Mmmm a chimwendo nenani Zina Peter musiyeni munamiza mwana chani. 2019 munatinamiza zomwezo, leronso 2024 mutiuzenso zomwezo. Mukuona ngati ndife zitsiru? Tasankha kale chisankho mu mtima mwathu odzamuvotera. Chifukwa padakali pano ngati si mukudziwa amalawi tili ku aigupto kuphula njerwa za moto. Tili pa umphawi wa nyooo. 😊
@ShillahLawrence
Сағат бұрын
Kodi Mega Farm yo ili kuti?ndiye bwenzi anthu ndi Njala?
@beatsbymcstevens
2 сағат бұрын
Pena ndumaona ngati dpp ndiyimene ili m'boma like why should a ruling party waste time arguing with opposition parties? Smh...
@MascotAnderson
2 сағат бұрын
Chakwerayi nde mumamunamizatu mpaka dziko lonse limapemphelera chakwera kkkkk
@Dorah-zl9uf
Сағат бұрын
😂😂😂😂😂
@MphatsoSoko-p3l
2 сағат бұрын
Chimwendo ndikape uziwauza anthu kuti ikupangitsa ndi devaluation kod Kutenga Ngat amalawi ndimbuli et Muthu mwagetsa ndalama ndi over 100 percent
@SelinaGamaliyere-q8v
2 сағат бұрын
Wasala pangono kufa nawenso busy kulimbana ndi dpp bas
@AshrafShadid
Сағат бұрын
Ndadutsa pa zalewa koma mmmm ndimayesa ngati pali nsonkhano wa mfumu achita kundiuza ndathu kuti ndi apule kuli nsonkhano Eshhhh boma ndi anthu ake
@Kabwilachikangawa
Сағат бұрын
@@AshrafShadid 😂😂😂😂😂😂😂
@KelvinMangwengwe
2 сағат бұрын
Chimwe you just waist your time to against with DPP
@Jacksonmuhackeya
Сағат бұрын
Ukulephela ndi masamu omwe ukunama kuti mulimi akagulisa 10bag ya chimanga akagula 10 bag ya feteleza Kodi pa k100000 paja mwasisa zonama zonse mwamaliza ndie kampeni sinayambe
@ShillahLawrence
Сағат бұрын
Kudziwa kulakhula ,lakhulani za Kuchikangawa
@IdahKadewere
2 сағат бұрын
Koma chimwendo ma comment wa muwawone muzivela chisoni zinazi umangowona waziyamba😅😅😅😅
@AmissKumakanga
2 сағат бұрын
Munyera mwayamba kufun vot ya marawi nyerowako watinamiza kwakwan
@mollymasangano473
Сағат бұрын
Kikikiikiki Mr Chinankodwa kutha mau zanyanya 😅😅 koma muma Bagula Nkuluyu.😢
@hanifahmponda8711
2 сағат бұрын
Aaaa iwe galu kwabasi ndi MCP yakoyo anthu oyipa dzedi ngati kuli chipani choyipa dzedi nde MCP imeneyi kupha kuba kupondeledza ufulu wa munthu
Chimwendo pathako pako pamoz ndi chikangawa wakoyo ndiwe galu
@BrightZionga
Сағат бұрын
Iwenso Joyce ndichisilu ukambe za ku mwanza kwanu konko ku Neno kwathu kulibe zomwe ukunenazo iya
@BrightZionga
Сағат бұрын
Kkkkkk chimwendo matumba 10 achimanga k390000 kugulira matumba atatu a fertilizer pamene nthawi ya peter mthalika anali matumba 25 a fertilizer what a shame
Пікірлер: 63