Congratulations to Mr. Zimveka for his great acting in these all episodes. He is doing an excellent job portraying his character and the difficult situation the way character should be acting and how he is going through. Mr. Zimveka's acting feels very REAL and GENUINE. He clearly working hard to understand the role deeply and bring the character to life in a believable way. His performances have been truly impressive and engaging for us to watch. Well done, Mr. Zimveka, for your outstanding acting skills and commitment to your craft. You have set a high standard with your powerful performances bringing the comedy to real life
@ThomasiSalijeni
4 ай бұрын
Faraoooooo more 🔥🔥🔥🔥
@lovemorenaluso8965
4 ай бұрын
Farao and Chisomo ndiinu Madolo, iwe Zakhwima wati ayaya samasamala zithunzi zanu😂😂😂
Koma tu serious ngati chisomo ungaione iyi comment chisomo u are so cute ilove u chisomo
@rabsonkaunda4554
4 ай бұрын
Koma Faraoh. Akuzunzika eeeh. kuletsedwa kukwatira, kuchoka ayi koma adzikhala single. kkkkk Zimveka inuyo mmatha ndipo mmakhala serious bwana. I like your character
Atonde NSO no mutende mkhazi amene munabalekera mutengane ndi amayi akeabora Komaso chisomo amurore faraow watopaso no Komaso David abwererane ndimkhaziwake
@masasadannck4726
4 ай бұрын
Kodi chisomo program ikuiyendesa bwanji kkkk 🔥🔥🔥🔥
@jrculdickson6629
4 ай бұрын
Kwaife ife amene school yanthu tinaphunzira pa dzenje taziwa kale kuti chisomo akumukonda pharao😂😂😂😂😂koma sakufuna kuoneka ophweka kutengeraso kuti mimba ilipo kale 😂😂😂😂 pharao my blood from mulanje wawina kale miaziyo mtima pansi man imwani kae msuzi wa nyembao nyemba zeni zeni muzipeza pansi😅😅😅😅
@ElickPhiri-bf2jt
4 ай бұрын
Chisomo sankha chimodzi farao azipita or else banja liyambikepo 😂😂😂
While achina makwale, their acting style seems to be somewhat outdated and not aligned with contemporary approaches- modern life. The performances come across as overly EXAGGERATED, which may not resonate well with modern audiences accustomed to more naturalistic and subtle acting techniques. It might be beneficial for the actors to explore more realistic and grounded methods of portraying their characters, focusing on conveying genuine emotions and nuanced character development. Additionally, adapting their performances to reflect contemporary social norms and cultural sensibilities could make the characters more relatable and engaging for today's viewers
@nkhalangomultimedia
4 ай бұрын
Thanks so much and well noted
@BlessingsMakalani
4 ай бұрын
Ndizomwe ndimayembekezera kudzera kwachisomo and Farao
@AfickDaud
4 ай бұрын
Pharaoh2 ukuonda ase nkhan yake ndi chiso yemweyu? Chiso aona plan don't worry kkkk
Пікірлер: 203