Saulosi Chilima sitizamuiwala anali munthu amene anabwadwa munthu was mwayi munthu wokondweka country wide munthu wolimba mtima simple man no one like him
@dysonfysonchifundo2284
3 ай бұрын
Tidzakumbukila potipangitsa kukhulupilila Munthu olakwika nkango uli pa mpando, koma mzimu wawo uwuse mu ntendele, kungodandaula Moyo wake wapita ngati mwanapiye eish
@samuelmanda6588
3 ай бұрын
Ndidzamukumbukira chifukwa cholimba mtima kuti dziko lino ndila wina aliyense, tikhale ndi chiyembekezo kuti zinthu zisintha ndipo tsogolo lathu ndi lowala tikakhala ndi masomphenya. Kudzichepetsa kunalu mwa akulu aja mmmmmmm ayi enafe titengeteko phunziro. Experience yawo pogwira ntchito ndi ma private sector he had results oriented mindset.
@glorynkhata1185
3 ай бұрын
Kungot wamwarira imfa yosakhala bwino koma kudziko ayi amaba kwambili chitukuko amapanga ku family kwake ndi ku ma party ndi amene amamudziwa za ubwino wake ine kulibe kungot mariro sitimasekerera RIP TO ALL CRASHED IN THAT BAD ACCIDENT
Ndidzawakumbukira chifukwa sanadwale ena apanga naye njiru ndi nzeru zomwe anali nazo osati zambuli zili ku mcp ko akuuzeni tanthauzo ya democracy mchiwewa sizophana ngati nthawi ya kamuzu ayi sithani a mco ino ndi nthawi ina zosiilana za dziko izi
@MisheckChapomba-m7j
3 ай бұрын
Chitsime chija chinali chakuya now ic mmene madzi mulibemo chilima King of national unity
@georgephiri4181
3 ай бұрын
Wayifeladi mbendela ya Malawi koma Chakwela ambuye amuwone
@Shannie-uw4wm5fn8k
3 ай бұрын
Ndipo ineyo mmmm nayenda wapansi kukafika ku city center koz of this man nditsiku losaiwalika pamoyo wanga😊sleep well mr king man we shall forever remember you
@stevielee5404
3 ай бұрын
Ause mumtendele adatisinthitsa kaganizidwe
@SarahMusama-eu7wt
3 ай бұрын
Taluza anthu anzeru awili saulosi and bingu
@AmonPhiri-h4o
3 ай бұрын
Anali munthu okonda kupephere koma anthu❤❤
@SakaPrince-s8m
3 ай бұрын
Chilima was a good man than the one who is in power
@saidiBerason
3 ай бұрын
Miyambi yake monga njoka saweta
@PatrequeFanuelKaussiwa-nq9ou
3 ай бұрын
Mkulu ameneyi tidandaula kwambiri ngati munthu koma pa chitukuko anaika Malawi pa ma vuto polowetsa mcp mboma
@nkosikhonasiphiwemdlalose227
3 ай бұрын
Ine siwandale ndipo kumalawi ndinachoka ndili wachichepele komano nkhani ya Chilima yandikhunza ndipo ndalira ndikulirabe kuona mmene afela atagwila colona manja Mulungu wa moyo tichitileni chifundo nkhondo iyiyi ndinu nokha mungaikwanitse palibe chinsisi panziko
@MaryBanda-n3h
3 ай бұрын
Amen 🙌
@LeendaDeborah2005
3 ай бұрын
Kwa ine he looked so brave nthawi ya campaign but I don’t know what happened to him when he got in power. Adangoyamba kukhala zii all of the sudden. I may have never liked him that much once he got in power koma ineyo ndikudana kwambiri ndi mtundu wa imfa yomwe yamutenga. Wafa imfa yosayembekezeleka ndipo yowawilatu. Ambuye mukatamandike
@DianaChimseu
3 ай бұрын
😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@isaacbwanali4699
3 ай бұрын
Ine aChilima ndidzawakumbikila chifukwa chakudzipereka kwao potumikila dziko- komanso potumikira Yehova pamoyo wao. Mzimu wao ndi ena onse omwe adatayika, pangozi iyi yandege iwuse mumtendere waYesu ❤🎉
@DennmichSimb
3 ай бұрын
Mr Chilima was Genius man.The youth of Africa has lost the great leader.He had good visions for the country of Malawi.
Пікірлер: 53