Ineyo a Limpompo fm ndili pa mbuyo pano ❤❤❤❤❤ mumatiuza zoona ndithu
@FazilCastin
23 күн бұрын
Ine Langa ndi Funso Kwa inu Mr ntanyiwa Kodi Radio yanuyi imafikira anthu akumudzi. Chifukwa enafe tili ndi mwayi womvera komanso tili moyenda Monga out off country. Chifukwa akumudzi ndi amene akufunika Kuti adzidzitsata komanso ndi amene Anga Vote
@VeronicaChirwa-ct4os
23 күн бұрын
Zoonadi akumudzi akufunika azizidziwa chilungamo cheni-cheni. Ndi amene amathamanga kukavota.
@Vwalavwata
21 күн бұрын
Ndipo ndimaisata kwambiri radio imeneyi from Malawi mzimba
@JeanBanda-zy6wu
23 күн бұрын
Koma a chakwela mukuwoneka mulibe mtendere ndipo simunati mzimu wa munthu ndiwoopsa soseji mukuimva kunyung''unyatu ngati madimu musova😂😂
@MarthaMbewe-uk5nn
23 күн бұрын
A UTM mukalola manyiwo musalamo nokha mu mgwilizano wanuwo ife zikwangwani talodza kale ku DPP mutsalanaye RUTO wanuyo
@MaryNyirenda-nq3mh
23 күн бұрын
😂😂😂😂😂😂chi RUTO bwino
@user-do2cs8nf4b
23 күн бұрын
Kkkkkkk koma apatu misala yayambika😂muziwona munakhetsa mwazi wa anthu osalakwa
@Stewartchikoja
23 күн бұрын
Respect sibonda
@MaxWell-d7o
23 күн бұрын
Ine sindipitako
@BlessingKimu-yk8uj
23 күн бұрын
Moto wachilungamo tilinanu limodzi ifemso before amthu tikudziwa amthu okudana ndi chilungamo.
Respect you Ntanyiwa Kumulakwira Chilima ndiena onse anafela mundege😢😢😢
@user-ny3it3jp9l
23 күн бұрын
Lipopo❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤ fire 🔥
@georgesmart3791
22 күн бұрын
Kutha kwa Shasha... Apm 2025❤❤❤❤
@user-mh7cc8up4i
20 күн бұрын
Zinakanika kukambilana naye chilima chifukwa amaziwakuti chilima ndimuthu wachilungamo koma ngakhale mwamumpha zimu wa chilima ulamula ziko lamalawi ngakhale anachoka pakatipathu koma muchisomo chamulungu tilamulidwa ndi chilima S K C still I remember you 💔💔😭😭😭
@MandalaChaona
23 күн бұрын
Koma Malawi Chikangawa Party ikusavuka sinati . Mimbulu yoyipa iyi, Mwazi wa anthu osalakwa ukupengesani. Tiye nawo Mchimwene NTANYIWA kuwayika pambalambanda basi.
@Vwalavwata
21 күн бұрын
A khristu a CCAP ena ndi opusa amangosapota zilizonse even akuiziwa kuti akuzipereka yekha kwazigawenga kuti zimuphe
Ubwino wake mgwilizano anthu anavota zaka 5 nde zaka 5 zikatha anthu akavotanso sikuti avotelanso alliance ayi akavotela kumene akufuna kaya avotela DPP kaya avotela AFORD kaya MCP kaya UTM sikuti akavotela alliance
@user-pp6kf6vu2y
22 күн бұрын
Nyimbo yu tigairen inu❤❤
@mathewsmbaluko8522
23 күн бұрын
Zikachitika timvela kwainu ❤❤
@cacksygustarf6260
23 күн бұрын
Ntanyiwa❤
@Mrssamalanngwira
23 күн бұрын
Limpopo ❤❤❤❤ 🔥
@user-vw7tj2ss3l
23 күн бұрын
Mbiri yoipa mpaka kale kale
@FocusGeorge-qz4sh
23 күн бұрын
Yomweyo chikangawa
@InnocentNitamanMilanzi
4 күн бұрын
Ngati zinali zonama kuti anapha chilima nchifukwa chani akumamanga anthu kodi nkhani yokunamizira umalimbana nayo?ndikunama ndi iwe sataniki chilima anthu azifa ndi nhlaka chifukwa cha iwe
@GeraldChisokeza-er5cf
23 күн бұрын
Zilungamo zokhazokha
@UsenLashid
23 күн бұрын
What is that Kuti anthu akasiye matelefone uyaluka galu iwe Sunati mulungu wathu wanthu ndi wa Moyo amene anafafaniza aiguputo ndipo Lero mulungu wemweyo akufuna kufafaniza chakwela ndi chipani chake zichitike mulungu wanthu wa Moyo timakudalilani sitimadalila chakwela Ayi zichitike mudzina la yesu khristu nanuso azibusa muzayankha mulandu Kwa mulungu
@Jamesmwale-iz4ri
23 күн бұрын
Koma muti nichani
@giftwankhama9914
23 күн бұрын
Comrade mumatha.
@user-eh1mg3ww6d
23 күн бұрын
Koma chakwela sutizamuiwala ndithu muchita kusowa chiyakhula mmm ndipo watikwana
@HalisonSolomon
19 күн бұрын
KUYALUKA BOMA LA MCP KUSAFUNA KUVOMEREZA KUTI ZAWAVUTA
To honest this government it's full or shit n evil....munthu ukamayandikil kumwalira sunvaa kapena ndinene kut mbuzi ikakondwa amalonda Ali pafupi.....tionana nthawi yovotaa
@JackNagoli
23 күн бұрын
Km guys mukutinyamula 🎉
@user-sm8gx4vf1v
23 күн бұрын
Mafumu ena alibe fone aku ntcheu adziwa bwanji nanga
@SamukLungu-zg7fl
23 күн бұрын
Kurikwabwino akhirisithu apite koma ma phone awo aka wayike since azika record zose chifukwa ngati sapita sitiziwakuti akufuna kurapachani
@mellipherjohn7158
23 күн бұрын
Limpopo moto kut buuuuuu🎉🎉
@MosesKalenge
22 күн бұрын
📺📡❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤👑
@vincentbarnes5872
22 күн бұрын
Sitikufuna DPP, MCP, UDF kapena PP ayi. Tikufuna kupitiliza vision ndi passion ya Dr Saulos Klaus Chilima with UTM basi. The grace of God is upon UTM party
@DanielJuwawo
23 күн бұрын
Mantha kwambir
@GraceZumazuma
23 күн бұрын
Ali ndi tsoka chikangawa ndi banja lake mpaka kufikila m'bado wake wa chi 4 otembeleledwa ulibe mwai
@MarthaMbewe-uk5nn
23 күн бұрын
Koma ameneyu GALU kwambiri wamiyitana ndani NYANI ameneyo apite akapemphere ku Assembles kwake komweko GALUUUU!
Пікірлер: 95