Ulemu wanu brother Ntanyiwa ifetu timakunyadirani nonse Bakili Muluzi TV ,the D.C and crew yonse pa Limpopo FM osaiwala brother Salo .DJ munyanane komaso Mr Samuel
@MEGANABIGAILMNTHALI
33 минут бұрын
Papa ntanyiwa, papa Kalindo, papa muluzi TV, brother nsalo we Love you so much our kings keep it up we will continue praying for you guys mumatiimila.
@augustMag
Сағат бұрын
Hy Mr Mtanyiwa, Bakili Muluzi TV ndi The DC Boooon Kalindo president wa aphawi nonse ndimakudyadirani MCP singamake pa Inu Ndipo kukupezani inuyo our brothers you both stay safe and blessed ❤❤❤❤❤❤❤❤
@MathewKalinkhu
50 минут бұрын
100% support brother, keep it up, atsekuleni maso a Malawi.
@Kabwilachikangawa
2 сағат бұрын
THOSE WHO LOVE LIMPOPO FM WITH COMRADE NTANYIWA LETS ALL GATHER HERE,LETS ALL SHOW SOME LOVE❤❤❤❤❤❤
@ShamimuBisani
51 минут бұрын
Welcum broh eeee koma basi bola kumapita ku Burkina Fasso kumakakhal kuli president odzindikira osati izi zoyendera jackson ngt nkhuku zachtopazi
@Dineojere
Сағат бұрын
❤ my vot DPP
@VincentChikopa-z6c
Сағат бұрын
Kkkkkk koma comred ntanyiwa ndi dolo komano osamaulura azakutolani 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤❤❤❤❤❤
@stevenmwamadi3035
3 минут бұрын
Ndi madoro team imeneyi onse the Dc bakiri muluzi TV comrade ntanyita brother salo sangawakwanisse team imeneyi ndi poison kwambili amene angamalimbane nawo azivaya yekha one buy one
@stevenmwamadi3035
25 минут бұрын
Allah alipo mpaka chilungamo tichiziwe basi akuona ngati akuchenjera koma akunama akunamizira kudwala cholinga choti thawi izidusa ndiye akuzinamiza
@KennedyPhiri-h9h
Сағат бұрын
😂😂😂😂 inu ndi dolo big man ulemu wanu
@PhilimonMasina
3 сағат бұрын
Kma mumandiwaza timu yanu mumandimvetsa kukma
@praisemtambo3140
Сағат бұрын
Mumatiyi milila❤
@Musa1828-l5d
2 сағат бұрын
Mr ntanyiwa please osayelekeza kukumana ndi Big Joe asakunamizeni apa plan imene cholinga mukhale ngati mulilimodzi kuti akupheni please samalani izi
@patrickmatabwa5828
Сағат бұрын
A kongeresi sangakukonde Ntanyiwa kkkkkk ndi awa akutukwanawa sakusowanso......
@stevenmwamadi3035
21 минут бұрын
Mr Comrade ntanyiwa Allah azikudarisanu mpaka crocodile utuluke mu boma komaso chilungom tichiziwe basi Allah adalise dziko rathu kuti chipani cha Satana cha mcp chituluke mu boma crocodile team
@MikeGomani-tb9np
Сағат бұрын
Koma bola inu a Mtanyiwa mukhale naye patali big G .Mwina ndi nyambo yoti inu muganize zokumana naye kenako azakupelekeni.😅
@Mpungwe123
3 сағат бұрын
Tinaifufuta chifukwa audio inali yosakwanira...tipepese now zonse zakonzedwa. Enjoy.
@ShamimuBisani
58 минут бұрын
Apology accpted but keep moving we r tired with this nonsense leadership may God almighty protect u guyz where u r God bless u
@DianaMmagisa
2 сағат бұрын
Big up big joe
@ChikumbutsoMaluwa
2 сағат бұрын
Ulibe zochita Zina galu iwe
@ChrissieNyasulu
2 сағат бұрын
Koma samalani Ntanyiwa sionse amati ambuye ambuye omwe akalowe ku mwamba
Пікірлер: 55