Aaaaaaaaa koma kalindo ndi munthu wankulu kwambili ndipo amayankhula saopa kanthu
@user-lz5yv4vj6h
17 күн бұрын
Kkkkk koma Born aaaa ndi president wanthudi ,l salute you sir
@josephinemisomali6840
17 күн бұрын
Ndimadikira Dc kuti lero atichani apa nditha kukagona 😂😂😂 Boni kalindooooooooo!!!
@NelsonbastonMandela
17 күн бұрын
Kkkkl mpaka police 200 koma bon kalindo ndimunthu okwiya kwambiri 😂😂😂😂😂
@robertchitsulo8006
17 күн бұрын
Bon kkkkkkkkk akuti aputa milandu yambiri iwe ndi 1 basi kkkkkk
@SamfrayGvng
15 күн бұрын
Eeeee ai ndagonja nanu big up a 🙋DC
@user-mk7fh5ml8s
16 күн бұрын
Mr kalindo ife tidalira inu basi❤❤❤
@user-jk8sh7fh2d
17 күн бұрын
Wakumuzi kwenikwenni za pa social media -zi saziziwa kuti inu muma -aimilira
@user-uc1pd1tc2x
17 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂😂😂😂Nyau kumva pain 😂😂😂
@AufiThera
16 күн бұрын
Kod Aku Germany aja bas angotithera ndalama mosemuja lipot osabwerensa aaaa ndiye angopita kwawo wapas amenewo iyaaa
@TougiedaAjam
16 күн бұрын
It's the Dc keep it
@PeterKathewera
16 күн бұрын
Kodi kwanu sanakuvoteren bwanji😢😢
@AlickMakunganya-o4w
16 күн бұрын
Ichichi sichamasewera Adaaa😂😂
@PetroMatias
17 күн бұрын
🤝🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🤝🤝🤝🤝
@user-hh4wn4vf9e
16 күн бұрын
DC 🥰
@EvsonNgurube
16 күн бұрын
Bon kalindooooooo
@Homeofpeace321
17 күн бұрын
Za Imfa Ya Chilima Tisaopsezane, Ngati Simunamuphe Tiuzeni Kuti Chinachitika Ndichani? Ku MCP musabise zinthu zoti munapanga nokha, Chakwela Ukhale ndimanyazi Ubusa wake Uti Unkapanga iwe Okupha Nzako Chifukwa Chautsogoleli?
@AufiThera
16 күн бұрын
Wanthu wanthu DC 💪
@user-hh4wn4vf9e
16 күн бұрын
DC ❤
@MariamJaffali
17 күн бұрын
Ndodo ija ituluke DC tatopa ndi chakwera ife kkkkkkkkkkk the DC ❤❤❤❤
@sir-wanton-2001
15 күн бұрын
Kkkkk chikumvesa kukoma a Malawi ambili
@user-fz3gu2ez1o
15 күн бұрын
Kkkkkkkk Mwana ovuta kulera Hehehehe
@MisheckAselo
17 күн бұрын
Amafuna kukuipisirani Mr DC koma akunama 💪
@user-uc1pd1tc2x
17 күн бұрын
Bon Kalindo the DC (The most dangerous child)❤❤❤❤❤❤
Пікірлер: 65