Aliyese ali ndi choice asiyeni anthu azimwa inu vuto lanu ndichani? Zausilu basi agalu inu mumaziwa mankhwala ndiinu nokha basi ? Osanena kuti business ilowa pansi bwanji machende anu nonse
@MisheckAselo
14 күн бұрын
Aaaaa chakwera pa ulimi okhao ndiye mukunama fertilizer saoda ku butchery
Ena Ku MDF, Ndiku MCP Mupemphele Musaluze Zisankho 2025 Imfa Ya chilima Ija Ena Muzamangidwa, Sindikukuopsezani ichi Ndilungamo ndithu
@WisikiBlack-gj4gu
17 күн бұрын
Yaaa zoona arv is powerful
@user-co3wr3rn4h
17 күн бұрын
In fact tose angoni tikanakhala pamoz mzimba ntcheu tiyeni tigwilane manja kumuzimbaso akanazisiya kaye tilimunyengo yolila
@KenChitete-pg3ws
15 күн бұрын
Ndani angavotele atupule,,olo atakhala opambana ku convention mwina Bambo wake ngati akulephela kuwina pawu mp kudela lakwawo adzawina u president????
@EamonChikanda
15 күн бұрын
Kodi a Chakwera adakhalapo nduna or mp asadakhale president? Its better Atupele coz anakhalapo muma unduna ambiri komanso he has had been served in different government parastetals. So he is eligible to serve the sit
@user-dv6rt6vb6e
14 күн бұрын
Mbuli munaivotela ija nde imaziwa chani?anthu kuyesa kukuuza kuti mbuli ziikuziwa chilichotse iyi koma inu kakaka laro ndi izi Malawi wasanduka Zimbabwe
@user-un6qv6sj3h
18 күн бұрын
Kupusa kwa chakwera kumatumiza anthu ku Israel kukalima pamene mukulephera kumawalimitsa kwao shame on you MCP
Imagine to bring those mega farm in our country is better than to go work outside the country that's not good
@Eric-gb9ms
17 күн бұрын
@@kingsleyhopematchaya5184mbuli ndiwe you don't know nothing about economy
@kingsleyhopematchaya5184
17 күн бұрын
@@Eric-gb9ms my brother send 2million this month from Israel ndipo taona kusitha kwa m bale wathu komaso sakakamiza mukhala ngati anakakamiza muthu bwanji
Пікірлер: 18