Muyalukatu agalu inu chaka chake ndichino keep it up my comrade
@user-uc1pd1tc2x
14 күн бұрын
❤❤❤❤❤❤❤Mbambande Gra ayalukadi
@paulpaseli6310
15 күн бұрын
Machine bakili muludzi
@user-ne7rn4ki3c
15 күн бұрын
Without Bakili Muluzi TV and the great journalist we are nothing why this is the only TV channel that reveals the hidden story. I❤ the guy coz he exposes the secret of the useless government under Chakwela to let us know. May Allah the almighty protect him as he did with Moses pamene falao amkafuna kumupha.kunkuyu avule dzina la Moses coz Moses amene tikumudziwa ife adali ooa Yehova ndibwino atamatchedwa Yudas ndikupha kwakeko
Iweyo ndi number 1 umatha kafukufuku Bakili Tv mulandire ulemu wanu bro, pitilizani kutisegula maso may God protect everywhere you are
@ulongwearomakawanga2318
15 күн бұрын
Best and reliable TV in malawi
@user-mw8dq4is6k
14 күн бұрын
Our best TV Bakili muluzi Inu ndi big man pazofufuza kulibeso Malawi yonse🔥🔥🔥
@JafaliAkimu-ll1bf
15 күн бұрын
mkulu wa police nkhope ngati chiswa bumbu zigawenga chakwera pantumbo pa make
@user-hm9nc7lz6e
15 күн бұрын
Kkkkkk
@ChrispinTaombe
14 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂
@thomasyohane987
15 күн бұрын
Eeeeh, Kodi mwaziziwa kuti ngakhale kumamiziku anthu asiya kumvera ma radio angomvera Bakili Muluzi Tv ??
@peterchikwakwa8476
15 күн бұрын
I can be true
@user-hm9nc7lz6e
15 күн бұрын
Zoona zake
@actuarialscience2283
15 күн бұрын
Zoona anthu akumaika nkhani zake pa loud speaker. Let's do that midzi yonse ya ku Lilongwe , Ntcheu, etc. Anthu asafe ndi MCPigs.
@user-be5fc3ed1i
15 күн бұрын
Anthu anasiya kalekale kuvera chiwayalesi Cha radio1 ndizinanzi sopano anthu angoveza Bakili muluzi tv bon kalindo ndi Limpopo FM mosogozedwa ndi mtanyiwa 😂😂😂
Bambo, Bambo; haaa!! "Ndaitenga ku Statehouse kumene kumakhala Chakwera". Inu basi ndinu patali. God shield you
@SiphoZungu-tt9iu
14 күн бұрын
Koma amawapeza bwanji ma information amenewa eish bakili muluzi ndi 1
@RichardJere-oz7tu
13 күн бұрын
Pamenepo 😂@@SiphoZungu-tt9iu
@AngellMoyo
12 күн бұрын
Ine to say the fact I don't understand him kkkkk u know uyu akuvesa chimbenene ruling party kkkk
@user-nd9cm3yl7e
14 күн бұрын
Boma la mcp kuyambila kale silipanga chitukuko km kusaka athu tiyeni tipephe mwini moyo atilanditse kuzoopswazi but God is not human body atimenyela khondo yawe bless yours and you me love getting blessed with God amen
@joyahmedjoma4615
15 күн бұрын
Allahu akbar may Allah protect you brother all the time your the best tv ❤❤❤❤
@ApocheC.
14 күн бұрын
😂😂😂😂 🙌
@IbraheemclassickmahmoodIbrahee
15 күн бұрын
Our best brother man mmatiphuzisa mokwanira timakunyadilani
Once a wise man said,, Malawi OSAOPA , OSATOPA, OSAFOOKA📌✊ VIVA MA NYASA, VIVA BAKULI MULUZI TV VIVA✊✊✊✊
@AbuOsman-ts6ef
15 күн бұрын
🎉❤❤Bakili muludzi oyeeee osawopa osa
@JafaliAkimu-ll1bf
15 күн бұрын
kunkuyu adapha witika chakwera adapha chilima boma la zigawenga zokha zokha ili zitsiru mbava
@AiameAdamo-su1nt
15 күн бұрын
Great freedom fighter we salute you!
@KwapataLovemorejun
15 күн бұрын
Watching live from Denmark, bakili muluzi tv l respect you
@shayrafernandeslatif9556
15 күн бұрын
Ndipoo mawu mawuu ine ndimaImvela chisoni ife Malawi,😢tawonane azanthu ku kenya,
@gregorychristian3805
15 күн бұрын
The best ever TV love you king 👑
@Thewarrior7093
15 күн бұрын
Agalu amenewa ayaluka ndithu . Amva kuwawa sanati akhaula . Ife tili pambuyo pa bakili muluzi TV nganganga ur the best
@KunyengaMoyo
15 күн бұрын
Angotipha tonse amalawi atsale okha agalu amenewa
@milajimussa4120
15 күн бұрын
Best tv in Malawi
@GeoffreyDoctor-p5n
15 күн бұрын
Siber security minister! Kuying'alula to the maximum 💃. Tell dem straight 🇱🇾
@Moses51
15 күн бұрын
Best TV in Malawi keep up update 💪💪💪🇲🇼🇲🇼🇲🇼 kalikose tikaziwa social media is best because we know true
@innocentchirombo2073
15 күн бұрын
Ipondeni fadah ❤❤❤
@dalitson3558
15 күн бұрын
Sitingavotele zigawenga za mcp
@user-xd2uz1bh3l
15 күн бұрын
The best tv in the world
@user-Grant260
15 күн бұрын
Much respect elder ❤❤❤
@JonathanMunthali-n3c
14 күн бұрын
Inu ndiamuna recturer, professor akazawina peter azakupaseni reward
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
15 күн бұрын
Ndpo Mai yolamuyo ndi onyasa kwambiri akuoneka ndi chinkhope yakeyo
@mikemakamo7360
15 күн бұрын
Fire 🔥 instudio keep going our comrade atambasule aziwe kuti no secret under the sun
@IbnTaymiahIbrahim
15 күн бұрын
Best tv 🎤🥰💞
@rashidsaid2232
15 күн бұрын
That's why we love our only bakili muluzi channel TV every explation it's their own witnesses no matter how u hate it mr promise president with ur ministers mcp evil government of Malawi
@munashemoyo4190
15 күн бұрын
Mai wapolice kuchita kunyasa nkhope chochi tiyeni nawoni osawasiya ai ayaluke bas tatopa ife
@alickziba6756
15 күн бұрын
Opposition parties, this is the time to invest a lot in security services. Every opposition party has to have heavy security
@Sleemsteri
13 күн бұрын
Chakwera akungoyalukabe uku eeish so sad kkkkk angoni mwayamba kulimbana nawowa muwakwanitsa koma? These are born warriors tu ohoo
This guy is number one,,,and he is not alone 😂😂😂muli finger mkatimu,alipo akumuuza zinsisi from state house, chakwera galu iwe uyaluka,,,pantumbo pako pamozi ndi gulu lako
@EliasApofu
15 күн бұрын
Ulemu wanu wa bakili muluzi tv ❤
@RAJABSTYLESTYLE-yi1el
14 күн бұрын
bakili muluzi tv iweyo ndi number one ndipo iweyo ndi womphuzila kuposa achakwela enafe mwatitsakula maso ndi chilungamo chanu ndipo musasiye ayii ndipo mulungu ayenjezele mzeru zina
@ElonBlack1999
14 күн бұрын
This is why I liked DPP not MCP
@ibrahimalfred6539
14 күн бұрын
You always talk the truth bakili maluzi TV
@user-uc1pd1tc2x
14 күн бұрын
Koma guys tiyeni tigwirizane Bakili Muluzi Tv tiipatse award eeeeeee imatha ndi akatundu zedi❤❤❤❤❤
@Dinalamakanjira
15 күн бұрын
Ulemu wanu big brother
@user-oc9vl9xz8e
15 күн бұрын
Anthu samakhulupilila nkhani ngati izi koma amakhulupilila chinachake chitachitila guys tigwilane manja kuchosa MCP kulibwanji ikazawinanso 2025 azapha mitundu yonse azasale a Chewa okha Mmalawimuno
@JohnRasheed
14 күн бұрын
I remember wht my grandfather used to tell me about mcp zikungofanana nzomwe chakwela akupanga
@user-zr7wk4oq2x
15 күн бұрын
Koma akulu awawa eeeh🙌🤣😂 Akuti ndaitenga konko ku state house 😂 Ulemu wanu captain
@zelliachamboto5744
15 күн бұрын
Hahahaha ndipo ndi moto buuu
@user-du9qs4tb6u
13 күн бұрын
Bakili muluzi your are the one we trust sitiopa sitifooka osachita matha
@johnmiselo2230
15 күн бұрын
They will not kill you And am happy to see that you got that receipt 🧾 from state house where chakwera stays
@IssaBwanali-v6r
15 күн бұрын
Go ahead big brother
@user-eh1mg3ww6d
15 күн бұрын
Mai yolamu mwaipa khope Ndi m tima omwe ite mulungu akuoneni
@Lunnah-b1t
11 күн бұрын
God please keep him safe ,u really love Ur country
@tisuhmakhwah7085
14 күн бұрын
MCP trying to be strong in a democratic nation nzosatheka izi.
@BenissoneErnesto-eh6zs
15 күн бұрын
Inu ndinkhani zina brother watching from Mozambique never give up BG brother tili pano kukusatiran 🎉🎉🎉
@ShadyShariefAlieck
15 күн бұрын
Indeed bro keep it up a good job brother
@JohnstonNyirenda-zw6jd
14 күн бұрын
Kalikose tikamva , our SKC is still with us
@saidichirwa5456
14 күн бұрын
Mkulu iwe mulungu awonjezele masiku amoyo wako ndithu.Ulindiukadaulo osati wamasewela ayi.Malawi yense pano anakukhulupililadi ndithu.Moyo wanga ndadziwa ma history ambiri kuposa kusukulu kamba ka chanel imeneyi❤
@davidcainoiss2762
15 күн бұрын
Viva ..best tv ever connected from London
@isaaczuze
15 күн бұрын
Chakwera ndi munthu woyipa kwambili ndi amalawi sitinayembekezele zimenezi
@yohanekanjana4925
14 күн бұрын
Best of the best journalist, eyes of the country, we know kuti chakwela ndi gulu lake la zigawenga spent sleepless night planning to silence you. But you're in our prayers, God is gonna fight for you.
@user-ul1fb4yn5o
12 күн бұрын
I love bakili muluzi tv timakunyadiran, Comrade
@user-mz4tk1pw3f
15 күн бұрын
Ulemu wanu big ❤❤❤❤ ndimakunyadilani kwambiri
@user-xx5dc5wl7g
14 күн бұрын
If there's a journalist who knows tracking government Pvt things ndiye Bakili TV believe u Will never attack this giy
@user-be5fc3ed1i
15 күн бұрын
That's why l like this chanel chifukwa Akayankhula amationesa umboni kp it up Bakili muluzi tv.mbuzizi zayamba kuyaluka ndipo ziyalukadi sazayiona voti yathu agalu awa tinawabitera kamba ka manifesto achilima za MCP tinazitaya kalekale iya
@LionPhiri
12 күн бұрын
You got my endless respect brother... awululeni ayaluke kumene dziko laMalawi likuyenera kudziwa chilungamo.
@MisheckAselo
15 күн бұрын
😮Boma ili litipweteka ndiana omwe kupanda kusamala tikutha ndi ana omwe 😭😭
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
15 күн бұрын
The best tv but MCP must know A TIME IS SELFISH, MULUNGU AMAKONDA MALAWI, CHAKWERA MUST GO enough is enough
@AbuMussah-wi7gb
15 күн бұрын
The best tv and speech i ❤
@macbestermtonga3015
15 күн бұрын
😂😂😂 Kama jacket
@MUSTAPHERMALIDEN
14 күн бұрын
Koma anyaniwa tikazawachotsa m'boma chaka cha mmawachi dziko likuna likuziwen big man not now because we know anthu akukusakan but next year amalaw tikufuna tizakuziwen akulu 💪
@AlbertDuke-of9nn
15 күн бұрын
inu ndi one big,mzelu Ngati king Solomon
@Penior265
10 күн бұрын
I think this guy is not mad there is something behind guys lets focus
@arafatMtyala-bo8ev
15 күн бұрын
Mumaitha big broh, iloweleni ndi mkabulula momwe anthu amenewa akuwonjeza kosakhala bwino
@martintivalenji320
15 күн бұрын
Thanks for the update best TV ever
@dontreybanda278
14 күн бұрын
More fire big boss, akanganya amenewa alira.
@fyopokappata9738
Күн бұрын
Nthawi ya Peter mumapqnga zomwezi pano ndia Achakwera mukupangaso chimodzi modzi . Mwalowa ndinu ndinuyo big ... Inuyo loaning m'boma tione ngati mungayendetse aaa .
@user-et5vn3yh4j
14 күн бұрын
Inuyo mumanena chilungamo god bless you my brother ❤
@princedetbozsmallboy1749
14 күн бұрын
Chakwera sanakhalepo mbusa ndichigawenga kuyambila pachiyambi pamozi ndi nkazi wake zigawenga koma satitha. Akulu ndinu patali tisaname mukuvesa kukoma ndithu
@user-qq1uj7ct6n
14 күн бұрын
You are No 1 bro.. Chiyembekezo chathu chili mwa inu sir. God keep you safe. Amene amaikira kumbuyo MCP Mmmmm ndi athakat anthuwa sure
@user-cy9zp4fb2m
15 күн бұрын
God shud keep on protecting you our brave journalist
@PrinceThom-pe6ie
14 күн бұрын
May the Lord protect you with the protection from heaven
@EphraimNaveya-hz1du
4 күн бұрын
Timakunyadirani bg for true information,Kodi mbuzi imeneyi chakwerayo ndi mbuzi zinzakezo apha anthu angati,iyenso adziwe kt sazakhala wamuyaya
@HsienSawez-hr5xq
15 күн бұрын
Great bakili
@YONA-v5o
15 күн бұрын
Bwana ndimakunyadilani I wish you all the bey💯❤
@alicegama8138
15 күн бұрын
Kama jacket 😂😂😂😂😂
@user-bw2cv9sd7x
15 күн бұрын
ing'alule fada ayaluke agaluu amenewa ur the one who bring truth to us
Пікірлер: 824