Ulemu wako the DC iweyo sangakumange akuziwa kuti olo ukhale mundende Koma voice yako izamvekabe
@TamUs-u2h
2 сағат бұрын
Kalindo mzeru zamuthera kkkkk guys, Ben Longwe wamupepelesa
@bridgetmajor3646
4 сағат бұрын
Boma .....iliri Ayi ndinthu yatikwana .....the dc inuyo ndi 1😂😂😂
@TameeraInglis
2 сағат бұрын
Mr DC Winiko more faya
@BrianJoe-z7u
2 сағат бұрын
Boooon kalindo DC inuyo inuyo
@MarcyKamaga
4 сағат бұрын
the dc ukunena zowona ukuwonera patari ndipo usazafe uzangosowa koma uyu chikangawa akuti pweteka mtima ukuwawa kwambiri m'mene anaphera skc mzimu wa sauros uwuse mwatendere
@calvinjamal7117
2 сағат бұрын
Bonon Kalindo mwana oopsa kwambili iwe dolo
@TecksonKaima-dr6er
4 сағат бұрын
Koma Mr born mwamva!!!,apuletu ayamba kufa ziwalo,moti pano mkono siukugwira ntchito.moti week yamawa timva afa mkabudula😅😅😅😅😅😅
@MosesMottah
4 сағат бұрын
Akulu mukhaliketu
@chirwaellace1093
4 сағат бұрын
Eya nkono waku manzere wapanga paralyse😅😅😅😅😅
@VictoriaBakuli
3 сағат бұрын
😂😂
@ShamimuBisani
3 сағат бұрын
Kalimdo sukunama nkhondo yafikapo panopa Iran Hezbroh Labanon ndi Palestine akuti akufuna kubwezera znse zomwe Israel yachita ku Gaza ndye kutha kwa Israel kwafika ndye anthu aja zoti Netanyahu angatumize anthu aja kunoko ndakaika mutu sukugwira Netanyahu panopa ndye zioneka
@ArchangelBanda
3 сағат бұрын
Israel shall stand forever Let's talk about zinazo koma osati kutha kwa Israel
@IssahAluba
2 сағат бұрын
😂😂 wayitulukira Dc 🙌
@vittazomba
2 сағат бұрын
Hahahahaha koma ziliko
@FatiwelloKatema
3 сағат бұрын
Tirimbikire kugwirantchito yotithandiza zikorathu
@BlessingsChipetuka
2 сағат бұрын
Ulemu upite kwa my president the DC koma mlungu ashamed nanu
@BlessingsChipetuka
2 сағат бұрын
Mlungu akudalitseni the dc
@Andygoz21
4 сағат бұрын
Zikachitika timamvera Kwa iwe DC
@ThivadoartistDyson
2 сағат бұрын
Tiyen teyen kwacha pamsei
@frankiechasokoneza5802
3 сағат бұрын
Born Kalindo the DC
@OwenYobe
3 сағат бұрын
KKkk koma DC Koma nde tiyamule ma truck awiri tikangulitse feetilizer tiwaone ngati avomele
@SostinMatchado-z2o
4 сағат бұрын
Koma DC umaseka momukweza munthu BP ase power
@AlphaPoison-u3w
2 сағат бұрын
Tchaya iweee 😂
@bridgetmajor3646
4 сағат бұрын
Koma The dc 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
@DavidKadewere
5 сағат бұрын
Mr chakwela kkkkkkkk kom ayi zikom 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@BoscoJosaya-u3r
4 сағат бұрын
The DC ❤
@PulayaKalaka
4 сағат бұрын
Proper Ganda
@JamesLongwe-qz9fd
3 сағат бұрын
Ndiwe wa chikangawa 😂😂
@TecksonKaima-dr6er
4 сағат бұрын
Mwamnyooooo auzeeee
@MosesDicostar
4 сағат бұрын
😅😅😅😅😅 born kalindo ndlibe nawe mawu paka ukusaka ndende kkkkkkk😅
@Thewarrior7093
4 сағат бұрын
No wonder nkono wake wathyoka galu wa munthu
@MarcyKamaga
4 сағат бұрын
ndipo akayiati mwatikhumudwitsa kwambiri ndipo murungu akuyendereni zowonadi mayi zukani mama chipani chathu chikutiwawa kwambiri koma chakwera murungu akurange koopya
Kalindo muuze Chakwerayo kuti dzulo lomweri Iran yayankhul pa Aljazeerah kuti yakonzeka 100% kuphulisa Israel ndye kutha kwa Benjamin Netanyahu kutha kwake kwafika panopa
@ArchangelBanda
3 сағат бұрын
Kkkk maloto chabe amenewo Israel shall stand forever
@RoseThindwa
5 сағат бұрын
Boma ili more tricks😂😂
@EvanceGilmon
3 сағат бұрын
Zazii
@SelinaGamaliyere-q8v
4 сағат бұрын
Boma la mamafia
@RebeccaFinias
5 сағат бұрын
Bambo nyoooo tsopano
@WestonGawaza
4 сағат бұрын
UTM ikalipo ndi mphavu chaka chino osasintha maudindo zinkhale mene zinaliri .MARRY chilima president Anenekuti tipange History malawi ziko lose lapasi
Пікірлер: 65