BON KALINDO NDIMUNTHU OKONDA AMALAWI NDILIKUNO KU SOUTH AFRICA I LOVE YOU SPEECH MR KEEP LIKE THAT
@MikeSymon-si8dw
14 сағат бұрын
Powerful message.... Eeeish dziko latiipira ili mmmmh... God have mercy 🙏🙏🙏🙏
@ShamimuBisani
Күн бұрын
May good Lord almigty bless u Kalindo umayankhul zoona zokha zokha koma vuto akutilamulirawa ndi asatana sakumva za anthu vuto ndiomwe akuombera manja boma lopsali
@SymonPaul-s8h
14 сағат бұрын
Pitilizan kumenyera nkhondo a malawi 🇲🇼 osauka inu mr DC mulungu apitilize kukudalitsan
@DevelopmentFund
Күн бұрын
Thank you much to remind leadership of Malawi may not sleep wakeup?
@MdalaSamson
Күн бұрын
Boni kalindo ndi muthu olimba ntima ndipo alibeso zake ndipo sazapezekaso muthu ngat uyu okonda ziko lake komaso okonda athu ake
@ruthkundwe7448
Күн бұрын
Ndipo u r saying rite,kudabwa antu kutulusa ntawi yokuta ita,ai zikomo,wish SKC was here
@lucymsiska5903
Күн бұрын
Ndalama zaphwekazo bwenzi ukutiganizirako ifeyo, we are working hard in a wrong county, please unmalawi me😢
Kutero kuti munthu wanzeru zake kumakataya nthawi pa mzere kupsya ndi dzuwa kuvotera Mr Chikangawa? Ayi ndithu wake up Malawi
@LuckiaMatemba
Күн бұрын
God bless you Bon
@GiftNgwira-e8l
Күн бұрын
The DC more fireeee
@haroonali9460
7 сағат бұрын
That's great son of Malawi, big up
@FebbieNjewa-g3k
21 сағат бұрын
DC wathuwathu keep it up
@LoyidKarebe
Күн бұрын
Keep on updating us
@AlickKapapa
Күн бұрын
Namweso inu who DC mbalami yolala siyimakoma inu poti inuti a Malawi mma supporter ngakhele wina anya manyi kuma supporter kuti eeee anyela manyi abwinu palizelu nde born kalindo yo akhala akusuta chamba,kanundu etc of course ngwa DPP koma zelu palibiletu chifukwa mkumuwona akazuka basi uje uje
Kodi DC uyu ngati ndi president wa anthu osauka bwanji amasankha anthu a mcp. Munthu akalakwa amangidwe
@ThomasMlowoka
Күн бұрын
The DC 🎉🎉🎉🎉 Our president 🔥🔥🔥🔥
@AnthonyJimmy-i4c
17 сағат бұрын
A'ba'le
@WilliamNyilongo
Күн бұрын
❤❤❤❤🎉
@nickmumba2131
20 сағат бұрын
❤
@JoaquimNasiyaya
16 сағат бұрын
Apolice ndiwo mangidwa ndi boma
@AlickKapapa
Күн бұрын
Osandandaula mtalalata motani vuto palibe khalani a opposition konko and ndi timavote tanu tochepa boma ndilomweli 2030 woooo chapani sasinthasintha ngati zovala ayi koma president yes inu a opposition we happy to be you as opposition just making noise so that Boma lizigwila nchito bwinu bwinu
Пікірлер: 157