Zimangovuta koma Hon Enock Chihana ndi wamzeru Kwambiri kuposa Chakwera and I wish next government azakhale minister of agriculture muli MZERU zakudya🔥
@worldfamous_23
Күн бұрын
Ayi akungokamba zotukula chipani osati dziko!! Incompetence singapose apa
@ZioneMkangadzula
Күн бұрын
mmm
@jacksonmaster2288
Күн бұрын
Kwambili mmmm nkuluyu ndi wanzeru
@WorriedNdhlovu
Күн бұрын
Vuto ndale za kumalawi ndi zosankhana mtundu kuyendela zigawo
Brilliant.All who are against your speech ndi mbudzi.They don't know Who you are.They don't know how democracy came to Malawi.Continue liberating Malawians.Making alliance to remove this foolish government is the only way forward.nonse amene simumva izizi ndinu agalu.
@ChrissyKandodo
Күн бұрын
Ndipo straight
@MaulanaKhalid-z4l
Күн бұрын
Salute ❤ my guy
@CharlesZisiyana
Күн бұрын
Liked his vision but unfortunately Malawians ignore such people
@timothychisambi8469
Күн бұрын
I think is the best time to give government to someone from northern region like chihana this guy is very intelligent I like his confidence n he can be a good president we have been looking for like the late Bingu..
@SolomonNjolomole
Күн бұрын
Ndakhala ndi chidwi kumvetsera za mzeru kuchokera kwa a chihana.very powerful speech.
@AyandaJanga-fe7wp
Күн бұрын
Dr chihana your speech is very important to all Malawians we are so proud of you because you are talking the main point
@billymhoni9527
20 сағат бұрын
Man who fought for this goverment is really deep in ground😢😢😢😢 My Bhiyeni
@allangerson4367
Күн бұрын
Dr Chihana mbambande much love
@GeorgeTambala-j1m
Күн бұрын
Watching from Johannesburg in south Africa we are together
@OmarManjawira-up3ns
Күн бұрын
Boma lachita misala ili😂 only facts Dr Chihana
@MavutoDytonElatonLumbe
Күн бұрын
Achitsiru awa
@ShemieMavuto
Күн бұрын
Kudana ndi zomwe akunena chinaha ndimunthu wakufa kaganizidwe@@MavutoDytonElatonLumbe
Very true and very powerful massage to all malawian nations.
@Viviennezimpita-fu6fq
Күн бұрын
Bravo Hon. Chibwana this interview has opened my eyes and 💯with you 👏👏👏
@AlbertEngelbercht
Күн бұрын
Zimangovuta koma Enock chihana ndikatundu wanzeru, Malawians let's give him chance 2025
@GraceMkandawire-t7m
Күн бұрын
Enock chihana ndakatundu mfundo yokhayo ndikumenya kugwetsa l love you speech
@DONNEXKhama-bk1gy
Күн бұрын
Bravo to enock chihanah Powerful pambuyo panu bwana
@SalimGabriel-g7n
Күн бұрын
We always cry over spilled milk. We booted out DPP because of similar issues Chihana is talking and very same people joined the Alliance and are the same akupakula mu chithumba chawochi. So don't bother that even if we put them on driving seat will do the wonders. Same fate will be falling upon us. Its very pethetic for the nation.
@makhalidwemclean1987
Күн бұрын
komasotu Malawi tizidziwan kuti ma politician expertise yawo ndi kulankhula,so akamalankhula amapanga zoti at the end of the day ndalama apange.
@thomasmember2485
46 минут бұрын
Mr Chihana powerful Speech there and you're fit to be in Government rit now
@GeorgeMughogho
Күн бұрын
Chihana I have liked your your ideology and if anything you have my vote keep up the good job and don't go astray you seem to have what Malawians are looking for. Thank you Brian for the good interview. GOD BLESS MALAWI.
@JamesChiphazi
Күн бұрын
Atupele Ali khwapa mwa mcp sangatisunge maganizidwe eke ndiongoyang,Ana mpandalama dzelu alinayo koma alindivuto losayang,Ana umphawi waamalawi anatenga maganizidwe abambo ake adyela
@LuckyMagola-x3t
Күн бұрын
Powerful speech,wise leader
@MafavukeJere
Күн бұрын
Powerful speech❤
@AustinMhone-r3s
17 сағат бұрын
what a man our problem in Malawi is regional politics we to federal system of government we hv good leaders in the country who can change Malawians life imagine Malawi is the poorest country in the world.
@joegibsonzulu2599
21 сағат бұрын
Kutsitsa mfundo zomveka. This is a trrue leader who knows what is good for the country and its citizens
@MonicaSteve-t5p
Күн бұрын
Mr chihana good speech mukuyenera kugwira ntchito ndi DPP Malawi ayenda bwino ndinu munthu oganiza kwambiri ❤
@MartinMpoya
Күн бұрын
Lets give him avote guyz akuyakhula fundo zoti zitha kusitha malawi wathu
@brendachitete6739
22 сағат бұрын
I agree with him on politicising the Mega farms issue, we are really not serious as a country.
Apm president and chihana vice president, Kabambe minister of finance,(Dpp,Aford and UTM
@SamseyHassan
14 сағат бұрын
Right guessing buddy 😊😊😊😊😊
@GodfreyKamphiripiri
2 сағат бұрын
Kaswiri kwambili Enock chihana❤❤❤❤❤
@petertaulo8014
Күн бұрын
We need people like Enock Chihana in our Government he sounds brilliant
@francismvumbe5750
Күн бұрын
I support what Mr. Chihana has been saying,
@georgemponda
Күн бұрын
Enock ndi brains zimangovuta🎉🎉
@billymhoni9527
20 сағат бұрын
I agree Enock Chihana is briliant Brains ...Malawi needs a new Leader Chakwera Is Dumb...
@MasaukoSalijeni-wb6hp
21 сағат бұрын
We need more chihanas in this country
@RaphaelMaunde
22 сағат бұрын
Bravo Hon. Chihana keep it up 💪
@Shukraanyg
21 сағат бұрын
This guy is very interagent and wise man
@ChrissyKandodo
Күн бұрын
Komatu this man eeeeee muli mzeru heavy
@HamzajOsman
Күн бұрын
❤khaniyo ndiona
@NathanLubangaKaunda
21 сағат бұрын
I really support you bwana chihana
@LesterPatrick-s2m
Күн бұрын
Ulendo uno Chihana is going to be a vice president there is a wisdom in him osati uyu amkagulitsa kuchipikuyu
@solobertkamunga2826
20 сағат бұрын
Enock Chiahana had no weight in Tonse Alliance
@billymhoni9527
20 сағат бұрын
I agree Bomaa ili was doomed from the Start...
@DjshukulanGift
Күн бұрын
MCP ndiyosavuta kuchoka even pagiraund pavuta,koma pokut akudalila Mac ndiomwe angawabere mavot kuwapasa
@MathaNamanja
Күн бұрын
Anthu ake omweomweo!just shifting from one side to another,Malawi akunvetsa Chisoni tsopano
@kingsleymsampha2260
Күн бұрын
Youths let's and all wise people let's gather here.
@alexsumani6823
Күн бұрын
Bravo Hon, brave polician , thumbs up
@ThomasSalaka
23 сағат бұрын
Make sure the alliance u will have now should have sound documents for the benefit of all parties involved and Malawian citizens.
@CliffMoyo-n7d
18 сағат бұрын
The guy is brilliant
@LuciaOsman
Күн бұрын
Enock chihana is the brilliant guy km athu ambili samazindikira zimenez
@MillieMalakam
Күн бұрын
Chihana thanks so much for your speech
@joanahwchiwangah9267
19 сағат бұрын
Mr Chihana longosokani kukwera mitengo kwa zinthu sikuno kokha ai check ⛽ prince in SA compared to 🇲🇼 then come to the table.
@victormaluwa6710
Күн бұрын
Kuyankhula mwa mphamvu Mr Chihana. Let GOD heal our Malawi
@SleepyCamera-eb1te
21 сағат бұрын
If you were wise enough, simukanapanga alliance ndi anthu amene analephera
@BennieKanama-yr3sh
Күн бұрын
Kamzingeni your right Maganizo muli nawo atati apitilira Malawi itha kusuntha
@ThomasSalaka
23 сағат бұрын
But the man is wise I can sense from his speech
@allangerson4367
Күн бұрын
Brian you are brilliant
@BlessingsManyamba-e6o
Күн бұрын
We need people like you to run the government
@ThomasSalaka
23 сағат бұрын
Chihana is light why depending on donors all the time? Timayika azitsogoreli wopanda matsomphenya,I think it's time now Malawians we need to be serious povota
Musatichedwetsa apa ,nkhani ndikumanana mipando ku tonse ndichifukwa mudachokako wooo!
@sostinjustin7447
Күн бұрын
Mwina mukuwonelano 2063 uyu Waveland chawayitiyu Ndi Dr Chihana yemwe ndi president wa afford, pomwe mu suit ya blackiyo ndi brain banda mtolankhani yemwe anatiyimilira kwa dzaka dzambili kuchokera ku time's TV 2024
@obedjere7403
Күн бұрын
Genius
@waterfallsinternational1342
Күн бұрын
Powerfully articulated....
@AmosScott-z9x
Күн бұрын
Bwana kamzingeni mwayankhulatu chilungamo chokhachokha MCP ulendo ulipo ndithu pa 16 September 2025
@VitumbikoChitetejere-g1w
Күн бұрын
Aaaaa munthuwina akungopanga ma plan wina kupanga chinthucho ndiye dolo ndani osanama pano boma ndilomweli
@paulnyondo7572
16 сағат бұрын
Boma lachita misara koma dzonati anthuwa apengatu .presdent chihana koma😂😂
@GeoffreyShariff
48 минут бұрын
inock Chihana NDI atupele muludzi ndimatha kuwonapo kena kake sogolo la ziko lathu la mkaka NDI uchi zimangowona kuvuta
@paulnyondo7572
16 сағат бұрын
Brian wavala suit yakuhunga 😂😂😂😂
@miltonkanyamula9486
3 сағат бұрын
Musatinamizepo apa . Inu a chihana ndinu munthu wongufuna kunamiza anthu . Munthu wopanda chilungamo...
@danielmagwaya1074
Күн бұрын
Ng'ona zonse tikuzithamangisira madzi 2025 Ng'ona siziyenera kukhala ku mtunda malo amodzi zitiwonongera anthu
@MercyKziphondo
Күн бұрын
Mukati boma ndilomweli mukunena boma lamanu panyini panu a mcp
@billymhoni9527
20 сағат бұрын
We are the Biggest Jockers In southern Africa..Malawi..😢😢 Shame malawi....Wina nkumati Bomaaa ndi lomweli Boma ili foreign aipeza kuti from this month to next year..😢😢😢
Kumalawi aliko anthu oti akhoza kulamulila dziko bwino ndithu ngat uyu enock chihana koma vuto amalawi timavotela munthu akakhala wa kwathu Kaya ndiopanda nzeru bola ndiwakwathu pa chifukwa ichi malawi sadzasintha chifukwa kutheka munthu yemwe akhoza kutukula malawi akuchokela komwe kuli anthu ochepa that's why malawi will never change until titakhala anthu odzindikila koma vuto umbuli 4 example ndimachokela ku mpoto koma sindingavotela munthu Kaya pot akuchokela kumpoto no timayamba taona Kaye munthuyo chifukwa even kumwela anthu azinjoya kwinaku akulila koma mbili imakhala yot kumalawi kuli mavuto
@EvanceKambewa
Күн бұрын
Mwayankhula mwa mzeru a chihana
@paulnyondo7572
15 сағат бұрын
Kamajeket anali nji njinga yakapalasa kkk.koma lero zinyumba magalimoto
Zaugalu a Chihana kodi mesa ku Mec ko muli ndima komishonala Anu inu musatinamize ife a malawi
@inessmsiyambiri8517
Күн бұрын
Eeeeee gule kwao
@vincentmapepa2940
Күн бұрын
mapwala ako ase sukudziwa kuti dzikoli lawola ndi corruption, government must do the will of malawians.
@Saeed-r3z
Күн бұрын
Ndi ntsogoleri ozichephesa ndikumuvetsa bwino bwino
@GreyMwanyimbo
Күн бұрын
Awa akanangosiya ndale
@Paworo-h5r
Күн бұрын
Aaaa chihana please kamalidzeni ka building ka pa mphompha health centre Rumphi district chiyambileni 2014 idakali pa foundation simunamalidze mumangopangila compaign chaka chilichonse mpake u mp unakanikani, khuluku number one aaaa khuluku iyii
Пікірлер: 233