakuphaanthu
@TrensphoreDzindiwo-k3w
2 ай бұрын
Muledzo amaneyo
@lucksongondwe8266
2 ай бұрын
Ndi fiti imeneyo ikupha oho
@user-xs3pk1vp8i
2 ай бұрын
Zaziii
@takondwajamesdickson7917
2 ай бұрын
Koma ndiye kusakaniza nkhanitu Nanu zosakomanso ai aaaa
@user-ol1hf7ru1v
2 ай бұрын
Eti zosagwilizana
@user-ww9rj2wx8d
2 ай бұрын
Komatu chakwela wandikwana
@SaidiMbawa-st6bj
2 ай бұрын
Mukuphatikiza nkhani
@pepichikako7122
2 ай бұрын
When was Chihana ever a President. You people ndiboza. Peter Chani apa. Pick someone else to be a better President. Now, this is making me question if Peter is the one who got Chilima killed. Time will tell
@edsonnyasulu5394
2 ай бұрын
Mcp koma yilimumadzi kupha chilima
@user-dp7bc7yy6s
2 ай бұрын
Eeeeeee nthawi yakamuzu
@user-zi8pj5ey4t
2 ай бұрын
Anthu amamwalira ndi malo mungowazapo mankhwala pamenepo sachedwa apita
@AlliSaiti
2 ай бұрын
Nanga idi amini anali wa khaza? Kupusa bas
@actuarialscience2283
2 ай бұрын
MCP ndi ufiti
@user-zg9se4rw6v
2 ай бұрын
No mitu
@christophergibson72
2 ай бұрын
Maona ngati basi muzingotukwana basi mulimose Boma ndi chi machine
Propaganda yake ndiye yaumbuliso bwanji,munawelengako za Idi Amin.Mbuli ngati inu ndiamene m'mabweletsa zipolowe m'mayiko.Umbuli umenewu ku ma inu? Kkkkk
Пікірлер: 67