Atsogoleri tikuyamikireni koma nkhani zanu simukumaliza mukaziyamba ngati mukunena kuti ntchito zomwe akugwira anthuwa ndi malipiro pa zomwe achita powotcha wa police ku Nsanje kutanthauza kuti anatumidwa ndi abomawo, ndiye a bomawo akuuzani chilungamo chotani? Inu mukadaulula zifukwa zomwe adamuwotchera wa police kuti womutumawo adziwe kuti abisala mmbatata musamangochulukisa kuseka ndi kamangoyimba nyimbo ayi, ifeyo timamvetsera ndi chidwi kuti nkhanga zaonanji tidziwe koma mumango nena molumpha lumpha ngati kuti zomwe mukuwulusa ndi zongopeka so please help us we love you
@SheenahMwalabu-iz3pr
9 ай бұрын
Ndipo message yomwe imasowa muno ndeiyiyi kkk kumatambasula bobo ngati muja apangila DC Kalindo, otherwise zikumavuta kuzitsatatu. Love you ❤❤
@user-oj5ye6bj9q
5 ай бұрын
That's true muzimalizisa nkhanizo kut tiziziwa zoona zenizeni wr real love you mr Comrade
Пікірлер: 94