The DC president wa anthu osauko oyamba muno Malawi 🇲🇼 mawu akulu akoma akagonela
@ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan
3 ай бұрын
Ndikufuna number ya born Kalindo please or his group on Whatsapp ineed to thank him
@Elinalungu-wv9zu
3 ай бұрын
Eee Mungu tenda miujiza ju ya hawa watu katika jina la yesu khirsto. Atuna machaka ju yako wewe ndo mwanzo na mwisho katika jina la yesu khirsto uliye hai Amen.
@ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan
3 ай бұрын
Tiuzeni zoona ife zilipati koma ndege yasowa ilikuti mwayika nyumba
@MoosahAyami
3 ай бұрын
Dziko la malawi kupanda kukhala ndi ndege ya Emergency ndinu opusa kwambiri koma kuba ndiye number 1
@GiboSunset
3 ай бұрын
Ngati titi afe tifa chifukwa cha mbendera 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼 imeneyi!!!!!Osaoopa,Ambuye aludalitseni,(amfana oganiza bho heavy)
Born kalindo he did his best kumuchenjeza chilima kuchoka ku Mgwilizano, MCP izizi ndizo imatha, kunali amatenje, agadama anapita choncho
@GoodwellKachere
3 ай бұрын
Part of life
@wilsonfelix6559
3 ай бұрын
Bon kalindo adanena kale izi kuti mzako akukutumiza ku maiko enawa siimunthu
@BenissoneErnesto-eh6zs
3 ай бұрын
MCP zibwana ilibe yabwera kuzakhaladi eshiiiii
@chesterphiri7523
3 ай бұрын
Absolutely
@RiteRoderick
3 ай бұрын
Yabwera kuzakhala kwaniko????😂😂😂😂😂😂😂😂 Ku Lilongwe ku Nyau?
@promixphotography8056
3 ай бұрын
Boni kalindo saname kuti ziku Muno mwalowa zigawenga eti yhooo
@ChiukuseIbrahimJNapoloMakungan
3 ай бұрын
We are waiting the results of chilima here where is now ?
@cassimyusuf6683
3 ай бұрын
Dege kusowa mmawa koma osafotokoza mpaka 5 koloko, amabisa chani nthawi yonseyi
@petrokagona1708
3 ай бұрын
It has been too long. Why silent for all these hours. Vice president is one of important figures in a country. Failure to arrive at a designated place for a number of minutes, something would be done earlier than this
@agnesgwaza9165
3 ай бұрын
Anthuwa ndi zisilu mwamva or munthu kupulumukako ma hrs wonsewa ndiwopusa kwambiriii
@petrokagona1708
3 ай бұрын
Judas received money from the priests to betray Jesus. During the Last Supper, Jesus prophesied that one of the apostles would hand Him over to the priests. Judas, who was among the disciples, felt sympathy like the other apostles, even though he had the money for the deal in his pocket. He had time to repent but neglected his salvation. Later, he went to the chief priest to return the money, but it was too late-the chief priest told him that the money was no longer his concern. Overwhelmed by guilt, Judas hanged himself, losing both his life and the ill-gotten money. Sin can indeed have dramatic consequences. Let's wait and see.
@PatrickNampota
3 ай бұрын
Aha mcp ija ndi imeneyo mwina sitimaziwa kuti mcp nchiyani
@JafaliAkimu-ll1bf
3 ай бұрын
am not trust chakwera belive me this story
@JonesChingaya-yf4gg
3 ай бұрын
Lets pray for the vice president, this is so sad.
@nana-aka9ka
3 ай бұрын
What about the others
@ephraimphalawala4720
3 ай бұрын
Let's pray all are safe in Jesus name
@Jermah51kennias
3 ай бұрын
Aaaaah ukupenga iwe
@edsonphangula5817
3 ай бұрын
Country without hercopter very poor am Malawian am still here in South Africa but am disappointed very bad I pray to my God to be found
@marryphili5419
3 ай бұрын
Achilima kusamva boni Kalindo anakuchenjezani kuti muchoke kumungwiliza koma munakakamira lelo si izi zakuchipani zimenezo
@LeendaDeborah2005
3 ай бұрын
Koma ndipo Simukunama nkomwe. Adachenjezedwa kangapo ndithu
@MelvinVanRooyen
3 ай бұрын
Aboni kalindo amanenetu koma eee kaya
@HopeChipeta-i8p
3 ай бұрын
Bon kalindo tisamuphweketse amanena zoon ndipo ulemu wake
@serakillo8668
3 ай бұрын
Rest in peace chilima...phuno salota unakamvera. Born kalindo zonena zake. Iwe chilima izi tsizikanachitika ai😱😱 mzimu wake chilima uwuse mutendere chakwera wasala pang'ono naye iye afa ndi ife amalawi tisasula chakwera.
@KondwaniNguleti-x1q
3 ай бұрын
Chilima kusamva Boni Kalindo adakuuza kuti mutaye Chakwera by the way utulukemo mu Tonse Alliance lero ndi izi wakugulitsa 😂😂😂😂 Chakwera simunthu wamba
Nkhani imeneyi ndiyovuta kwambili chifukwa president amayenela akwele ndege imeneyo km chodabwitsa chakuti chakwela anakana kukwela ndegeyo why
@MwanaRosario
3 ай бұрын
Which president is this Mr. Chakwera? Since 10 am until now, the president of a country has no information about his vice president? Great spell on this president. Mia, where did it go? So open your eyes
@Omarmulanje
3 ай бұрын
Chakwela mapwala ako.waphano chilima uja
@TrezawaKondesi
3 ай бұрын
Km musayelekeze kitiphwetekela apm muzipagana a tosenu
@RiteRoderick
3 ай бұрын
Kumangokhalira kuba misonkho basi koma osamagura Hellecopter ya dziko?? Mmmmm malawi ai zikomo
@jameskachulu8141
3 ай бұрын
Akuyiva kukoma
@johnfikilini3667
3 ай бұрын
nkhani yandege yonkhayo musiyireni, hello ndi ine jaki
@TopoTopo-bm4vw
3 ай бұрын
Komatu born kalido ananena koma mumati aaa wama drama uyu ndizimezitu
@preciousedansa6898
3 ай бұрын
Ndimaganiza pastor olemekezeka Lazalo Chakwera he is very good friend of Prophet S. Buuuu ... Amene anakwanisa kugura 🛩️🛩️🛩️of expensive Jetu 😂. Na zopanga hayalazo ndiyekuti Malawi amwaliliratu now. He should supposed to ask help from prophet. I guess Kwa busa Chakwera sizikadakhala zovuta kuthandizidwa. I'm shame of myself as Malawian chokha chongova kuti dziko lathu lilibe even emergency helicopter which asilikali anthu angagwilise ntchito munyengo ngat imeney. Ooooooh Lord please bless Malawi as poor country in Africa. We have only ndege zawusiku😢🪆 even 'bomaso kumene amagwirisa malisero . Ndimadabwatu asilikali akuno ku South Africa akamati Malawi is #1 khani za nkhondo asilikali awo osaziwa amakwera malichero popita kunkhondoko. Atukuka bwanji Malawi atangozaza ndiiiii Eeeeeish ! Apezeketu koma Sawulosi. Else Lazalo.... You will explain nicely pankhani imeneyo....
@StiveriaChikonga
3 ай бұрын
🙏
@dondamissonchdziwe3958
3 ай бұрын
Ndalama zonse abazi,osagula ndenge?isakhale ngati za Iranitu
Sadick Mia beleka nyama ndi ena ambili mukufunaso musowese chili ndi kadzi wake muzatenge bwano💔
@HevenChiwaya
3 ай бұрын
Mau a kulu akoma akagonela ziziwika
@sparkdymon3429
3 ай бұрын
The DC ananatu
@kekeaufi9834
3 ай бұрын
How 🤔🤔🤔
@JosephChimaliro-ju9px
3 ай бұрын
I would love to know the one's who accompanied the VP during the trip coz the president assigned
@AlinafeTembo
3 ай бұрын
Use GPS from your 4n you can see where ndege is your 4n can show u all part of chikangawa ngati tilibe zipangizo zofufuzala mdziko Muno ndiye kuti malawi Sali safe
@ShamJali
3 ай бұрын
MCP ndi chipani cha afiti guys sadic Mia kumupha today ndi chilim
@GraceChapata
3 ай бұрын
Vice president akwera ndege bwanj imene sili kofitabo eeee
@Amgwagwa
3 ай бұрын
Zaku iran eeeeeeeeeee
@jrculdickson6629
3 ай бұрын
zayamba movuta tu paja mcp mbiri yake ndikupha zayamba basi
@Jessymsowoya
3 ай бұрын
😭😭😭😭😭😭😭 Very sad news
@FelixLivison-mk2cf
3 ай бұрын
Yes am the one who want to ask you this question Brain?
@KeddwaBenjaminMkandawire
3 ай бұрын
Ndipo ndipo wina apita wamoyo apa Izi ndi za achihana ndi aBakili nthawi imeneyo chamuma 90tens umo
Пікірлер: 252