Amfumukazi avala Juzi ya Pilira wantchito wa amai a Sikono. 😊
@harrisonnavayah6480
Жыл бұрын
Me konda this comedy
@PaulNdalama
Жыл бұрын
Jemason wabudula mmemo wagulu
@user-cv3zw9ic6d
Жыл бұрын
Abale munthu akuganizidwayo gilin'ande komadi sananame kuti love is blind eti mumandimvetsa kukoma anthu Inu pitilizani namoyo atengana ndi Giling'ande keep it up
@AliceDandaula-ug8rj
Жыл бұрын
Namoyo mulilise mfumu kazi wataya yekha makina
@mackgozambia
Жыл бұрын
Watching from Katete Zambia
@sidreckrashid9327
Жыл бұрын
Watching from Taiwan, my warm heart of africa
@SquareBoma-vl2rj
Жыл бұрын
Komatu Banja lanu a Padela mmmm munakumana ma actors okhaokha eeeee keep fire burning guys, mumakwanira!!
@patricksinyala1345
Жыл бұрын
🤣🤣🤣 Koma amaliro ndi mwanawao eishiii
@JustenChikanda
Жыл бұрын
Afumukazi ayilira ya gili
@GOEMENGONDWE
Жыл бұрын
Padera kungoyamba motomoto 🎉🎉🎉 Basi😅😅😅😅😅
@yassinrashid7012
Жыл бұрын
Padera akufuna kunamiziranso kukomoka yeti😅😅
@user-ow3gp8uz6p
Жыл бұрын
Pabwalo tapasowa pangani zoti tikamve watch out
@maliyadaitoni
Жыл бұрын
Koma namoyo kwauza zochita mfumukazi kk
@RabeccaSaka-y3q
Жыл бұрын
Padera afera mmanja mwa anthu
@abrahamnkosi4160
Жыл бұрын
😂😂😂😂 koma farai anakonza,,,, watching from Eastern Cape tsitsikamma storms river south Africa
@HusseinMm-z3j
Жыл бұрын
Eeeee falayi anadza eeee akut stock taking
@Deajay-jn8cf
Жыл бұрын
😂😂😂😂😂
@bernadettechoma
Жыл бұрын
Ati komatu iwe ndikuwsa😅😅😅😅
@hamiltonlemilton7322
Жыл бұрын
Jemason ofunika mpini 😂😂😂😂😂
@preciousmatenje1425
Жыл бұрын
Kkkkkkkkk osakhala ndi thinking
@abdulboniface9832
Жыл бұрын
Namoyo uli bho
@user-ie4wz7cs4r
Жыл бұрын
ndimakuko ndaninose
@ethelsawerengera2140
Жыл бұрын
Banja ilinso nde likubebetsa bwanji ndaseka 😂😂😂😂😂😂
Пікірлер: 93