Ndipo ndizoonadi tilipo ambiri tinachokako ku Malawiko khani kulibe ndalama pano tili ndi zaka 7 panopa mu Botswana timafuna kubwera kumeneko koma kwacha yakeyo 😂😂
@FaithTricia-q5d
Ай бұрын
Ndipo zoonad sukunama the DC woyeeeee
@user-ih7li3im4s
Ай бұрын
Iweyo ndiwa mfundo kuposa manganya sure
@DannyDaka-sn2fj
Ай бұрын
Ndimalondola khani za bon kalindo nkhani zimandingila mtima koma video ndiimozi naimozi?
@thulanimpphiri6873
Ай бұрын
Munyamata opusa ndi amene akulandila 2000 ndikuononga chilungamo wachinyamata opusa ndi amene akusangalala ndi ngongole yomwe singamupindulire . Tachinyamata sitikufuna kupita kumaiko akunja tikufuna ziko lanthu mukhale ntchito tizigwira muziko mwanthu tiyeni tizuke . Opposition wamphavu kumalawi ndi DC tantiwa bakili TV kalua game changer munyanyiwa . Anthu inu muyambise chipani kumalawi kuzasintha simukufuna kubera amalawi komaso mumayima pa chilungamo. Osagulidwa ndi ndalama ngati ena.kuti president wako wamwalira mosaziwika bwino iwe 7 days ndikulandira udindo pali zeru
@Costance-nf7ue
Ай бұрын
Manganya alindinzeru chisilu cha munthu chimenechi chopanda mfundo fotseki
@PaulKanyoza-bi4xi
Ай бұрын
Uthenga wachilimbikitso ndipo watisegula maso
@user-sw8bb3iz7x
Ай бұрын
Viva kalindooooo
@Extratremendouszeus
Ай бұрын
Abon kalindo.....point of correction;Chilimatu sanali munthu wabwino ndipo balibe chabwino chomwe anachitira amalawi...km a malawi akuonetsa kut ali kumbuyo kwake chifukwa cha mmene adaphedwera ndi MCP..Km musanene kut akanasintha zinthu...he was the worst
@70878823100
Ай бұрын
IWE NDAGWIRIZANA NAWE
@CosterMustafa
Ай бұрын
The DC please kapangeni mademo lero kumangochi chifukwa chakwera walawila lero kumeneko akut akuyendara mmafamu kumeneko Ky akufuna chani😂😂😂😂Ife ctikufuna the DC ndipo pelekelani micro foni kumeneko mutiuuze zosatila💪💪💪
@user-nf3ik3ff6y
Ай бұрын
The Dc bon kalindo good Messnge ❤
@user-ns2po8ng5k
Ай бұрын
Bravo No Retreat No Surrender
@UsenLashid
Ай бұрын
Kudziva ndi kudzikuzi ndi kulalatila ena chifukwa cha ntchito yomwe umagwila zimangosonyeza umbuli Pa ntchito yakoyo, uyembekezele zinthu ziwili pa ntchito yakoyo kuchotsedwa kapena kufa,,,
Пікірлер: 37