Bola inuyo osati garu chawezi mbuzi yamunthu sapota wa mcp otukwana amalawi
@WarezGroup
15 күн бұрын
Komanso APM BOMA 2025 Palibe WINA APM my vote
@user-du9qs4tb6u
16 күн бұрын
Koma steve konda banda uli ndi ulemu ndi amalawi osati galu chawezi kodi mwamuyitanilanji kùmibawa akufuna anthu azida ndi mibawa tv yabwino chawezi usamale usamapite pa pa tv utaledzela panya pako
@RobertLuka-wy9cl
16 күн бұрын
Chawezi awononga tv yanu galu ameneyu
@user-dp7bc7yy6s
16 күн бұрын
Inu ndiye mumaima pa chilungam km si galu uja Chawez ndi nyani wachabebr
@isaihmagani5697
15 күн бұрын
Chawezi ❤❤❤❤umatha kulankhura mwachifundo mwachisoni mwa bwino momveka bwino
@tingamasi106
15 күн бұрын
Follow how professional times tv is with it's kwagwanji and hot current osati zoyankhula ngati program mumapanga kuti muzionera nokha
@Eric-gb9ms
15 күн бұрын
Yah but forget about mcp 2025
@user-nf3ik3ff6y
15 күн бұрын
Apm boma
@ZapitaSamalani
14 күн бұрын
Akuluakulu chilungamo chiyende ngati madzi kaya wagwilidwa ndi amuna kaya akazi lamulo ligwile ntchito basi mavenda enieni amadziwa poyala katundu wawo
@user-nf3ik3ff6y
15 күн бұрын
Good message guys ❤
@marryphili5419
15 күн бұрын
I like you guys ♥️♥️♥️♥️
@Moffat-oi4yx
13 күн бұрын
Kondwa Banda ndi wabodza mukunyadila ndalama zangongole muzabweze ndinu pamodzindi ana wanu amenewo akazachokapo 2025
@geraldtuwaga-iz6ll
16 күн бұрын
Ali zunguli zunguli ntchalitchi atavala jejete Yolanda 😂😂
Ndichifukwa chake dziko la Malawi silimatukuka chifukwa Cha m, sanje ndi khaza
@jameskachulu8141
15 күн бұрын
Apm boma ine kuno ku south Africa ndi magulisa agalu koma anangondiuza malamulo amagulisidwe akhe sanandilande
@JosterDick
15 күн бұрын
Mmm koma konda Banda ndiwa mcp kuyambila kale kale nthawi imeneyo mukukhala kuchiwembe. Nde zomwe mumayakhula zopepelazi pena ife sitimadabwa nanu😂😂😂😂😂😂😂
@WarezGroup
15 күн бұрын
Zowonadi Timava kukoma Ndi mibawa t/v
@honourablemcgregorysc97tv
16 күн бұрын
Mumakwana ndi Gwedegwede
@user-sj5bl7hw4o
15 күн бұрын
Ndende ya ku south Africa akayidi amalowa mbulanda Koma anthu amalowesabe mafoni kudende
@user-hm9nc7lz6e
16 күн бұрын
Ine ndi mkona sindimavera program yanu
@francis12fombe54
16 күн бұрын
Banda banba ndakuthokodza kwambiri ife maveda
@PeterFly-mv2nq
15 күн бұрын
Koma chawezi muchose
@DaviebTembo
16 күн бұрын
Kambani zoona tifuna chilungamo
@hassammaulana4529
15 күн бұрын
Ndimadabwa ma grass a Maso alikuti
@user-xc6nl9yh4i
16 күн бұрын
Iwe umakamba chilungamo
@ThoccoBondo-mx7vt
16 күн бұрын
Mbambande inuyo
@josephgrevaxio2847
15 күн бұрын
Dpp vote
@DicksonMadula-yh6ec
11 күн бұрын
DPP My vote
@tingamasi106
15 күн бұрын
Achawezi mukuti akunyasidwa asamaonere uko nde kuononga bznes yaeni, Zina kulibwino osayankha simufa be professional my brother. Izi zomati siyani kuonerazi mmmm doesn't sound professional
Пікірлер: 38