God bless you my president Dr Game Changer chulungamo ukuyenda ngati madzi
@user-qv4ko6ps4j
Ай бұрын
Powerful speech and APM ndi munthudi obadwa ndi u munthu kuposa mambalayi chifukwa mu leadership yake adali ndi mphamvu yolamula Asilikali kuonetsa mphamvu ku chakwela demonstrations koma adalola chakwela kupanga zofuna zake ndi a fool guy mtambo mpaka adalanda bomadi ,kod akadakhala chakwela akakhala pheeeee? Boni kalindo akuvutika kungomenyela ufulu chabe kulibwanji kuli kufuna kumulanda u president wo ngati adapangila chakwela yo kwa APM? MY VOTE FOR THE DPP (APM)
@gizzykondwani865
Ай бұрын
Good one ❤
@marryphili5419
Ай бұрын
DPP woyeeee more 🔥🔥💯
@thulanimpphiri6873
Ай бұрын
Apm or akhale okalamba koma umunthu alinawo. Sugar 500 kwacha pano 4500 kwacha just 4years hmmmm ndiye wina misala yamugwira avekere mcp oyeee kupenga or mphusi
@eliffagondewe8214
Ай бұрын
Ndipo. Ulemu wanu bwana, mwatidziwitsa pitilizani kwauza an thu coz ena anawona kale kuti chipani Chana khuma ndi mcp 2 ndipo bisalira anthu amutulukila kale satana ameneyu APM my vote🔥🔥🔥🔥
Zoona Timothy ndi mwana oputsa my vote A pm boma 2025
@AlinafeKuyenda
Ай бұрын
Zoona zake bwana simukunama
@johnkambala692
Ай бұрын
Mabodza awa
@user-op3nx5qt4q
Ай бұрын
DPP Boma 💙💙🌽🌽🌽🌽💦 💪💪 2025 it's my vote
@robertchitsulo8006
Ай бұрын
Kkkkkkk achina kuluyu timati ndani uyu wamakutu ake oimilirayi kkkkkk
@JamesChimera-hw1nv
Ай бұрын
Ungosanza ndulu ufune usafune mcp mboma 2025
@patassonelucaszovuta3431
Ай бұрын
Koma za nankhunwa zisiye adayamba zake akupanga za chipani chake inuyo dzipangani za achina namalomba
@user-qv4ko6ps4j
Ай бұрын
Member wa MCP mwana wa njoka iwe
@user-uc1pd1tc2x
Ай бұрын
Peter Munthalika ndimakina zedi size ku Malawi kulibe
@user-qb2lt6qj1p
Ай бұрын
Pitilizan mukvw
@spargomw
Ай бұрын
Ng'alurani bwana. Kosheda NDEVU kaja ulendo kazitiuza chani pa campaign? 1,000,000 job. Fertilizer 5pin.Mbuzi yamwana mchifukwa chake akungokhalira Milandu coz akuzuzitsa mizimu ya anthu osalakwa
@user-uu9pv6jd4v
Ай бұрын
Kkkkkkk mpaka Munthalika kkkkkkkk
@innocentkandulu2825
Ай бұрын
kkkkkk yes wina aliyese akhale ndi ID asabele ayi
@andrewntawanga7878
Ай бұрын
Inu anthu panopa anatopa ndikunamizidwa aliyense akudziwa kuti adzavotera ndani
@dondamissonchdziwe3958
Ай бұрын
Woima makutuyo Ndi Ken nsonda Koma akulu uyu Ndi Game changer diiee
@user-kx4og4mv5y
Ай бұрын
❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-lg6ym4hz3w
Ай бұрын
Ndipo voice ya ubusa iyi osati za ndale
@user-lw4hw9ce4w
Ай бұрын
APM ndimasasu ndipo akuzagwesa manyaka onsewa
@user-zg6mn8qr4m
Ай бұрын
Apm my vote 2025 🔥🔥
@charleslimbani8590
Ай бұрын
Player akatulusidwa mgaraundi amabwereramonsooo?????Peter anatulusidwa kale ......musaophyetsee anthu akuluuuu.... Anthu akuziwa ma weakness a Peter ngati mwapasidwa kanthu mungodya mukhare pansiiii koma Peter economy anayilepheraaa
@JafferTiles-hp4mu
Ай бұрын
Sanatulitsidwe koma anamubera ,koma poti ndi president wodekha ,nchifukwa anasiila mbavazi,,lero ndi izi tikulira nazozi mdziko mwathu momwe
@ChaibishuSwadck
Ай бұрын
It's true big mn❤
@user-lk8kj9zv6x
Ай бұрын
Dpp boma iloooo
@AleksaWilliams-qc6cn
Ай бұрын
💪💪💪💪❤️🔥❤️🔥❤️🔥❤️🔥
@user-uu9pv6jd4v
Ай бұрын
Tidzavotera yemweyo olo mukule vimau
@user-gj4li2gc8o
Ай бұрын
Iwe Mr mutholo takambako za nzeru uyu ukumukambayo tinamchosa kale takambako za nzeru
Peter analephela kale ndipo tinamchosa momuthothola
@alicemalika677
Ай бұрын
Akuba inu mumafuna muzikaba
@user-st6bt5vv9c
Ай бұрын
Nkhani niimeneyo palibeso wina amwene angatithe kuli sintha ziko koma APM NI DPP BASI Thambo wakhuta nyemba uyu siyeni adye ndalama za satanic za bushirizo ifeee amalawi tooonse ambiri tiri ku dpp nankhumwa pepani samalani chuma chanu ngati chiridi chanu SAMALANI
@JamesNsembe-eo2go
Ай бұрын
Dpp woyee
@JohnBanda-ux9fy
Ай бұрын
Zoonad big
@user-gj4li2gc8o
Ай бұрын
Anaphunzira chani peter muthalika tonsefe sitikuziwa chifukwa primary ,secondary, even college yake sitikuziwa kumene ankaphunzira kaya ma degree awa amangogula
@duncainjimmy
Ай бұрын
Komano zoti anali Lecture waku University of America mumadziwa ?
@user-uc1pd1tc2x
Ай бұрын
@@duncainjimmyAnthu asiyeni ndiopepera awaaaa Peter Munthalika ndimunthu owopsa
@andrewmandawalaphirithepillar
Ай бұрын
Inu ndi opepera eeti zoti adaphunzira pa Dedza secondary school sumaziwa?
@NgomaRaheem
Ай бұрын
Akulu inu ndi achitsilu et ediot
@MussaDisi
Ай бұрын
Iweyo kumtundu kwako komse mutati muphatikizane maphunzilo anu onse kuphatikizanso azigogo ako onse palibe chomwe mungapange oloko half ya Peter yoo simungafike komanso simuzafika
Пікірлер: 75