Mungowadyera ndalama a UDF ndi DPP. Muzikhala ngati Bon Kalindo sachulutsa bodza chifukwa ali pa ground. Limpopo FM kuchulutsa nkhani zopeka. Anthu sakukukhulupirirani bwanji yawina MCP ku Mangochi??
@eunicesaiti
2 ай бұрын
Following bwana.
@BysonPhiri-gu4io
2 ай бұрын
Fire 🔥🔥
@swintonchirwa1897
2 ай бұрын
Keep it up big Man
@GeshoMwakitwile
2 ай бұрын
Tinakutulukani ndinu a boza
@AlgentChilanga
2 ай бұрын
Mmodzi mwa MCP ndiweyo😂 ife nganganga pambuyo pa ntanyiwa Bakili muluzi tv ndi the DC mwana wowopsya kwambiri Bon kalindo 😂😂😂
Akanawasiya a police afe ndi njala chifukwa ndi anthu opanda nzeru akukhala kumbuyo kwa mcp ndi chakwera nanga bwanji osamuuza chakwerayo awagulire chakudya , a police ndi anthu oipa
Пікірлер: 152