Ali Maso rwaa! Ngati Nazikambe kkkkkkk koma Manganya😂😂😂
@JamesChiphwanya-tb3tq
Күн бұрын
Abwana president chakwela Ali ngati chidole kapena kuti katuni ena amagomungwila ntchito zaumunthu uyu mulibemo ndipo ndi khutukumve chakwela wa mwazi uyu
@user-cj2bo4lf7c
2 күн бұрын
Chakwera waononga dziko la Malawi .angongwetsa kwacha mosanganizira anthu osauka
@Aisha-db6ds
2 күн бұрын
Kunkuyu mapwala ake ndithu
@kubengovender6996
Күн бұрын
Keep it up brother man!!
@user-ec4jo9cu4d
2 күн бұрын
😂😂😂😂😂ati kagowero kkk km naseka bwanji
@user-dh1oi8mb4v
21 сағат бұрын
Akunamizana akuti awina ndipo sawina anthu ameneyo ndipo azafa ndi mtima ndithuu my vote for Dpp hoyee
@nationsmpweti8088
Күн бұрын
Abwana bwanji mzakhale president zikuwoneka kut muli ndi nzeru zoti mngasinthire znthu
Onse ndi amagazi mmanja kumkuyu sakudziwa comwe akuyakhula
@MosesPhiri-l6e
2 күн бұрын
Let me correct you in Mzimba sugar ndi k 2495 in big mart shop ya fair price Chakwera dziko lamukanik passport anasiy kupang ndet only in lilongwe zoona zak achinyamat ntcht njee Achoke I will support that
@ORTONPHIRI-i1z
Күн бұрын
Chakwera chomwe wa kwanitsa ndi Mabokosi AMALIRO osati chitukuko Chitsiru cha munthu .
@user-vb1iq5un5p
2 күн бұрын
Koma pa udindo wa upulezidenti uja umafunika kukhala okhwima nzeru.😂😂😂akt amakajambulitsa zithunzi ku china akazawo Ali pompo ..
tafufuzani za ku Burkina Faso kuli president wazeru kwambili mutibweletse mbili yake bg man
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
Күн бұрын
Yes plz
@stainmujiwa3617
Күн бұрын
Kkkk ati kamuyenda njila anadya matako agalu.nde ndi nkazake ngt otupa mutu uja😂
@CatherineDesire
Күн бұрын
Komanso Mzuzu airport Ngati airport ya witchcraft kkkkkk
@AngellachifundoMwale
2 күн бұрын
He has forgotten about the boolet train your just reminding him now poor Malawi that used to be a milky and honey country shame on us 😂😂😂😂
@AubreySymon
Күн бұрын
Ndiana sakuziwa kathu auze mwina aiwala. 😅😅😅
@MercykanchureJohnson
2 күн бұрын
Tikhara kuti tikungotukwana bas pa social media sizitithandiza Ife tingopanga zoti Mulungu atione ndikutivera chisoni basi Tizizivera chisoni kuti Mulungu atikhululukire
@msatisi.reangfordphiri
2 күн бұрын
Kkk koma ndaseka yandibaya yomanga kagowero ku ku airport
@OwenTembo-xq6ug
Күн бұрын
Tell tell my favorite bro Lai malawi ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-xe1so5xj2w
Күн бұрын
Chakwera tatopa nayo bolani afe basi anthufe tatopa naye kwambiri
@thomasbodo4099
Күн бұрын
President uyu ndi pa nja penipeni munthu osadziwa chimene akuchita ndi munthu wanji
Malawi politicians are all poor minded because all of them are just after money after these ones other Gandangazi are coming ooh my beautiful country 😢😢😢
Chakwera zimene wakwanitsa kupha chilima basi palibepo chimene akupanga komaso nanga asikali Aja Amati azapanga ma video ya momwe chilima alikuti anthu Aja chonde asawaphesotu
@DalitsoPhiri-sq5nl
2 күн бұрын
Awuzeni agaluwa apange zoti kumwelako anthu onse akhale okhozekera kukaponya ma vote awo powapasa chaudzika in time cz ngati izi sizitheka obviously mcp izabela ma vote komanso kuchepa kwa anthu ovota kumwelako zizathandizira kuti mcp iwineso ndiye chonde yesesani kuti anthu kumwelako axavote ndithu
@edsonnyasulu5394
Күн бұрын
Kkķkkk koma iwe akuthyola kholingo chakwela ndi satana
@CatherineDesire
Күн бұрын
Akadzi akenso sanatchene Childress cha kumidzicho mpaka China sure bwanji manyazi chimodzi chokhachokha
@kondwamlungu8384
2 күн бұрын
Zikomo Bakili TV Pamozi ndi aulusi ena ndi ena pomatiziwisa
@RhodneyBwa3
2 күн бұрын
Kunkuyu ndi mfiti otheratu
@SymonNamalomba-sh3fu
Күн бұрын
Gautrain from Pretoria to OR Tambo international it takes 1, 30minutes is only 45kilometers
@harrisbanda5891
2 күн бұрын
Ameneyudi ndi kamwendo njira akudya matako agalu 🐕🐕🐕😂😂😂😂, mbwaa ya munthu 😂😂😂😂
@antonymoyo
2 күн бұрын
They will be no one who will fix this Malawi let's just be honest the one who can take over will be worse than this
@MichealDPhiri
23 сағат бұрын
😅😅😅 at bola Vasco da gama 😅😅
@PatrickTchuma
2 күн бұрын
Dziko la Malawi silidzasithaso ngt atsogoleli anthu sadzasintha
@user-is5dl7np9g
2 күн бұрын
Zoonad MCP singawineyi, thanks bro for informing us
@AmandaConstance-fx8cr
2 күн бұрын
Hello sir morning's ❤❤❤ Mwati vasco dagama eti😅😅😅😅😅😅
@user-zr7wk4oq2x
16 сағат бұрын
Bwana kumanena kuti mwamaliza 🙄😫
@josephndalama5494
15 сағат бұрын
Amangokhala chateee😂😂😂😂
@ElonBlack1999
Күн бұрын
Iwe osamaba za bakili muluzi tv
@rashidadan2533
2 күн бұрын
Kumkuyu ndi Mr nonsense
@user-jl6sq3ph1b
Күн бұрын
Mangochi lake city and makanjila road and international Airport Mangochi 5star hotel palibe chimene wakwanilisapo palibepo ngakhaleso analonjeza mafuta onsika ndi fetelazer zambir
@user-nm1jj5qv8i
2 күн бұрын
Welcome bwana for today again Amen ❤
@homeremedys3748
Күн бұрын
Nthawi Yakamuzu Timagula packet ya Sugar k1 , nyama 1kg 20 tambala, thumba lafeteleza lili pa k2 koma boma ili zonse zafika mma sousande, what a shame
@hanifahmponda8711
2 күн бұрын
Aaa uyu chakwela ndi MCP yakeyi wawononga dzinthu kukwela passport ndiyi akupanga katon KWACHA YASALANO CHIDZUDE CHA NDALAMA PANO KUMANGA ANTHU PA DZIFUKA ZAZIIII dzotsedzo ndikuphatso chilima aaaa awa ayende bwino adzazabweletso boma MCP ndi agalu kwabasi
Пікірлер: 330