Nanga akakuonetsani ma video akalekale ndiye mudzatani kapena achitenga chimangacho ndikumangoyenda nacho koma osagawa nanso mudzikhala ngati boma lanu la mcp mumaliziwa bwino bwino simwanena kale kuti makolo anu ndi a mcp
Ukunena Kuti ulibe chipani tagonena Kuti ndiwe wa chikangawa bwanji
@MrMagombo
Күн бұрын
Pitani ku embassy ya malawi mukapange ma Demo ayaluke a Ndale.
@BittiBitti-g4t
13 сағат бұрын
Ngati Inu siwandale musatinyase
@FrancisKalavina
Сағат бұрын
Nde ukuona ngt ukunenazi zithandiza mboloso nawe iwe osamsngpanga uhule bwanji kumeneko
@NicolasKamunga-rv9vr
22 сағат бұрын
Ndi mcp ndi tambara yamweuja zichimanga timachiziwa chija ndiye tingodwa nkhuku zokhazokha opanda ufa 😂😂😂😂😂😂
@Janekapats
19 сағат бұрын
Yambanipo inunso kuthandizako basi enafe tidzibwera pambuyopotu
@HarrisonMwanga-xy4sc
17 сағат бұрын
Sinu,wa ndale koma, UTM ndi boma basi njala idzatha mcp ndi president wake chakwela atachoka.ndalama,akungotyolela mu matumba mwao ndi nduna zake for that,kulodzedwa kubela vote likubwelali mutu wa oulutsa vote yobelayo'udzadulidwa tatopa nanu uthengawu upitetso kwa ameneyo kaya atodwala kaya nkhadwala tilibe nazo munthu oipa kwambili ameneyi.
@StewartGoma
22 сағат бұрын
What happening in malawi is not good The best way is to change president who can change the life of Malawian to a better life Chakwela is surrounded with stupidly advisers Let's change leadership new president like Burkina Faso president who care more about his people
@fiskanichiumia7733
21 сағат бұрын
kugawana ndi osowa siudindo wa boma lokha ayi inuso zochepa mulinazo gawilaniko osowa kuthandizana ndi boma
@MaliGomani-z4k
23 сағат бұрын
Iwe 😂😂😂😂iwe iwe mphuvu ya hule
@WilsonFelix-j9n
23 сағат бұрын
Zoonadi chemwali
@DanielDoctor-t3p
Күн бұрын
Ena kumati boma ndi la chakwela kusaganizira moyo umene uli kunza chifukwa tikamuvotela chakwela ndithu kuli Mavuto kutsogoloku lero zili bwino si mukulandila ti 2000 sindikudana ndi chakwela ayi koma zintchito zake iiiiiiiiii Amalawi chonde tikavote mwanzeru anthu chomwe akudziwa ndi kuba
Пікірлер: 29