Munthu alephera umeta , inu mukuganiza kuti angathandize zigawo za boma. Komanso alephera ugula lamba wa mciuno waaake. Basi tili ndi munthu. Amalawi pepani
@FrynessMoyo-to2du
2 күн бұрын
😂😂😂komaso chakwera ndi onyasa series ananyasa dzose
@GoodwellRaphael
2 күн бұрын
Lazarus chikangawa chakwela Full name President of Malawi😂😂
@IsaacMusa-py2jm
2 күн бұрын
Powerful 👊
@chippakaribafox2865
3 күн бұрын
Azimayiwo alire kumene asamapuse kudikula mmisonkha ya mbuzi zimenezi
Пікірлер: 98