Inuyo mulungu adzingokuonjexelani moyo wautali basi ,chifukwa mukutimvetsa kukoma
@FrynessMoyo-to2du
3 ай бұрын
Asilikari anthu ntchito yao ndi kuchinda mahule mutchesi umu😂😂
@priscillamangata4023
3 ай бұрын
Umwa chani
@DavidJackson-ox4xm
3 ай бұрын
I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa.
@JuuuKomba
3 ай бұрын
Koma iweyo pokhapa pot awagwila ndakuimikila manja mwamba athuo agwidwad
@PeterMphanza
2 ай бұрын
Nice job comred mwana wa amama kuno ku Zambia
@WatsonNtchito
3 ай бұрын
Mademo akayambire kumamfumu hotel komweko tiyeni tonse tikasokhane popo pa mfumu hotel ku ma room achulidwawo osaopa
@FrynessMoyo-to2du
3 ай бұрын
Akulu akulu mukulankhula koma sitikumva 😢
@UsenLashid
3 ай бұрын
Komaso Mr ntanyiwa musalore Kuti anthu 8 amene agwidwawo asatuluke Ayi kufikila chakwela atule pansi udindo komaso dziko la South Africa asawapange rilizi Ayi kufikila lamampho atamuzenga mulandu chakwela
@mthawisakaunda
3 ай бұрын
Akatula udindo chakwerayo, azibale ake onse azachotsedwe ntchto. Galu watitopetsa
@Hassankazembe-d3o
3 ай бұрын
May God bless you comrade Ntanyiwa
@BitonFred
2 ай бұрын
Anthu akumalawi umbuli, anachotsa peter, ati wabwino chakwera, pano akufuna peter yemwe uja, mmalawi wanzeru sakuyenera kupeleka vote ku president yemwe analephera kale, votelani atsopano osati apeter muthalika
@FrynessMoyo-to2du
3 ай бұрын
Koma chakwera wandikwana one day ndi kupedza people they call gringo
@HevenChiwaya
3 ай бұрын
Asilikali a ku Malawi ndi ogona tulo zitsilu zimalimbana ndi anthu wamba usayelekeze kuvala kabudula wa makaka ndiye amaonesa mphamvu zawo ati wavala unform yawo mbudzi
@BraghtYohane
3 ай бұрын
Ntanyiwa iweyo ndi number one radio yako timainyadira kom athu athawa ziko lili rawo kom kumeneko moto kuti buuuuu mumtimamo angokhuta mphuma lokhalokha km mulimba Ntanyiwa woyeee
@FrancisNyayi
3 ай бұрын
Apapa ndatanganidwa kuwerenga nkunvesera😂😂
@BrunoChakukuma
2 ай бұрын
Ntanyiwa woyeeeee
@EllenPhiri-xt8pt
3 ай бұрын
Kuti muone ku mcp kuli anthu osaoneka bwino okhaokha pamaso ndionyasa ndi mtima momwe
@blacksonpeshes5057
3 ай бұрын
kom mukutivetsa kukoma ndikapanda kuva uthenga kuchokela kwainu sindipuma bwino kod mudarikuti mosemunja
@MikeMerecah
3 ай бұрын
Ma activists athu musakhare chete kunoko akumangidwa mwachisisi mudziwe zimenezi, anthu osatchuka panopa Ali ku area 30 guyz,
@MathpeterLemon-ls1ns
3 ай бұрын
Pano malawi ndi North Korea 😭😭😭
@JamesIsaac-zi4kb
3 ай бұрын
Chakwela ofuna adibwe kanyenya basi
@stanleychisasa4343
3 ай бұрын
Boss mbuyomu munatiuza kuti athu aku German ofufuza ndege aja anali okonza miseu lero muti ndi aku butcher which is which Big man?
@AugustineIshmael
2 ай бұрын
Zachamba basi dikilani 2025 vote yanu ndiye nuclear power osati zabibi zanuzi
Ankolo ku malawi kulibe a silikali akanakhala kuti alipo zikuchita galu ameneyo mukumuti chokwerayu atamukhazika kale pansi, koma nawo asankha kugwirantchito ndi chipani ayiwala makamulo awo ndi mbuzi za silikali za manu pansi ndi mbuyao chakwerayo tionana chaka cha mawa onse amene akupha ndi chakwera tikhaulitsa boma ili lapita olo ataopseza motani zosatheka
@misoMoyo
3 ай бұрын
Limpopo FM ineyo ndimachedwa Ku ntchito kuti ndimvere basi nkhani ZANU mumandidalitsa ine ndi m,ngoni weni weni more fire inuyo a Mr Ntanyiwa
@mipeacemakermw9501
2 ай бұрын
Mwatukwana president 🤣🤣🤣🤣kzitem.info/news/bejne/uIh60YVurJFkZ6Asi=PkGoYsuJRKSW0v4p
Kodi inu apolice ndi asilikali ntchito yanu ndi chiyani kumalawiko? Kodi mukuyang'anila zika Zanu zikuphedwa Kodi inu ndinu apolice opanda ntchito pamodzi ndi iwe wa mkulu wa asilikali utule Pasi udindo coz your usiless man dammit asilikali inu achilungamo menyani nkhondo please
@chadreckchibwithala1493
3 ай бұрын
zinamizanani pano pa limpopo kwachwera ali pheee kukozanyasi zomwe inapanga dpp . alikuti anthu omwe agidwa aaa opusi mtanyiwa
@HalisonSolomon
3 ай бұрын
Iwe mutuwako suyenda ngati akutuma a mcp anthu akufinya ndi chakwera wakoyo ngati akupasa ndalama ulibe manyazi wekha otsutsa pano aaaaaaaa ona kolowera
@NisharChibisa
3 ай бұрын
Mumakwana
@MandalaChaona
3 ай бұрын
M C P -- Malawi Congress Party M C P = Malawi Chikangawa Party 👹👹👹🔨⚒️⛏️
@BitonFred
2 ай бұрын
😂😂😂😂
@maluli5691
3 ай бұрын
Asilikali Aku malawi ndi asilikadzi.west Africa asilikali sakunyengelela kulanda boma
@shadreckphiri1799
3 ай бұрын
If what comrade is saying is the truth,then Chakwera must be the worst president in Southern Africa.
@GeshoMwakitwile
3 ай бұрын
Nde inu mukuganiza kut olo patabwera peteryo zinthu zingasinthe foundation ya Malawi kuvuta konseko ndi chipani Cha udf olo mutatani Malawi sazasintha
Malawian kuwopa too much that’s why amakonda kulepheresa mademo so don’t tell us ngati muziwona zoti sizingatheke zochita mademo! Aaa why amakonda kulepheresa mademo
@GraceZumazuma
3 ай бұрын
Koma Malawi walowa chibwana chakwera anapita ku sukulu koma?pano akusekedwa ndi anthu akunja omwe
@ConfusedAstronaut-qv6wq
3 ай бұрын
Koma chakwera anthawa wauyouyo mbwiyache.
@SeephyMfaume
3 ай бұрын
MCP Pamtumbo pawo ndithu
@MariamAlabi-t3n
3 ай бұрын
Ku Malawi aku shooter ma movie rekani amenyane
@AnaffSayamika-uh6vg
3 ай бұрын
Chakwela ndigalu kwabasi
@RhoxinahMalamba
3 ай бұрын
Chopweteka kwambiri ndi choti ndalama za nkhani nkhani zikuthela kulipira anthu a kunja amene zomwe akuchita mudziko lathu phindu lake opindula ndi ochepa
Пікірлер: 99