Va police palibe vomwe vikuchita vimangodziwa kupempha ndrama pamseu ndikumanga mbava yoti anthu aigwira kare anthu eniake,ndipo vitengelepo phunziro mwina vingayambe kugwira ntchito bwino vipewa va mbalevo
@MosesShaibu-ee8hn
22 күн бұрын
Madokotalanso ali ndivutolawo munthu akumuwona ali pamzele komakungobwelawinawake wawudindo amakudusila chifukwachani winayusi munthu kodi?
@OfwaMwambila
23 күн бұрын
If u stopped by the police officers on the road in ur 🚗 .who is supposed to follow the other? 4me i don't go out to a police office who stopped me coz i had no intention of stopping.u stop me,u come to me &tell me why you stopped me not me coming to ask u
@AlasonPaulo-ht7zb
22 күн бұрын
Zoonadi Inu muli bwino kwambili
@gwatandingo9502
22 күн бұрын
Wanga kufa mwana chifukwa cha wa police wandigwira nayeso adzafera pompo ineyoso natopa nawo mbuzi zimenezo pofunika osamawanyengelera😢😢
Пікірлер: 35